Chithekitale commited on
Commit
c6c7834
·
verified ·
1 Parent(s): 8c2124c

Upload metadata.csv

Browse files
Files changed (1) hide show
  1. metadata.csv +6 -0
metadata.csv ADDED
@@ -0,0 +1,6 @@
 
 
 
 
 
 
 
1
+ Id |Raw text |normalised
2
+ 10APR10_14|Mukupitilira kumvera nkhani mwatsatanetsatane pompano pa wayilesi ya MIJ FM Koma tisanapitilile ndi nkhanizi|Mukupitilira kumvera nkhani mwatsatanetsatane pompano pa wayilesi ya MIJ FM Koma tisanapitilile ndi nkhanizi
3
+ 10APR10_15|Ndipo Mu nkhani za m’mayiko ena………… Anthu okwana makumi atatu (30) aphedwa ndi zigawenga mdziko la Nigeria.Gulu la zigawenga a mifuti, anachita chiwembu dera la Benue|Ndipo Mu nkhani za m’mayiko ena………… Anthu okwana makumi atatu (sate) aphedwa ndi zigawenga mdziko la Nigeria.Gulu la zigawenga a mifuti, anachita chiwembu dera la Benewu
4
+ 10APR10_16|lachisanu sabata latha, ndipo kafukufuku wa apolisi ali akusonyeza kuti gulu lazigawengali linaombela anthu okhala mdelali|lachisanu sabata latha, ndipo kafukufuku wa apolisi ali akusonyeza kuti gulu lazigawengali linaombela anthu okhala mdelali
5
+ 10APR10_17|Ngakhale gulu lomwe lachita za chiwembu-zi lisakudziwika, akuluakulu ati akukayikila anyamata oweta ziweto omwe akhala asakugwilizana ndi gulu lina la zifwamba dera-li|Ngakhale gulu lomwe lachita za chiwembu-zi lisakudziwika, akuluakulu ati akukayikila anyamata oweta ziweto omwe akhala asakugwilizana ndi gulu lina la zifwamba dera-li.
6
+ 12APR10_19|Akuluakulu ena a boma ati akhala akutumiza achitetezo ochuluka m’dera-li ngati njira imodzi yothetsera kusamvanaku|Akuluakulu ena a boma ati akhala akutumiza achitetezo ochuluka m’dera-li ngati njira imodzi yothetsera kusamvanaku.