audio stringlengths 43 45 | text stringlengths 0 24.1k | start_time int64 0 1.83k | end_time float64 1.74 1.85k |
|---|---|---|---|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_101.wav | Basi kagoneni, mawa paja ndi la sukulu Basi kagoneni, mawa paja ndi la sukulu | 0 | 5.44 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_102.wav | Malume zilibwino kwambiri Malume zilibwino kwambiri | 0 | 5.056 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_103.wav | Kakuoneka kuti kakomatu ka series kamenekaKakuoneka kuti kakomatu ka series kameneka | 0 | 6.08 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_104.wav | Katundu uja mpakana panoKatundu uja mpakana pano | 0 | 4.352 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_105.wav | Katundu afika liti?Katundu afika liti? | 0 | 4.288 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_106.wav | Mwanyamuka?Mwanyamuka? | 0 | 4.608 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_107.wav | Ndine chikanda ndimafuna kuti tilankhulaneNdine chikanda ndimafuna kuti tilankhulane | 0 | 6.08 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_108.wav | Zikomo kwambiri phone yafika pano ili ku ChancoZikomo kwambiri phone yafika pano ili ku Chanco | 0 | 5.503188 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_109.wav | Kodi amwene mwafika?Kodi amwene mwafika? | 0 | 5.952 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_110.wav | Ndimayenela kunyamuka dzana waku Rwanda koma ndinadwala COVID. Ndimayenela kunyamuka dzana waku Rwanda koma ndinadwala COVID. | 0 | 5.45675 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_111.wav | Nde ndamuuza anditumizile ine, ndekuti utha kungopanga invoice ya $2500. Nde ndamuuza anditumizile ine, ndekuti utha kungopanga invoice ya $2500. | 0 | 9.079063 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_112.wav | Kapena ndizapange deposit yokwana 2000$Kapena ndizapange deposit yokwana 2000$ | 0 | 4.620813 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_113.wav | Kodi za ndalama zija alipo angandilipirire 2000$ ndimpatse ma kwachaKodi za ndalama zija alipo angandilipirire 2000$ ndimpatse ma kwacha | 0 | 6.03725 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_114.wav | Mmawa uno atha kukatengaMmawa uno atha kukatenga | 0 | 3.018625 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_115.wav | Unakumana naye mamuna wa Nia?Unakumana naye mamuna wa Nia? | 0 | 3.901 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_116.wav | Nde yama diaper ija munditumizila week yammawaNde yama diaper ija munditumizila week yammawa | 0 | 3.71525 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_117.wav | Phone yabwino ndalama zingatiPhone yabwino ndalama zingati | 0 | 3.041875 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_118.wav | Chawezi zoona izi? Mwayamba kulemba tiana tu?Chawezi zoona izi? Mwayamba kulemba tiana tu? | 0 | 4.29575 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_119.wav | koma abale anzanga zinthu zake phone ija nde yasokonekeleratu ayi zimachitikakoma abale anzanga zinthu zake phone ija nde yasokonekeleratu ayi zimachitika | 0 | 8.9165 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_120.wav | Avomere basi kuti zitengera eni akefe kufuna apo biii azichita kugwadaAvomere basi kuti zitengera eni akefe kufuna apo biii azichita kugwada | 0 | 5.108438 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_121.wav | Kodi ndiye azawatolera motani ma loan wa koma? Kodi ndiye azawatolera motani ma loan wa koma? | 0 | 4.690438 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_122.wav | Mpamene pataulurike zonse apapa, amaba misonkho.Mpamene pataulurike zonse apapa, amaba misonkho. | 0 | 4.527938 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_123.wav | Okathandizira kugawa tilipo ambiri masanawadi.Okathandizira kugawa tilipo ambiri masanawadi. | 0 | 5.688938 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_124.wav | Zikomo kwambiriZikomo kwambiri | 0 | 2.670313 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_125.wav | Eyadi, tonse zitikwane basi.Eyadi, tonse zitikwane basi. | 0 | 4.017063 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_126.wav | mudzawona ngati moyo ngophweka...mudzawona ngati moyo ngophweka... | 0 | 3.529438 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_127.wav | Malume panongo zinthu sizikuyenda osati sewelo.Malume panongo zinthu sizikuyenda osati sewelo. | 0 | 5.317375 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_128.wav | Chaka Chiko mvula yagwa mowononga zinthu, mpaka napolo ku chikwa ndi nsanjeChaka Chiko mvula yagwa mowononga zinthu, mpaka napolo ku chikwa ndi nsanje | 0 | 6.176563 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_129.wav | Ngati mupitilize nkhalidwe wanuwo moyo wanu simupita patali.Ngati mupitilize nkhalidwe wanuwo moyo wanu simupita patali. | 0 | 4.806563 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_130.wav | Kwezani mowa tsitsani mafuta ophikila chondeKwezani mowa tsitsani mafuta ophikila chonde | 0 | 5.363813 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_131.wav | Lero ndiye tiumwa mowa kwabasi.Lero ndiye tiumwa mowa kwabasi. | 0 | 3.784875 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_132.wav | Koma aise ukununkha kwambiri, koma wasamba?Koma aise ukununkha kwambiri, koma wasamba? | 0 | 5.108438 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_133.wav | Mkamwa mwako mukununkhaMkamwa mwako mukununkha | 0 | 3.761688 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_134.wav | Amayi ndi abambo ako adusa pompano akupita ku msika.Amayi ndi abambo ako adusa pompano akupita ku msika. | 0 | 5.03875 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_135.wav | Anzanthu mwatchenatu zovala zokongola, akugulirani ndani?Anzanthu mwatchenatu zovala zokongola, akugulirani ndani? | 0 | 5.03875 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_136.wav | Zimakhala zonvesa chisoni kwambiri pamene wataya wokondedwa wako.Zimakhala zonvesa chisoni kwambiri pamene wataya wokondedwa wako. | 0 | 4.87625 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_137.wav | Ndikunva maluno mthupi.Ndikunva maluno mthupi. | 0 | 3.738438 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_138.wav | Madzi akatentha mundiyitane ndizasambe.Madzi akatentha mundiyitane ndizasambe. | 0 | 4.040313 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_139.wav | Inu mukuona ngati zikamatha zaka 10 moyo wanu ukhala wosinthika?Inu mukuona ngati zikamatha zaka 10 moyo wanu ukhala wosinthika? | 0 | 6.664188 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_140.wav | mmene munayambila muja mavuto amenewa azakuthelani koma, kapena tiziti alipo anakutembelerani.mmene munayambila muja mavuto amenewa azakuthelani koma, kapena tiziti alipo anakutembelerani. | 0 | 8.289563 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_141.wav | Bread uja sikuti angokweza mtengo kokha atchotsamonso ma slice awiri Bread uja sikuti angokweza mtengo kokha atchotsamonso ma slice awiri | 0 | 6.339063 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_142.wav | Mmoya wanga wnse mvula sinagwepo mochuluka chonchi, mwina dziko likutha.Mmoya wanga wnse mvula sinagwepo mochuluka chonchi, mwina dziko likutha. | 0 | 7.035688 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_143.wav | Pamene ali iye uja ali ndi zibwenzi zisanu kuphatikiza akazi anayi. munthu amene uja ndi hule ndithu.Pamene ali iye uja ali ndi zibwenzi zisanu kuphatikiza akazi anayi. munthu amene uja ndi hule ndithu. | 0 | 9.10225 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_144.wav | Tiyeni tilimbikile kulima chimanga mwina tikhonza kukolora zochuluka ndikupedza ndalama.Tiyeni tilimbikile kulima chimanga mwina tikhonza kukolora zochuluka ndikupedza ndalama. | 0 | 6.292625 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_145.wav | Amene sanasonkhe nawo sadya mmemo.Amene sanasonkhe nawo sadya mmemo. | 0 | 3.947438 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_146.wav | Mu dziko lathu panopa chili chonse chakwera. katundu akudula mopitilira muyezoMu dziko lathu panopa chili chonse chakwera. katundu akudula mopitilira muyezo | 0 | 5.2245 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_147.wav | Lero ndiye mwatchena asisi, zimenezi mwagula ku mbeya?Lero ndiye mwatchena asisi, zimenezi mwagula ku mbeya? | 0 | 4.249313 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_148.wav | Awa ndi makulina akulu, chombo cha p anseu.Awa ndi makulina akulu, chombo cha p anseu. | 0 | 4.342188 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_149.wav | Malaya awa akundithina kwambiri makamaka mimba yangayi yakula kwambiri.Malaya awa akundithina kwambiri makamaka mimba yangayi yakula kwambiri. | 0 | 5.526375 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_150.wav | Ku ntchito sindipitako ndadwala.Ku ntchito sindipitako ndadwala. | 0 | 2.92575 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_151.wav | Mayi ake ndiovuta kwambiri, anayamba apenga misala ali mwana.Mayi ake ndiovuta kwambiri, anayamba apenga misala ali mwana. | 0 | 4.551125 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_152.wav | ife kuno tilibwino tose zikomoso nanu kuti muli bwino eya achikambe nawo ah alibwino indetu kulima masiku ano mabize mabize zikomo zikomo | 0 | 17.664 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_153.wav | Ndachoka pang'ono, ndikubwela, ndikubwela pompano. | 0 | 4.864 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_154.wav | ati a ati amakaikila ama amona ngati kuti mwina tungo mdoja kuti mwina mpandowo ungojambulidwa sukupangidwa and then nde eh atauona kunali ku ukhalilatu akangotele eh naisi chair akangotele nice chair ndamuuza kuti aha tapanga mani ndumenewotu mukanika nokha chifukwa choti mtengo sitikuvana hehe | 0 | 30 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_155.wav | 30 | 33.792 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_156.wav | inde ndili ku mzuzu ndabwela kodi ndabwela liti lasti ofu lasti wiki eh mna mnapeza ka ga ganyu mmalowetsa data nde nabwela chifukwa cha zimenezo nde basi ndangomkhalilatu e | 0 | 20.650688 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_157.wav | ah ife tili bwino kuno zoipa mzomwezi za dzanjai izi kuno koma achikambe nde eh mmimba kutsegula kamwazi eyetu kaya odwala waja azione aliko bwanji pano | 0 | 14.506688 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_158.wav | aise ndine lameck tu kuli bwanji kumeneko muli ku lilongwe kapena ku mzuzu tasimbani za moyo braz | 0 | 12.288 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_159.wav | Dzina langa ndine Carlo Beya, interview number one community leader, Nsangwa village T/A Kayembe Dowa. Tikuyamba!!
Choyamba ndufuna ndidziwe kuti inu mudzi muno muli ndi udindo wanji? Ah Choyamba ndufuna ndidziwe kuti inuyo mudzi muno muli ndi udindo wanji? Ineyo mudzi muno ndili ndi udindo monga ku khola la za ngÕom... | 0 | 30 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_160.wav | 30 | 60 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_161.wav | 60 | 90 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_162.wav | 90 | 120 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_163.wav | 120 | 150 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_164.wav | 150 | 180 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_165.wav | 180 | 210 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_166.wav | 210 | 240 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_167.wav | 240 | 270 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_168.wav | 270 | 300 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_169.wav | 300 | 330 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_170.wav | 330 | 360 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_171.wav | 360 | 390 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_172.wav | 390 | 420 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_173.wav | 420 | 450 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_174.wav | 450 | 480 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_175.wav | 480 | 510 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_176.wav | 510 | 540 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_177.wav | 540 | 570 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_178.wav | 570 | 600 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_179.wav | 600 | 630 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_180.wav | 630 | 660 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_181.wav | 660 | 690 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_182.wav | 690 | 720 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_183.wav | 720 | 750 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_184.wav | 750 | 780 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_185.wav | 780 | 810 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_186.wav | 810 | 840 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_187.wav | 840 | 870 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_188.wav | 870 | 900 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_189.wav | 900 | 930 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_190.wav | 930 | 960 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_191.wav | 960 | 990 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_192.wav | 990 | 1,020 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_193.wav | 1,020 | 1,050 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_194.wav | 1,050 | 1,080 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_195.wav | 1,080 | 1,110 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_196.wav | 1,110 | 1,140 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_197.wav | 1,140 | 1,170 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_198.wav | 1,170 | 1,200 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_199.wav | 1,200 | 1,230 | |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_200.wav | 1,230 | 1,260 |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.