Chichewa stringlengths 10 500 | emotion stringclasses 7 values |
|---|---|
Kodi umboni umenewu ndi otani umene anthu awa akupereka kukutsutsa Iwe?" | anger |
Anthu atatu onsewa anasintha chonchi chifukwa choti ankafuna kutsanzira Khristu. | neutral |
"Ndipo iye pamodzi ndi makamu ake ankhondo adadzitukumula pa dziko popanda chilungamo ndipo ankaganiza kuti iwo sadzabwelere kwa Ife. | anger |
njira yanji akuchotsedwa ku (choonadi)! | anger |
"Ndipo opani Moto umene wakonzedwa kwa (anthu) osakhulupirira. | fear |
"Tawafunsani nkhani ya mudzi umene udali m'mphepete mwa nyanja; (anthu am'mudziwo) pamene adali kuswa (lamulo la) tsiku la Sabata (lomwe adauzidwa kuti pa tsikuli asamachite usodzi wa nsomba, koma m'malo mwake azichita mapemphero okha). | disgust |
Amapereka moyo ndikupereka imfa, Mbuye wanu ndi Mbuye wa makolo anu oyamba. | neutral |
"Ndipo motero tidampatsa ulemelero Yûsuf m'dziko (la Iguputo); amakhala m'menemo paliponse pamene wafuna. | neutral |
"Ndipo munthu (wokanira) amanena: "Kodi ndikadzafa nzoonadi kuti Ndidzatulutsidwa (m'manda) nkukhala wamoyo?" | fear |
Iye anayenda nane mwamtendere ndi molungama mtima, ndipo anabweza anthu ambiri mʼnjira zawo zauchimo. | neutral |
N'zimene zinawasonkhezera kukwaniritsa zimene anachita." | neutral |
Kodi Qur'an sinadzudzule ma Arabu achikunja chifukwa | neutral |
Ngakhale kuti kukhalapo kwake monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu n'kosaoneka, umboni wake ukuoneka chifukwa cha kukwaniritsidwa kwa maulosi. | neutral |
Ndipo A'adi adaonongedwa ndi chimphepo | anger |
Ndipo iye adaitana Mbuye wake kuti: "Awa ndithu ndi anthu oipa." | disgust |
""Ndithu Allah ndiye Mbuye wanga ndi Mbuye wanunso; choncho mupembedzeni; imeneyi ndiyo njira yolunjika." | neutral |
"Ndipo kachisanu (alumbire) kuti matembelero a Allah akhale pa iye ngati (iye) ali m'modzi mwa onama. | neutral |
(Zikadzachitika zimenezi) mzimu Uliwonse udzadziwa zimene Wabweretsa (zabwino ndi zoipa). | neutral |
Kuti tithawe kuchoka mnyanja yamoto, kulibe njira ina iliyonse koma kuti maina athu alembedwe mu Buku la Moyo. | fear |
ndipo amasiyira chuma chawo anthu ena. | neutral |
"Ndipo ndithu tidasiya chizindikiro mmenemo choonekera kwa anthu anzeru. | neutral |
Atumize Mzimu Wanu, ndipo iwo adzakhala analenga. | neutral |
"Kodi saona momwe Allah ayambitsira zolengedwa, kenako nkuzibwerezanso? | disgust |
"Koma amene waopa kuti adzaimitsidwa kwa Mbuye wake (pa nthawi ya chiweruziro), adzalandira minda iwiri (yaikulu yamtendere). | fear |
"Ndipo ngati utawafunsa: "Ndani adawalenga?" | neutral |
"Ndithu Allah amakonda amene akumenya nkhondo pa njira Yake (yofalitsa chipembedzo Chake), ali pa mzere (umodzi) uku ali monga chomanga, chomangika mwamphamvu. | neutral |
"M'menemo ndi momwe tikulongosolera mokwanira zivumbulutso kuti mwina iwo angabwelere (kwa Allah). | neutral |
(Komanso) ndinasonkhanitsa anthu onse (amene ankakhala m'mizindayo) ndipo ndinawalamula kuti abwerere kumizinda yawo." | neutral |
Ndipo iwo adzakhala ndi moyo m'dziko lawo, limene ndinapatsa mtumiki wanga Yakobo. | neutral |
Koma amene angafune (zina) Kusiya zimenezi iwowo ndiwo Olumpha malire. | disgust |
Ndithu m'zimenezo muli malingaliro kwa kapolo aliyense wotembenukira (kwa Allah). | neutral |
""Ndithu ine ndikukuoperani chilango cha tsiku lalikulu." | fear |
Ndipo adzawalowetsa m'minda yomwe pansi pake pakuyenda mitsinje; adzakhala m'menemo muyaya. | neutral |
" (Zikadzachitika zimenezi) mzimu uliwonse udzadziwa zimene wabweretsa (zabwino ndi zoipa). | neutral |
Ndithudi, yemwe mudzamulowetse ku Moto ndiye kuti mwamuyalutsa, ndipo sipadzakhala athandizi kwa ochita zoipa." | disgust |
"Ndipo angelo awiriwa anadza ku Sodomu madzulo, pamene Loti adakhala pachipata cha Sodomu. | fear |
Komanso tikulimbikitsidwa ndi mawu akuti: 'Omwe aopa Mulungu adzapeza bwino.' | fear |
"Kwa yemwe mwa inu akufuna kuyenda mu njira yoongoka. | neutral |
Ndipo munthu adati kwa ena, | neutral |
Ukadzatuluka udzakhala wokalamba komanso wekhawekha." | sadness |
Qur'an inabvumbulutsidwa Mmwezi wa Ramadhan, choncho Allah anaupanga mwezi wa Ramadhan kukhala wabwino kuposa myezi yonse. | neutral |
"Ndithu Ife tidawatumizira chimphepo champhamvu choulutsa miyala (ndi kuwagenda), kupatula akubanja la Luti; tidawapulumutsa (ku chilangocho) m'bandakucha, | anger |
Thangwe nsiku za wanthu wangu, zin'dzakhala ninga nsiku za muti, ndipo omwe ndawasankhulawo, wan'dzapfatsa na mabasa yakuphatidwa na manja yawo.' | joy |
Ndipo opani Allah, dziwani kuti Allah Ngwaukali polanga. | fear |
Ine sindili chilichonse koma mchenjezi ndi wouza anthu okhulupirira nkhani zabwino." | joy |
Kumwamba kapena kwa anthu?" | neutral |
Ngati helo alidi malo ozunzirako anthu, m'pake kuopa. | fear |
"Kenako kudzanenedwa kwa amene adachita zoipa: "Lawani chilango chamuyaya! | disgust |
"Ndipo Ayah Zathu zikawerengcdwa kwa iwo zolongosola chilichonse momveka, alibe mtsutso wina koma kunena kuti: "Tibweretsereni makolo Athu (aukitseni akhale ndi moyo) ngati inu muli owona!" | anger |
""Kupatula akapolo Anu omwe ali osankhidwa (oyeretsedwa) mwa iwo. | neutral |
"Nena: "E inu amene mudapatsidwa buku! chifukwa chiyani mukuzikana zizindikiro za Allah pomwe Allah ndi Mboni wa zonse zimene mukuchita?" | fear |
Komabe, umboni wosatulutsa mawu wa zinthu zakumwamba ndi wamphamvu kwambiri. | joy |
Kotero kodi izo kutsatira kuti ife kuba, ku nyumba ya mbuye wanu, golide kapena siliva? | surprise |
Ndithu taphunzitsidwa (mpaka tikudziwa) chiyankhulo cha mbalame, ndiponso tapatsidwa chilichonse; ndithu umenewu ndiubwino wopenyeka. | neutral |
Yosefe atawaona, anazindikira kuti akuda nkhawa ndi zinazake ndipo anawafunsa kuti: "N'chifukwa chiyani nkhope zanu zili zachisoni lero?" | sadness |
Ndipo ndithu lonjezo lanu ndiloona, ndipo Inu Ndinu Woweruza mwachoonadi kuposa aweruzi onse." | neutral |
"Ndipo tidampulumutsa iye ndi anthu ake ku vuto lalikulu. | sadness |
Ngati ndinu wachinyamata ndipo mwakumana ndi zimenezi, muyenera kuganizira za Mose. | neutral |
Kodi sakuona kuti ilo (fano lawolo) silikuwalankhula ndiponso silikuwaongolera njira (yabwino?) | disgust |
"Ndithudi, taona kutembenukatembenuka kwa nkhope yako (kuyang'ana) kumwamba. | neutral |
Ambuye ali pafupi." | fear |
Choncho Mulungu anamulanga ndi matenda oopsa akhate. | sadness |
Ndipo ndithu, lonjezo lanu ndiloona, ndipo inu ndinu Woweruza mwachoonadi kuposa aweruzi onse." | neutral |
"Onse awa, (abwino ndi oipa), timawapatsa awa ndi awa mwazopatsa za Mbuye wako; ndipo zopatsa za Mbuye wako sizotsekerezedwa (kuti zisamfike kapolo Wake). | neutral |
Chonchotu, atibweretsere chizizwa monga mmene adatumiziridwa (aneneri) oyamba." | neutral |
Ameneyu ndiye mwamuwona kuti ndiye wofunika punishment? | neutral |
Taonani,"Iye anati, "Moto ndi nkhuni. | anger |
Kapena kuwadyetsa (osowa) pa masiku a njala. | disgust |
Kodi angathe kukuthandizani kapena kudzithandiza okha?" | neutral |
Mbuye wako wanena (kuti): 'Izi nzofewa kwa Ine; ndithu ndidakulenga kale pomwe iwe sudali kanthu." | neutral |
"Kamuuzeni mawu ofewa mwina akalingalira (uthengawo) kapena akaopa. | fear |
"Ndipo (Nuh) adati: "Kwerani m'menemo mwadzina la Allah mkuyenda kwake ndi mkukocheza kwake. | neutral |
Kapena kuwadyetsa (osowa) pa Masiku a njala | disgust |
Pamene muwerenga, kumbukirani ndi uthenga wa Mulungu kwa inu ngati munthu. | neutral |
"Ndipo tidawagawa iwo m'mafuko khumi ndi awiri (osiyanasiyana) monga mitundu ikuluikulu. | neutral |
mwanayo) adzamuyamwitsira (mkazi) wina, | joy |
"Ndipo mwa amene tidawalenga, alipo anthu oongolera (anzawo) ku choonadi. | neutral |
Kapena angachite mantha kuti zidzawavuta kuchita zimene Mulungu amafuna akadzabatizidwa. | fear |
N'chifukwa chiyani wangokhala wekha kupereka ziweruzo ndipo anthu onse ali chiimire pamaso pako kuyambira m'mawa mpaka madzulo?" | anger |
Atamuuza vutoli, Yesu anamuuza momveka bwino kuti: "Inu mumalambira chimene simuchidziwa." | fear |
Ndiponso sadzawayeretsa (kumachimo awo); ndipo iwo adzapeza chilango chopweteka. | sadness |
monga mawu omveka, pamene khoma limodzi limaphimbidwa; | surprise |
Ndithu ine ndikumganizira kuti ndi mmodzi wa abodza." | anger |
Mwachitsanzo, Solomo anachonderera Mulungu kuti aziyankha mapembedzero a olambira Ake. | neutral |
mwa Mulungu ine ndimadaliramo; sindidzachita mantha. | fear |
Ndipo, ndithudi, ngati pali mwamuna mu aquarium iyi. | neutral |
Iwo sayenera amafanana zovala zachimuna kapena zovala za osakhulupirira. | disgust |
"Pamene m'bale wawo (Mneneri) Hûd adawafunsa kuti: "Kodi simuopa (Allah)?" | fear |
"Kufikira pamene adzatidzera (tsiku la Qiyâma, uku akulowetsedwa ku Moto). | neutral |
Atate, ndipulumutseni Ine ku nthaŵi iyi." | fear |
"Mawa lino adzadziwa (tsiku lakuwatsikira chilango,) kuti ndiyani wabodza wodzitukumula (iwo kapena Swaleh). | neutral |
"Nena: "Yendani pa dziko ndi kuona momwe Allah adayambitsira chilengedwe; kenako Allah adzaumba, kuumba kwina. | neutral |
Chifukwa ndaona zonse zimene Labani wachita kwa inu. | disgust |
Amphaka ngati dzina lawo limveka; | neutral |
"Kotero alemekezeke Yemwe m'manja Mwake muli ulamuliro pa chinthu chilichonse; ndipo kwa Iye (ndiko) mudzabweerera nonse. | neutral |
"Zimenezo nchifukwa chakuti iwo adakonda moyo wa dziko lapansi kwambiri kuposa wa pambuyo pa imfa; ndi kutinso Allah saongola anthu osakhulupirira. | neutral |
M'nthaka muli zizindikiro kwa Otsimikiza, (Zosonyeza kuti Mulungu alipo). | neutral |
ndipo zaka za moyo wako zidzakhala zochuluka. | neutral |
Uchiteni mzinda uwu (wa Makka) kukhala wa mtendere; ndipo ndipatuleni ine ndi ana anga ku machitidwe opembedza mafano." | neutral |
Zikomo...izo anali Old School. | neutral |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.