File size: 1,488 Bytes
c6c7834
 
 
 
 
 
1
2
3
4
5
6
7
Id |Raw text |normalised
10APR10_14|Mukupitilira kumvera nkhani mwatsatanetsatane pompano pa wayilesi ya MIJ FM  Koma tisanapitilile ndi nkhanizi|Mukupitilira kumvera nkhani mwatsatanetsatane pompano pa wayilesi ya MIJ FM  Koma tisanapitilile ndi nkhanizi 
10APR10_15|Ndipo Mu nkhani za m’mayiko ena………… Anthu okwana makumi atatu (30) aphedwa ndi zigawenga mdziko la Nigeria.Gulu la zigawenga a mifuti, anachita chiwembu dera la Benue|Ndipo Mu nkhani za m’mayiko ena………… Anthu okwana makumi atatu (sate) aphedwa ndi zigawenga mdziko la Nigeria.Gulu la zigawenga a mifuti, anachita chiwembu dera la Benewu 
10APR10_16|lachisanu sabata latha, ndipo kafukufuku wa apolisi ali akusonyeza kuti gulu lazigawengali  linaombela anthu okhala mdelali|lachisanu sabata latha, ndipo kafukufuku wa apolisi ali akusonyeza kuti gulu lazigawengali  linaombela anthu okhala mdelali 
10APR10_17|Ngakhale gulu lomwe lachita za chiwembu-zi lisakudziwika, akuluakulu ati akukayikila anyamata oweta ziweto omwe akhala asakugwilizana ndi gulu lina la zifwamba dera-li|Ngakhale gulu lomwe lachita za chiwembu-zi lisakudziwika, akuluakulu ati akukayikila anyamata oweta ziweto omwe akhala asakugwilizana ndi gulu lina la zifwamba dera-li. 
12APR10_19|Akuluakulu ena a boma ati akhala akutumiza achitetezo ochuluka m’dera-li ngati njira imodzi yothetsera kusamvanaku|Akuluakulu ena a boma ati akhala akutumiza achitetezo ochuluka m’dera-li ngati njira imodzi yothetsera kusamvanaku.