audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Apatu maiyu anafuula kufunafuna thandizo ndipo ali mkati molimbana ndi motowu anaona Kadzuwa akuthawa. Atamugwira malingana ndi Chatsira, Kadzuwa anatengeledwa ku polisi komwe anakamutsekera
Apatu maiyu anafuula kufunafuna thandizo ndipo ali mkati molimbana ndi motowu anaona Kadzuwa akuthawa. Atamugwira malingana ndi Chatsira, Kadzuwa anatengeledwa ku polisi komwe anakamutsekera
Female
ndipo atamutengera ku bwalo la milandu, anaukana mlanduwu zomwe zinachititsa mbali ya boma kubweretsa mboni zitatu zomwe zinatsimikizira za nkhaniyi
ndipo atamutengera ku bwalo la milandu, anaukana mlanduwu zomwe zinachititsa mbali ya boma kubweretsa mboni zitatu zomwe zinatsimikizira za nkhaniyi
Female
Apa oweruza Kingsley Buleya anagamula mkuluyu kukakhala ku ndende kwa zaka zitatu kuti ena atengerepo phunziro
Apa oweruza King’isile Buleya anagamula mkuluyu kukakhala ku ndende kwa zaka zitatu kuti ena atengerepo phunziro
Female
George Kadzuwa ndi wa m’mudzi mwa mfumu yaikulu Phambala m’boma la Ntcheu. Bwalo la Milandu la Rumphi First Grade Magistrate lalamula Dikiso Chirambo kukakhala ku ndende kwa zaka 7 kaamba kopezeka olakwa pa mlandu oluma khutu la mzake
Joji Kadzuwa ndi wa m’mudzi mwa mfumu yaikulu Phambala m’boma la Ntcheu. Bwalo la Milandu la Rumphi fesiti giledi majesitileti lalamula Dikiso Chirambo kukakhala ku ndende kwa zaka seveni kaamba kopezeka olakwa pa mlandu oluma khutu la mzake
Female
yemwe anali ndi ngongole ya ndalama zokwana K300. Oyimira boma pa mlanduwu, Kelvin Ng’ambi anawuza bwalo la milandu kuti Chirambo wazaka 34 zakubadwa anapalamula mlanduwu Mwezi wa January chaka chino
yemwe anali ndi ngongole ya ndalama zokwana filli handiledi kwacha. Oyimira boma pa mlanduwu, Keovini Ng’ambi anawuza bwalo la milandu kuti Chirambo wazaka fete folo. zakubadwa anapalamula mlanduwu Mwezi wa Januwale chaka chino
Female
Malingana ndi a Ng’ambi, Chirambo analuma khutu la nzakeyu Khima Chirambo kaamba ka m’kwiyo atalephera kubweza ndalamayo
Malingana ndi a Ng’ambi, Chirambo analuma khutu la nzakeyu Khima Chirambo kaamba ka m’kwiyo atalephera kubweza ndalamayo
Female
Atatengeredwa ku bwalo la Milandu, Chirambo anawukana mlandu oluma komanso kuvulaza munthu zomwe zinapangitsa Oyimira boma pa milandu kobweretsa mboni zomwe zinatsimikizira mlanduwu
Atatengeredwa ku bwalo la Milandu, Chirambo anawukana mlandu oluma komanso kuvulaza munthu zomwe zinapangitsa Oyimira boma pa milandu kobweretsa mboni zomwe zinatsimikizira mlanduwu
Female
Ndipo, popereka chigamulo chake Oweruza mlandu, Cuthbert Phiri anati Chirambo anawonetsa khalidwe la chinyama poluma nzake kaamba ka ngongole ya 300 kwacha chomcho akuyenera kukakhala ku ndende
Ndipo, popereka chigamulo chake Oweruza mlandu, kafubeti Phiri anati Chirambo anawonetsa khalidwe la chinyama poluma nzake kaamba ka ngongole ya fili handiledi kwacha chomcho akuyenera kukakhala ku ndende
Female
Dikiso Chirambo ndi wa m’mudzi mwa Kaulanda m’dera la mfumu yaikulu Mwahenga m’boma la Rumphi
Dikiso Chirambo ndi wa m’mudzi mwa Kaulanda m’dera la mfumu yaikulu Mwahenga m’boma la Rumphi
Female
Mai wina yemwe amagwira ntchito ya mnyumba ku Chilomoni mu mzinda wa Blantyre manja ali ku nkhongo atamuchotsa ntchito kaamba kouza abwana ake kuti awerenge ndiwo za matemba monga amachitira nthawi zonse akamaphika nyama
Mai wina yemwe amagwira ntchito ya mnyumba ku Chilomoni mu mzinda wa Bulantaya manja ali ku nkhongo atamuchotsa ntchito kaamba kouza abwana ake kuti awerenge ndiwo za matemba monga amachitira nthawi zonse akamaphika nyama
Female
Nkhaniyi ikuti abwana a maiyu akhala akuwerenga kuchuluka kwa ziwalo za nyama yomwe alamula kuti wa ntchitoyu aphike koma izi sizimasangalatsa maiyu
Nkhaniyi ikuti abwana a maiyu akhala akuwerenga kuchuluka kwa ziwalo za nyama yomwe alamula kuti wa ntchitoyu aphike koma izi sizimasangalatsa maiyu
Female
Malipoti akuti tsiku lina abwanawa atalamula kuti pakhomopo paphikidwe matemba, maiyu anawaitana kuti azawerenge kuchuruka kwa matembawo asanayambe kuphika
Malipoti akuti tsiku lina abwanawa atalamula kuti pakhomopo paphikidwe matemba, maiyu anawaitana kuti azawerenge kuchuruka kwa matembawo asanayambe kuphika
Female
zinthu zomwe zinakwiyitsa abwanawo ndipo anamula kuti wa ntchitoyo achoke. Pakadali pano Ndirande FM yamvetsedwa kuti nkhaniyi yafika ku ofesi yoona za ufulu wa anthu ogwira ntchito, labor office pa chingerezi
zinthu zomwe zinakwiyitsa abwanawo ndipo anamula kuti wa ntchitoyo achoke. Pakadali pano Ndirande rfuemu yamvetsedwa kuti nkhaniyi yafika ku ofesi yoona za ufulu wa anthu ogwira ntchito, leba ofesi pa chingerezi
Female
Mtsogoleri oyamba wa dziko Zambia Dr. Kenneth Kaunda wamwalira ali ndi zaka 97 zakubadwa. Kaunda, yemwe analamulira dziko la Zambia kuchokera chaka cha 1964 mpaka 1991
Mtsogoleri oyamba wa dziko Zambia Dokota kenefi Kaunda wamwalira ali ndi zaka nainte seveni zakubadwa. Kaunda, yemwe analamulira dziko la Zambia kuchokera chaka cha naintini sikisite folo mpaka naintini nainte wani
Female
wamwalira pa chipata china mu mzinda wa Lusaka atadwala kwa nthawi yochepa. Tiuzeni Maganizo Anu. Akhiristu komanso Asilamu m’dziko muno
wamwalira pa chipata china mu mzinda wa Lusaka atadwala kwa nthawi yochepa. Tiuzeni Maganizo Anu. Akhiristu komanso Asilamu m’dziko muno
Female
asayinirana m’gwilizano oyamba kulora ophunzira a chipembedzo cha chisilamu kuvala chovala chotchedwa Hijab pa nthawi ya maphunziro
asayinirana m’gwilizano oyamba kulora ophunzira a chipembedzo cha chisilamu kuvala chovala chotchedwa Hijabu pa nthawi ya maphunziro
Female
Mphunzitsi wina Dickson Lanjesi wa zaka 27 wayamba kugwira ukayidi wa zaka zinayi bwalo la Milandu litamupeza pa mlandu omenya ndi kuvulaza mkazi wake wakale
Mphunzitsi wina Diksioni Lanjesi wa zaka twente seveni wayamba kugwira ukayidi wa zaka zinayi bwalo la Milandu litamupeza pa mlandu omenya ndi kuvulaza mkazi wake wakale
Female
Mtsogoleri wa mpingo wa Synagogue, Church of All Nations (SCOAN), TB Joshua wamwalira. Tsamba la Facebook la TB Joshua Ministries latsimikiza za nkhaniyi lero ku m'mawaku
Mtsogoleri wa mpingo wa Ssunagogi, tchetchi ofu oneshonzi (SIKOWANI), Tibi Joshuwa wamwalira. Tsamba la Fesibuku la Tibi Joshuwa Minisitilezi latsimikiza za nkhaniyi lero ku m'mawaku
Female
Ndirande FM yagwira mau pa tsambali omwe akuti Mulungu watenga mzakazi wake, TB Joshua monga mwakufuna kwake. Ntchito yake yonse pano pa dziko la pansi inali yotumikira Mulungu
Ndirande efuemu yagwira mau pa tsambali omwe akuti Mulungu watenga mzakazi wake, Tibi Joshuwa monga mwakufuna kwake. Ntchito yake yonse pano pa dziko la pansi inali yotumikira Mulungu
Female
Komatu tsatanetsatane wa chomwe chadzetsa imfa TB Joshua yemwe wamwalira ndi zaka 57 sichikudziwika kufikira Pano
Komatu tsatanetsatane wa chomwe chadzetsa imfa Tibi Joshuwa yemwe wamwalira ndi zaka ffite seveni sichikudziwika kufikira Pano
Female
Nkhawa yakuchepa kwa chitetezo yakula pakati pa anthu okhala m'madera a Chitawira, Nkolokosa, New Naperi komanso Madera ena oyandikana nawo pomwe malipoti akuonetsa kuti umbava ndi umbanda ukukula kwambiri
Nkhawa yakuchepa kwa chitetezo yakula pakati pa anthu okhala m'madera a Chitawira, Nkolokosa, Nyu Naperi komanso Madera ena oyandikana nawo pomwe malipoti akuonetsa kuti umbava ndi umbanda ukukula kwambiri
Female
Nkhawazi zaululika pa mkumano wa pakati pa akuluakulu a chitetezo, atsogoleri a m'maderawa komanso apolisi omwe pakadali pano uli mkati pa sukulu ya Chitawira Primary
Nkhawazi zaululika pa mkumano wa pakati pa akuluakulu a chitetezo, atsogoleri a m'maderawa komanso apolisi omwe pakadali pano uli mkati pa sukulu ya Chitawira Pulaimale
Female
Poyankhula pa mkumano-wu, akuluakulu a za chitetezo-wa anati alandira malipoti ochuruka okhuza kubedwa kwa Katundu, kumenyedwa ngakhale kuphedwa kwa anthu kumene
Poyankhula pa mkumanowu, akuluakulu a za chitetezowa anati alandira malipoti ochuruka okhuza kubedwa kwa Katundu, kumenyedwa ngakhale kuphedwa kwa anthu kumene
Female
Adindowa aloza dzala anthu ena ochita ntchito za malonda ang'onoang'ono mmisewu ya maderawa ponena powaganizira kuti akukhuzidwa ndi izi
Adindowa aloza dzala anthu ena ochita ntchito za malonda ang'onoang'ono mmisewu ya maderawa ponena powaganizira kuti akukhuzidwa ndi izi
Female
Anthuwa apempha apolisi kuti akhazikitse njira zatsopano zokhwimitsira chitetezo pofuna kuti mchitidwewu utheretu
Anthuwa apempha apolisi kuti akhazikitse njira zatsopano zokhwimitsira chitetezo pofuna kuti mchitidwewu utheretu
Female
Anthu a m’mudzi mwa Matope ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre mawa alonga a Raphael Mzunga kukhala gulupu Matope
Anthu a m’mudzi mwa Matope ku Ndirande mu mzinda wa Bulantaya mawa alonga a lafaelo Mzunga kukhala gulupu Matope
Female
A Mzunga azozedwa pa udindowu kutsatira imfa ya omwe anali mfumu Matope, a Andisen Ramzy omwe anamwalira pa 13 August chaka chatha
A Mzunga azozedwa pa udindowu kutsatira imfa ya omwe anali mfumu Matope, a Andiseni Ramuze omwe anamwalira pa fetini ogasiti chaka chatha
Female
Poyankhula ndi Ndirande FM kuchokera ku likulu la banja la Matope, a Mzunga omwe akuzozedwa mawali anati zokonzekera zonse za mwambowu zili mchimake ndipo ndondomeko zopewera COVID-19 zitsatidwa
Poyankhula ndi Ndirande efuemu kuchokera ku likulu la banja la Matope, a Mzunga omwe akuzozedwa mawali anati zokonzekera zonse za mwambowu zili mchimake ndipo ndondomeko zopewera Kovidi-naintini zitsatidwa
Female
Mfumuyi yati kuzazodwa kwake kupereka mangolomera oti ipitirize ntchito za chitukuko zomwe inayamba kale kugwira itangosankhidwa ndi a ku banja kuti ilowe m'malo mwa malemu Gulupu Matope
Mfumuyi yati kuzazodwa kwake kupereka mangolomera oti ipitirize ntchito za chitukuko zomwe inayamba kale kugwira itangosankhidwa ndi a ku banja kuti ilowe m'malo mwa malemu Gulupu Matope
Female
A Raphael Mzunga akhala mfumu Matope ya chisanu ndi chimodzi kuchokera pomwe mfumu yoyamba ya m'mudziwu, Chomboto Matope inayamba kutsogolera anthu a mmudzimu
A lafaelo Mzunga akhala mfumu Matope ya chisanu ndi chimodzi kuchokera pomwe mfumu yoyamba ya m'mudziwu, Chomboto Matope inayamba kutsogolera anthu a mmudzimu
Female
Mnyamata wina wa m’mudzi wa Kasale m’dera la mfumu yaikulu Mpando m'boma la Ntcheu wathawa pa chikamwini zitaululika kuti wakhala akujambula malo obisika a apongozi ake koma iwo asakudziwa
Mnyamata wina wa m’mudzi wa Kasale m’dera la mfumu yaikulu Mpando m'boma la Ntcheu wathawa pa chikamwini zitaululika kuti wakhala akujambula malo obisika a apongozi ake koma iwo asakudziwa
Female
Malawi ochuluka omwe amakhala m'dziko la South Africa akupitilira kubwerera kuno ku mudzi ati Kaamba ka ka zotsatira za mliri wa COVID-19
Malawi ochuluka omwe amakhala m'dziko la saufi afilika akupitilira kubwerera kuno ku mudzi ati Kaamba ka ka zotsatira za mliri wa kovidi-naintini
Female
Izitu ndi malingana ndi mneneri wa chipata Cha Mwanza, Pasqually Zulu yemwe watiuza kuti anthuwa abwera kuno ku Mudzi potengera kuti Ali m'dziko la South Africa, Moyo wakhala uli ovuta
Izitu ndi malingana ndi mneneri wa chipata Cha Mwanza, Pasikwale Zulu yemwe watiuza kuti anthuwa abwera kuno ku Mudzi potengera kuti Ali m'dziko la saufi afilika, Moyo wakhala uli ovuta
Female
Dzulo lachinayi, chipatachi chalandira anthu 666 omwe afika m'dziko muno kuchokera ku South Africa Komwe anapita pokafunafuna moyo wabwino
Dzulo lachinayi, chipatachi chalandira anthu sikisi handiledi andi sikisite sikisi omwe afika m'dziko muno kuchokera ku saufi afilika Komwe anapita pokafunafuna moyo wabwino
Female
Boma labwezeretsa pa ntchito mabwanamkubwa 27 komanso akuluakulu ena okwana 7 omwe linawaimitsa miyezi yapitayo
Boma labwezeretsa pa ntchito mabwanamkubwa twente seveni komanso akuluakulu ena okwana seveni omwe linawaimitsa miyezi yapitayo
Female
ndi cholinga chofuna kuwafufuza pa momwe anayendetsera gawo la ndalama zokwana K6. 2 billion zomwe makhonsolo analandira zolimbanirana ndi mliri wa COVID-19
ndi cholinga chofuna kuwafufuza pa momwe anayendetsera gawo la ndalama zokwana sikisi pointi thu biliyoni kwacha zomwe makhonsolo analandira zolimbanirana ndi mliri wa Kovidi-naintini
Female
Mneneri mu unduna wa maboma aang'ono, Anjoya Mwanza wati ofesi ya mtsogoleri ndi nduna Ndi yomwe yalangiza unduna wawo kuti ibwezeretse pa ntchito mabwanamkubwawa
Mneneri mu unduna wa maboma aang'ono, Anjoya Mwanza wati ofesi ya mtsogoleri ndi nduna Ndi yomwe yalangiza unduna wawo kuti ibwezeretse pa ntchito mabwanamkubwawa
Zitamveka kuti ndalama za mliri wa COVID-19 zinasakazidwa, President Lazarus Chakwera anati boma lake lithana ndi mdindo aliyense yemwe apezeke kuti akukhuzidwa ndi izi
Zitamveka kuti ndalama za mliri wa Kovidi-naintini zinasakazidwa, pulezidenti lazalasi Chakwera anati boma lake lithana ndi mdindo aliyense yemwe apezeke kuti akukhuzidwa ndi izi
Female
Kupatula kuimitsa mabwanamkubwawa, a Chakwera anachotsanso Dr. John Phuka
Kupatula kuimitsa mabwanamkubwawa, a Chakwera anachotsanso Dokota. Joni Phuka
Female
Mkuluyu amachokera m’mudzi wa Makwani, mfumu yayikulu Dzoole m’boma la Dowa. Maanja okwana 1,000 ku Chatoloma ndi madera ena ku Kasungu
Mkuluyu amachokera m’mudzi wa Makwani, mfumu yayikulu Dzoole m’boma la Dowa. Maanja okwana wani sauzande ku Chatoloma ndi madera ena ku Kasungu
Female
tsopano atuluka mu nsinga za vuto la kusowa kwa madzi limene linayambaa mphasa kwa nthawi yayitali m’madera ambiri m’bomali
tsopano atuluka mu nsinga za vuto la kusowa kwa madzi limene linayambaa mphasa kwa nthawi yayitali m’madera ambiri m’bomali
Female
Sithole wauza Times 360 Malawi kuti anayamba malonda ogulitsa madzi pofuna kuchepetsa vuto la kusowa kwa madzi komanso kuti anthu azimwa madzi otetezedwa
Sithole wauza Taimusi fili sikisite Malawi kuti anayamba malonda ogulitsa madzi pofuna kuchepetsa vuto la kusowa kwa madzi komanso kuti anthu azimwa madzi otetezedwa
Female
Moffat Kajekeko ndi m’modzi wa makasitomala a kampani ya Sithole ndipo akuyikira umboni kuti banja lake tsopano likugwiritsa ntchito madzi a ukhondo
Mofati Kajekeko ndi m’modzi wa makasitomala a kampani ya Sithole ndipo akuyikira umboni kuti banja lake tsopano likugwiritsa ntchito madzi a ukhondo
Female
Akazi anga amadzuka m'cha mma wani koloko usiku kukasaka madzi, komanso madzi ake sanali otetezeka. Koma kaamba ka kubwera kwa kampaniyi, vuto la kusowa kwa madzi pano ndi mbiri ya kale
Akazi anga amadzuka m'cha mma wani koloko usiku kukasaka madzi, komanso madzi ake sanali otetezeka. Koma kaamba ka kubwera kwa kampaniyi, vuto la kusowa kwa madzi pano ndi mbiri ya kale
Female
Wayilesi ya BBC m'dzikolo yati Mfumu Charles ikudwala matenda okhudza njira yotayira madzi ndipo mfumuyi ikhala ikulowa m'chipatala posachedwa kuti akayipime
Wayilesi ya Bibisi m'dzikolo yati Mfumu Tchalosi ikudwala matenda okhudza njira yotayira madzi ndipo mfumuyi ikhala ikulowa m'chipatala posachedwa kuti akayipime
Female
A Charles analowa ufumu mai awo Elizabeth atamwalira. Mfumukazi Elizabeth yachiwiri inakhala pa mpandowu kwa zaka 70. A Charles anawalonga ufumu pa 6 May 2023
A tchalosi analowa ufumu mai awo Elizabefi atamwalira. Mfumukazi Elizabefi yachiwiri inakhala pa mpandowu kwa zaka sevente. A Charles anawalonga ufumu pa 6sikisi meyi twente twente fili
Female
Ena akuti matimu a mpira azikhala ndi sing’anga ngati akufuna kupambana pa masewero, pomwe ena akuti mankhwala sagwira ntchito mu mpira ndipo n’zotayitsa nthawi chabe
Ena akuti matimu a mpira azikhala ndi sing’anga ngati akufuna kupambana pa masewero, pomwe ena akuti mankhwala sagwira ntchito mu mpira ndipo n’zotayitsa nthawi chabe
Female
A aliwo mpulura a mighty wakawaka tigers ali ndi maganizo ena. Apolisi m'boma la Mzimba amanga wophunzira kugwira ntchito ku khonsolo ya M'mbelwa, Gibson Kapeye
A aliwo mpulura a maite wakawaka taigazi ali ndi maganizo ena. Apolisi m'boma la Mzimba amanga wophunzira kugwira ntchito ku khonsolo ya M'mbelwa, Gibisoni Kapeye
Female
wa zaka 29 pomuganizira kuti anaba lamya ziwiri zamtundu wa lenovo.Mneneri wa polisi ya Mzimba a Peter Botha
wa zaka twente naini pomuganizira kuti anaba lamya ziwiri zamtundu wa Lenovo .Mneneri wa polisi ya Mzimba a Pita Botha
Female
wati akuluakulu a khonsolo ya M'mbelwa ndiwo anadandaula za kusowa kwa lamyazi zomwe zinali zochitira kafukukufuku mu ofesi yoona kayendetsedwe ka ntchito za ma project
wati akuluakulu a khonsolo ya M'mbelwa ndiwo anadandaula za kusowa kwa lamyazi zomwe zinali zochitira kafukukufuku mu ofesi yoona kayendetsedwe ka ntchito za ma pulojekiti
Female
Ndipo apolisi akuti kafukufuku wawo wapeza kuti a Kapeye, omwe amagwira ntchito ku nthambi yoyang'anira ogwira ntchito ku khonsoloyi ndiwo anaba
Ndipo apolisi akuti kafukufuku wawo wapeza kuti a Kapeye, omwe amagwira ntchito ku nthambi yoyang'anira ogwira ntchito ku khonsoloyi ndiwo anaba
Female
Lamya yomwe anagulitsa ku Kasungu pamtemgo wa K20,000 ayipeza pomwe ina yapezakanso kunyumba komwe amakhala. A Kapeye amachokera m'mudzi mwa Simon, mfumu yaikulu Kyungu m'boma la Karonga
Lamya yomwe anagulitsa ku Kasungu pamtemgo wa twente sauzande kwacha ayipeza pomwe ina yapezakanso kunyumba komwe amakhala. A Kapeye amachokera m'mudzi mwa Simoni, mfumu yaikulu Kyungu m'boma la Karonga
Female
A polisi m'boma la Balaka apempha adindo a zipani zosiyanasiyana m'bomali kuti apewe mchitidwe wa ziwawa pamene nthawi yokopa anthu ikuyembekezeka kuyamba posachedwapa
A polisi m'boma la Balaka apempha adindo a zipani zosiyanasiyana m'bomali kuti apewe mchitidwe wa ziwawa pamene nthawi yokopa anthu ikuyembekezeka kuyamba posachedwapa
Female
Poyankhula ndi Times 360 Malawi pa mkumano umene polisi ya Balaka inakonza, mkulu wa polisiyi, Dan Suteni
Poyankhula ndi taimusi fili sikisite Malawi pa mkumano umene polisi ya Balaka inakonza, mkulu wa polisiyi, Dani Suteni
Female
wati anthu achipani sakuyenela kuyambisa zachipolowe pa nthawi yomwe akuchititsa msonkhano wa ndale m'madera osiyanasiyana m'bomali ponena kuti izi zimabwezeretsa chitukuko m'mbuyo
wati anthu achipani sakuyenela kuyambisa zachipolowe pa nthawi yomwe akuchititsa msonkhano wa ndale m'madera osiyanasiyana m'bomali ponena kuti izi zimabwezeretsa chitukuko m'mbuyo
Female
Malingana ndi Sauteni, iwo alonjeza kugwira ntchito ndi aliyense posatengela chipani chimene akutsatira
Malingana ndi Sauteni, iwo alonjeza kugwira ntchito ndi aliyense posatengela chipani chimene akutsatira
Female
Ndipo m'modzi wa anthu amene anali nawo pa mkumanowu Haja George Makalakala wati msokhanowu ndi wofunika kwambiri ndipo wabwera pa nthawi yake pamene zipani zikhale zikupangitsa misonkhano yosiyanasiyana
Ndipo m'modzi wa anthu amene anali nawo pa mkumanowu Haja joji Makalakala wati msokhanowu ndi wofunika kwambiri ndipo wabwera pa nthawi yake pamene zipani zikhale zikupangitsa misonkhano yosiyanasiyana
Female
Pamsokhanowu panali azipani monga, DPP, MCP, UTM, PP, UDF ndi zina
Pamsokhanowu panali azipani monga, Dipipi, emusipi, yutiemu, pipi, yudiefu ndi zina
Female