Dataset Viewer
Auto-converted to Parquet Duplicate
audio
audioduration (s)
0.52
42.4
text
stringlengths
3
501
duration
float32
0.52
42.4
score
float64
-44.97
-0.06
ndipo yobu anayankha kuti, zoonadi, ndikudziwa kuti zimenezi ndi zoona.
9.46
-10.265566
koma munthu angathe bwanji kukhala wolungama pamaso pa mulungu?
5.38
-6.654978
ngakhale wina atafuna kutsutsana naye, iye sangamuyankhe munthuyo ngakhale mawu amodzi omwe.
7.84
-11.428797
mulungu ndi wa nzeru zambiri ndipo mphamvu zake ndi zochuluka.
5.08
-3.513787
ndani analimbana naye popanda kupwetekeka?
4.34
-2.180903
iye amasuntha mapiri, mapiriwo osadziwa, ndipo amawagubuduza ali wokwiya.
8.76
-5.225481
iye amagwedeza dziko lapansi kulisuntha pamalo pake ndipo amanjenjemeretsa mizati yake.
7.96
-9.40664
iye amayankhula ndi dzuwa ndipo siliwala; iyeyo amaphimba kuwala kwa nyenyezi.
9.24
-8.134401
ndi mulungu yekha amene anayala mayiko akumwamba ndipo amayenda pa mafunde a pa nyanja.
8.82
-2.439217
iye ndiye mlengi wa nyenyezi zamlalangʼamba ndi akamwiniatsatana, nsangwe ndi kumpotosimpita.
12.9
-12.055559
iye amachita zozizwitsa zimene sizimvetsetseka, zodabwitsa zimene sizingawerengeke.
9.68
-5.272598
akapita pafupi ndi ine sindingathe kumuona; akadutsa, sindingathe kumuzindikira.
6.8
-14.689873
ngati iye alanda zinthu, ndani angathe kumuletsa?
4.6
-3.346789
ndani anganene kwa iye kuti, mukuchita chiyani?
4.52
-2.402993
mulungu sabweza mkwiyo wake; ngakhale gulu lankhondo la rahabe linawerama pa mapazi ake.
8.38
-6.790832
nanga ine ndingathe kukangana naye bwanji?
3.54
-6.217046
ndingawapeze kuti mawu oti nʼkutsutsana naye?
4.3
-11.459249
ngakhale nditakhala wosalakwa, sindingamuyankhe; ndikanangopempha chifundo kwa woweruza wanga.
9.54
-37.159729
ngakhale ndikanamuyitana ndipo iye ndi kuvomera, sindikhulupirira kuti akanamva mawu angawo.
8.8
-34.67207
iye akanandikantha ndi mphepo yamkuntho, ndipo akanandipweteka popanda chifukwa.
8.72
-27.760382
mulungu sakanandilola kuti ndipumenso koma akanandichulukitsira zowawa.
7.92
-14.312737
tikanena za mphamvu, iye ndi wamphamvudi!
4.2
-6.310073
ndipo tikanena za chiweruzo cholungama, ndani angamuzenge mlandu?
6.04
-3.399483
ngakhale ndikanakhala wosalakwa, zoyankhula zanga zikananditsutsa; ndikanakhala wopanda cholakwa, pakamwa panga pakanandipeza wolakwa.
13.26
-34.842247
ngakhale ine ndili wosalakwa, sindidziyenereza ndekha; moyo wanga ndimawupeputsa.
7.76
-12.731842
zonse nʼzofanana; nʼchifukwa chake ndikuti, iye amawononga anthu osalakwa ndi anthu oyipa omwe.
9
-43.252918
pamene mkwapulo ubweretsa imfa yadzidzidzi, iye amaseka tsoka la munthu wosalakwayo.
9.38
-6.07876
pamene dziko lagwa mʼmanja mwa anthu oyipa iye amawatseka maso anthu oweruza dzikolo.
7.82
-10.091639
ngati si iyeyo, nanga ndani?
3.24
-2.390084
masiku anga ndi othamanga kwambiri kupambana munthu waliwiro; masikuwo amapita ine osaonapo zabwino.
9.88
-14.1373
amayenda ngati mabwato a njedza pa nyanja, ngati mphungu zothamangira nyama zoti zidye.
8.06
-19.31358
nʼtanena kuti, ndidzayiwala madandawulo anga, ndidzasintha nkhope yanga ndipo ndidzasekerera, ndikuopabe mavuto anga onse, popeza ndikudziwa kuti simudzavomereza kuti ndine wosalakwa.
16.219999
-23.745808
popeza ndapezeka kale wolakwa ndivutikirenji popanda phindu?
6.4
-20.734715
ngakhale nditasamba mʼmadzi oyera kwambiri ndi kusamba mʼmanja mwanga ndi sopo, mutha kundiponyabe pa dzala, kotero kuti ngakhale zovala zanga zomwe zidzandinyansa.
13.9
-18.503939
mulungu si munthu ngati ine kuti ndithe kumuyankha, sindingathe kutsutsana naye mʼbwalo la milandu.
9.38
-27.208384
pakanapezeka munthu wina kuti akhale mʼkhalapakati wathu, kuti atibweretse ife tonse pamodzi, munthu wina woti achotse ndodo ya mulungu pa ine kuti kuopsa kwake kusandichititsenso mantha!
18.34
-20.179951
pamenepo ine ndikanatha kuyankhula mosamuopa mulunguyo, koma monga zililimu, sindingathe.
8.9
-31.714552
koma tsopano, yehova amene anakulenga, iwe yakobo, amene anakuwumba, iwe israeli akuti, usaope, pakuti ndakuwombola; ndinakuyitanitsa mokutchula dzina lako, ndiwe wanga.
16.32
-13.909834
pamene ukuwoloka nyanja, ndidzakhala nawe; ndipo pamene ukuwoloka mitsinje, sidzakukokolola.
7.58
-6.157608
pamene ukudutsa pa moto, sudzapsa; lawi la moto silidzakutentha.
5.86
-5.672008
chifukwa ine yehova, mulungu wako, woyera wa israeli, ndine mpulumutsi wako.
6.28
-3.780488
ndinapereka igupto pofuna kuti ndiwombole iwe, ndinapereka kusi ndi seba mʼmalo mwa iwe.
7.68
-6.856777
popeza kuti ndiwe wamtengowapatali wolemekezeka ndi wapamtima panga, ndipo chifukwa ndimakukonda, ndidzapereka anthu mʼmalo mwa iwe, ndidzapereka mitundu ya anthu pofuna kuwombola moyo wako.
15.92
-20.042549
usachite mantha, pakuti ine ndili nawe; ndidzabweretsa ana ako kuchokera kummawa, ndipo ndidzakusonkhanitsani kuchokera kumadzulo.
9.62
-24.249731
ndidzawuza a kumpoto kuti, amasuleni, ndidzawuza akummwera kuti, musawagwire.
7.02
-3.722626
bweretsani ana anga aamuna kuchokera ku mayiko akutali, ana anga a akazi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi; onsewo amadziwika ndi dzina langa; ndinawalenga chifukwa cha ulemerero wanga, ndinawawumba, inde ndinawapanga.
17.82
-15.021706
tulutsa anthu amene ali nawo maso koma sakupenya, anthu amene ali nawo makutu koma sakumva.
9.38
-6.567092
abweretu ndi mboni zawo kuti adzatsimikizire kuti ananena zoona, kuti anthu ena amve ndi kunena kuti, ndi zoona.
9.32
-6.079308
yehova akunena kuti, inu aisraeli ndinu mboni zanga, ndi mtumiki wanga amene ndinakusankha, kuti mundidziwe ndi kundikhulupirira, ndipo mudzamvetsa kuti mulungu ndine ndekha.
15.24
-12.326422
patsogolo panga sipanapangidwepo mulungu wina, ngakhale pambuyo panga sipadzakhalaponso wina.
7.6
-5.989388
akutero yehova, ine, inetu ndine yehova, ndipo palibe mpulumutsi wina koma ine ndekha.
8.3
-6.39843
ndine amene ndinaneneratu, amene ndinakupulumutsa; ndine, osati mulungu wina wachilendo pakati panu amene ndinalengezeratu.
10.68
-25.311016
inu ndinu mboni zanga, kuti ine ndine mulungu, akutero yehova.
6.02
-1.781113
ine ndine mulungu kuyambira nthawi yamakedzana, ndipo ndidzakhalabe mulungu ku nthawi zonse.
6.42
-2.984262
palibe amene angathe kuthawa mʼmanja mwanga, ndipo chimene ndachita palibe angathe kuchisintha.
7.64
-5.764726
yehova akuti, mpulumutsi wanu, woyerayo wa israeli akuti, chifukwa cha inu ndidzatuma gulu lankhondo kukalimbana ndi babuloni ndi kukupulumutsani.
13.2
-23.984167
ndidzagwetsa zitseko zonse za mzindawo, ndipo kukondwa kwa anthu ake kudzasanduka kulira.
7.98
-4.85169
ine ndine yehova, woyera wanu uja, mlengi wa israeli.
5
-4.582711
ine ndine mfumu yanu.
1.9
-1.439109
yehova anapanga njira pa nyanja, anapanga njira pakati pa madzi amphamvu.
6.06
-6.751146
iye anasonkhanitsa magaleta, akavalo, gulu lankhondo ndi asilikali amphamvu, ndipo onse anagwa pamenepo, osadzukanso anazimitsidwa kutheratu ngati chingwe cha nyale.
15.38
-16.700905
yehova ameneyu akuti, iwalani zinthu zakale; ndipo musaganizirenso zinthu zimene zinachitika kale.
9.1
-10.89904
taonani, ine ndikuchita zinthu zatsopano!
2.98
-1.605354
tsopano zayamba kale kuoneka; kodi simukuziona?
4.72
-4.501631
ine ndikulambula msewu mʼchipululu ndi kupanga mitsinje mʼdziko lowuma.
6.18
-9.238358
nyama zakuthengo, nkhandwe ndi akadzidzi zinandilemekeza.
5.32
-17.16884
ndidzayendetsa mitsinje mʼdziko lowuma kuti ndiwapatse madzi anthu anga osankhidwa.
7.34
-7.804178
anthu amene ndinadziwumbira ndekha kuti aziyimba nyimbo yotamanda ine.
6.32
-20.165384
komatu simunapemphera kwa ine, inu a mʼbanja la yakobo, munatopa nane, inu aisraeli.
8.98
-4.666229
simunabweretse kwa ine nkhosa za nsembe zopsereza, kapena kundilemekeza ndi nsembe zanu.
7.5
-20.211315
ine sindinakulemetseni pomakupemphani zopereka za chakudya kapena kukutopetsani pomakupemphani nsembe zofukiza.
10.84
-16.132109
simunandigulire bango lonunkhira kapena kundipatsa ine mafuta okwanira a nsembe zanu.
7.02
-6.159363
koma inu mwandilemetsa ine ndi machimo anu ndipo mwanditopetsa ine ndi zolakwa zanu.
7.4
-8.668964
ine, inetu, ndi amene ndimafafaniza zolakwa zanu, chifukwa cha ine mwini, ndipo sindidzakumbukiranso machimo anu.
9.74
-35.452236
mundikumbutse zakale, ndipo titsutsane nkhaniyi pamodzi; fotokozani mlandu wanu kuti muonetse kuti ndinu osalakwa.
9.6
-12.706884
kholo lanu loyamba linachimwa; ndipo atsogoleri anu achipembedzo anandiwukira.
6.74
-5.433934
chifukwa chake ine ndidzanyazitsa akuluakulu a nyumba yanu ya mapemphero, ndipo ndidzapereka yakobo kuti awonongedwe ndi israeli kuti achitidwe chipongwe.
12.36
-14.941694
ndimvereni yehova ndipo mundiyankhe, pakuti ndine wosauka ndi wosowa.
5.2
-16.135967
yangʼanirani moyo wanga, pakuti ndine wodzipereka kwa inu.
4
-3.374545
inu ndinu mulungu wanga; pulumutsani mtumiki wanu amene amadalira inu.
5.88
-6.524107
inu ndinu mulungu wanga.
1.54
-5.839418
mundichitire chifundo, inu ambuye, pakuti ndikuyitana inu tsiku lonse.
5.06
-7.658508
bweretsani chimwemwe kwa mtumiki wanu, ambuye, pakuti ndimadalira inu.
6.38
-6.259902
inu ambuye, ndinu wokhululuka ndi wabwino, wodzaza ndi chikondi kwa onse amene amayitana inu.
7.54
-8.489582
yehova imvani pemphero langa; mvetserani kulira kwanga kofuna chifundo.
5.86
-14.820835
pa tsiku la mavuto anga ndidzayitana inu, pakuti inu mudzandiyankha.
5.78
-10.310166
pakati pa milungu palibe wina wofanana nanu ambuye; palibe ntchito zolingana ndi ntchito zanu.
7.2
-5.477332
mitundu yonse ya anthu imene munayipanga idzabwera ndi kudzalambira pamaso panu ambuye; iwo adzabweretsa ulemerero pa dzina lanu.
11.34
-18.772198
pakuti ndinu wamkulu ndipo mumachita zodabwitsa; inu nokha ndiye mulungu.
6.14
-8.116363
ndiphunzitseni njira yanu yehova, ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu; patseni mtima wosagawikana kuti ndilemekeze dzina lanu.
10.56
-41.37598
ndidzakutamandani ambuye mulungu wanga, ndi mtima wanga wonse; ndidzalemekeza dzina lanu kwamuyaya.
7.62
-12.131342
pakuti chikondi chanu nʼchachikulu kwa ine; mwandipulumutsa ku malo ozama a manda.
6.68
-11.519662
inu mulungu wanga, anthu odzikuza akundithira nkhondo; anthu ankhanza akufuna kundipha, amene salabadira za inu.
11.6
-13.544672
koma ambuye ndinu mulungu wachifundo ndi wokoma mtima, wosakwiya msanga, wodzaza ndi chikondi ndi wokhulupirika.
9.9
-12.93224
tembenukirani kwa ine ndipo ndichitireni chifundo; perekani mphamvu zanu kwa mtumiki wanu ndipo pulumutsani mwana wa mdzakazi wanu.
12.62
-16.678186
mundionetse chizindikiro cha ubwino wanu kuti adani achione ndi kuchititsidwa manyazi, pakuti yehova mwandithandiza ndi kunditonthoza.
11.86
-17.971775
mayiyo ananyamuka nachita zimene munthu wa mulungu ananena.
5.68
-5.135348
iye pamodzi ndi banja lake anachoka nakakhala ku dziko la afilisti zaka zisanu ndi ziwiri.
7.78
-6.170766
zitatha zaka zisanu ndi ziwirizo anabwera kuchokera ku dziko la afilisti ndipo anapita kwa mfumu kukafunsa za nyumba yake ndi munda wake.
12.38
-8.123016
ndipo mfumu inkayankhula ndi gehazi, mtumiki wa munthu wa mulungu kuti, tandiwuza zinthu zikuluzikulu zimene elisa wachita.
12.74
-10.751536
End of preview. Expand in Data Studio

BibleTTS Chichewa — Aligned Bible Speech

116.1 hours of studio-quality, single-speaker Chichewa Bible narration, segmented and force-aligned at verse level into 45,728 clips (24 kHz, mono, WAV).

Languages

Dataset Structure

Audio is stored in the audio column (HuggingFace Audio feature). Parquet shards live under data/read/, one file per split.

from datasets import load_dataset

ds = load_dataset("CLEAR-Global/BibleTTS-Chichewa", "read", split="train")
field description
audio The clip. audio.path is the source file name, <BOOK>_<chapter>_<segment>.wav.
text Verse transcript, lowercase.
duration Clip duration in seconds.
score Alignment confidence for the clip (see below).

Statistics

split clips hours median / p95 duration (s)
train 40,150 100.81 8.2 / 17.8
dev 249 0.76 10.5 / 21.0
test 117 0.38 11.2 / 23.7
other 5,212 14.15 7.2 / 26.6
total 45,728 116.10 8.1 / 18.8

The corpus has a single speaker (one recording voice) and no speaker or demographic metadata.

Splits and the Alignment Score

Each clip carries a score from the forced aligner: the alignment confidence for that clip, expressed as an average per-token log-probability. Values are negative; higher is better. It is length-normalised, so long and short clips are comparable, and it is not correlated with clip duration or transcript length.

Every clip is published in one of four splits. Nothing is discarded:

  • train / dev / test — the cleaned set (40,516 clips, 101.95 h). A clip is included only if it passes both filters:
    1. score > -45 — alignment considered reliable; and
    2. no numerals in the transcript — Chichewa verse text containing figures ("…wa zaka '32'…") is kept out of the training splits because the numbers are spoken as words and do not match a plain-text transcript.
  • other — the 5,212 clips (14.15 h) excluded by those filters; not intended for TTS training as-is.

Dataset Creation

BibleTTS's Chichewa subset was published as unaligned chapter-level audio from Open.Bible released by Biblica. This release is the CLEAR Global verse-level segmentation of those recordings: each chapter was split into per-verse clips and force-aligned against the Chichewa Bible text, which yielded the per-clip transcripts, durations and alignment scores used here. Clips are 24 kHz mono PCM WAV.

Caveats

  • Single speaker, Bible-domain vocabulary: not representative of everyday spoken Chichewa.
  • Verse-level segmentation follows the Bible text; some clips are verse fragments, so transcripts are not always complete sentences.
  • The other split is deliberately unfiltered and therefore contains misaligned clips and transcripts with numerals.

Citation

@inproceedings{meyer22c_interspeech,
  title     = {{BibleTTS: a large, high-fidelity, multilingual, and uniquely African speech corpus}},
  author    = {Josh Meyer and David Adelani and Edresson Casanova and Alp Öktem and Daniel Whitenack and Julian Weber and Salomon {KABONGO KABENAMUALU} and Elizabeth Salesky and Iroro Orife and Colin Leong and Perez Ogayo and Chris {Chinenye Emezue} and Jonathan Mukiibi and Salomey Osei and Apelete AGBOLO and Victor Akinode and Bernard Opoku and Olanrewaju Samuel and Jesujoba Alabi and Shamsuddeen Hassan Muhammad},
  year      = {2022},
  booktitle = {{Interspeech 2022}},
  pages     = {2383--2387},
  doi       = {10.21437/Interspeech.2022-10850},
  issn      = {2958-1796},
}

@inproceedings{derenzi-etal-2025-synthetic,
  title     = "Synthetic Voice Data for Automatic Speech Recognition in {A}frican Languages",
  author    = "DeRenzi, Brian and Dixon, Anna and Farhi, Mohamed Aymane and Resch, Christian",
  booktitle = "Proceedings of the First Workshop on Advancing {NLP} for Low-Resource Languages",
  month     = sep,
  year      = "2025",
  address   = "Varna, Bulgaria",
  publisher = "INCOMA Ltd., Shoumen, Bulgaria",
  url       = "https://aclanthology.org/2025.lowresnlp-1.16/",
  pages     = "152--186"
}

Contact

CLEAR Global — tech@clearglobal.org

Acknowledgments

Verse-level alignment and packaging by CLEAR Global, continuing the Masakhane BibleTTS collaboration. Original recordings from the Open.Bible project by Biblica.

License

CC BY-SA 4.0 (SPDX: cc-by-sa-4.0)

Downloads last month
54