audio
stringlengths
43
45
text
stringlengths
0
24.1k
start_time
int64
0
1.83k
end_time
float64
1.74
1.85k
./data/chichewa-dataset\audio\segment_601.wav
Okay ah komabe mumachita bho. sinakha kuti muthu uziwerenga komanso kuti uzipanga ndi izizi sizimagwirizana iai.
0
7.594688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_602.wav
Okay ndiye mawa bwanji sizingatheke saturday?
0
3.328
./data/chichewa-dataset\audio\segment_603.wav
Lero sizingatheke ndili busy ndili busy. litakhala monday kapena lachiwiri kapena sunday.
0
8.618688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_604.wav
Okay ndimafunsa kuti mumafuna kuti ndizabwere mkoko? kuma hostel kwanuko.
0
6.485375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_605.wav
Okay ukutanthauza kuti ndizabwere kumenekoko? ndiye ndikufunsa.
0
4.693375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_606.wav
Tayankhulani chichewatu tikupangeni Mom Dad on the car Tayakhulani Tayakhulani chichewa Mukuzikakamiziranji? Ah Kuzikakamiza
0
18.599188
./data/chichewa-dataset\audio\segment_607.wav
Eetu aise koma aaa mpata ukapezeka leloro unakakhala kuti unalipo ndizotheka ndinakadya koma nanga si iwenso mpatawo? kodi iweyo umakhala mbali yake iti?
0
13.141375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_608.wav
Okay aise undiuza, undiuza. ine malo mu Blantyre ndimatha kudziwa kuti mu Blantyre koma nanga ndimakhala ku Chilimba Ndiye nanga ndiganene kuti tikakumana malo akuti? ine ndimadziwa kuti malo ambili ndi kuchiii.... and ndinakumana ndi ada ena ake akandiuza kuti tikakumane nawo kwakuti. ndinawauza kuti sindimapanga zach...
0
24.490688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_609.wav
Ndiye ndi ya wani week yokhatu nanga apapa ana atsala ndi 4 weeks. ndiye 4 weeks tikachotsapo week inoyi tatsala ndi 3. Pa 3 ndiye kuti ah nthawinso yolemba mayesoso. ndiye kuti ikhala one week survey yaketu. ndiye kuti 5 schools 5 schools 5 schools 5 schools. Eh kaya panja ndi unjeni ndi chani? ndichani panja? uh ndi...
0
26.965375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_610.wav
Ah unjeni of course ndi pilot chabe ndiye agotenga ma guy achina Prince kaya ndi athu 5 kaya. eh agopanga pilot sinanga unjeni eti akuti asitha ma tools. like ah mukavaya pa geli panja, kukhala ngati achina mothergroup anja chanichani zimene zinja azichotsa Ndiyeno akufuna angoyesa apapa lero ndi mawa. Angoyesa kuti ng...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_611.wav
30
36.778688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_612.wav
Ah ali bho athu amene awatenga MESIP woo apite MESIP yoo amenewo. akapange pilot. koma kwatsala 4 weeks yokha kuti ana atsekere school
0
10.069375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_613.wav
Ndinakumana naye dzulo ndiye sitinapange exchange ma namabala. Ndinakumana nacho dzulo. Eetu kaya akuzatani kaya ku Zomba kuno?
0
11.776
./data/chichewa-dataset\audio\segment_614.wav
Yesi bwana Matekenya!, ha bwana ine basitu ndimagofuna ndikukumbutseni tikumbutsane za pempho linja ndinakupemphani abwana. (waipeza?) pa pempho ndinakupephani abwana ndimafuna ndikukumbutseni kuti chonde abwana mbale wanga muesetse mundiyesetsere ndithu kutinso munandiuza kuti ah komano mwenzi wa mawa wa Malichi wo nd...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_615.wav
30
51.285375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_616.wav
Iii nambala ya Robert ndilibe. phone kusitha-kusitha basi tinataya nambala ya a Robert.
0
8.448
./data/chichewa-dataset\audio\segment_617.wav
Ah aise Rich ugule nambala ya TNM mwamva! Airtel yakoyi ah ife timakonda TNM. Tangulani TNM tizikuiimbilani.
0
9.898688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_618.wav
Kodi Rich kodi bwanji aise eh bwera. bwera kukhala ngati lero wadzuka mwa unjeni mwa libido eti ukufuna ukhale father wa Libido?
0
11.434688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_619.wav
Uwapatse moni akazako. wamva? akazako uwapatse moni. ufiketu moniyo?
0
8.789375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_620.wav
Ahaha inuyo munamwa mumamwa mwa mpikisano? simafunika kumamwa za mpikisanotu zimenezo. Ndiye pulasi kaunjeni unatenga unja special. Ah a Rich simumadziwa kuti timakhala mu Zomba nthawi yoseyi? Zomba aise Matawale.
0
18.688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_621.wav
Uh mh sinadzuke bho. Nthobwa lakuchikhoswe landitsegula mimba. Ee aise uli kuuu kuti? ku Balaka or kuuuu tanena bwinobwino.
0
13.568
./data/chichewa-dataset\audio\segment_622.wav
Eh a Richi! bho bho. mwadzuka bwinotu lero.
0
7.082688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_623.wav
Bho?
0
1.792
./data/chichewa-dataset\audio\segment_624.wav
Azathu a chamba dzukanitu. Dzukani kwacha. Ife tikuvaya kuma dis amwene.
0
8.362688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_625.wav
Timangolowa aise Phalombe, Phalombe. Iya Phalombe, Phalombe amwene zamafuta anatiletsa. Ndiyeso ndizivala zimene zinja mafuta iai-iai.tidwalatu hihihihi. iii aise ndikuona mawa ndatopa ndigone. Mawa tili ndi ma dis ndiye ndikukapanga lead ndiineyo. Ndakuuza kale uzabwereko pa Bananapa. eee kuchokera kumeneko kufika pa...
0
25.685375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_626.wav
Wana Dasitani ndine Antony Chikanda abwana. Ndimati mukhale pa laini kuti tiyakhulane. Ndithu mbale wanga
0
14.08
./data/chichewa-dataset\audio\segment_627.wav
Aise ndiye umagolowa mutu-mutu? ah ubwino wake uli ku chipatala uma...umangotenga zokumwa. Okay basi ife ma daso aise koma opandapo mowa eti. wakamva kameneko? bweratu! ubweretse watsalawo. hihihihih
0
19.370688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_628.wav
Hihihih ahaha mwana! hahah zachibwana basi. Mwana iai zitayeni. za anazo ayi. anawo mwabereka inuyo akwanira basi. akwanamo dziko muno. Kondomusotu ayi anatiletsa zamafuta. Zamafuta anatiletsa ife ndiye kondomu sitimavala.
0
21.333375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_629.wav
Hhihihih man! muzakakwatira muzakhala ndi mwana amene azakhale wanu. Chifanizo chanu. Waiona? aise nanga uzigothila pa bed ee basi, basi pa bed ndi mkondomu. Ah iai tatulutsani nkhope yanu.
0
18.005375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_630.wav
Ah ah kusandikonda ndiye kumeneko. Munakakhala kuti mumatikonda simungatiuze zokwatila amwene aaa. Mumatikonda zenizeni inu? Mutiuzilanji zokwatira? ah uzakwatire ineyo? hahahahah tikondeni amwene tiuzeni zina koma osati zokwatira.
0
19.029375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_631.wav
Hhahahahaha aise! advisor wako ndani amene amakulangiza zamahule? eee? aise inetu ndimalangiza zithu zabwinozabwino zokhazokhatu zokuti uzakwatire, uzakhale ndi mkazi modzi. waiona!uzakhale mkulu wa mpingo. waona. ndimalangiza zabwino zokhazokha positive.
0
17.152
./data/chichewa-dataset\audio\segment_632.wav
Ah koma Mulungu sangandipatseko amzanga abwino? kungondipatsa zingawenga zokhazokha. Sangandipatseko mzanga wina wake oti azindilangiza? azindiuza ma verse. Kungondipatsa ma hule basi. zidakhwa. iyaa.
0
15.445375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_633.wav
Iwe ndi wampingo wanji? hihihih
0
3.157375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_634.wav
Ndakutulukirani hihihih anyamata a libido. Nonse amene munali busy kukomenta mmene munja mkati munja ndimakuonanitu. Ndimadziwa kuti anyamata a libido awa. Achina Allan. iiiiii koma guys. Aise mawa ndizagofika ndifika ndikufuna ndizagokuona basi. Ndizagokuona kenako ndizavaye ku deni. Ndikufuna ndizakumanenso ndi mkazi...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_635.wav
30
39.082688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_636.wav
Hhihihihi Aise ine ndi wamtali aise hihihihih koma inu iiii eee athu afupiafupi amwene zimakhala kuti zimichira zanu zazitali ati msinkhu umakhala kuti unathawila malo amodzi. Ndiye kumenekoko, Mumalilitsa nazo azikazi. Azanu akoka dzulo. Mkazi kumagokuwa kuseliku Ah akumafika nawo pati kaya
0
23.637375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_637.wav
Kodi ukuti watani walakwa chani Kelvin? Wakutaa! Akuvutitsa Akuvutitsa? Uh Wavutitsa chani? Usandivutitse uone! Oh Ndikukuzatu ndikatenga chikwapu Akukatenga chikwapu chinja Akukatenga chikwapu? Uh Ayi sakumenya. Usaike mkamwa Bukhu uh
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_638.wav
30
42.048
./data/chichewa-dataset\audio\segment_639.wav
Hahahaha Eh eh wtokotatu aise. Kodi athu afupiafupi mumadziwa kunyenga, umadziwa? kodi umazitenga kuti ndiwe wamtali kapena wamfupi? iwe ndi ine chimodzimodzi basi. Ah man tatiyeni tizigomwa mowa.
0
13.397375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_640.wav
Ah amwene zonyenga zisiyeni. Zonyengeratu amzanu chipinda cha ukocho anyengana anakoka anyenga basi. Ife kutisiya kuno iwo kumanyenga uko. Ndiye chimkazi chake chimagolira ife kumamva kuno. Zachibwana. Basi ndasiya. Pa getipo ndizigosiya Agalu zi akazizo sizimabwera. Muzinyenga komweko uko ku balako kunoko mukamabwera ...
0
26.453375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_641.wav
Ah man inuyo mugotsegula nyumba yanuyo kuti athu tikafuna kunyenga tizibwera kuzanyenga kumeneko basi. Sikuti muzibwera ku mowa osanyenga basi muzizanamizila kugona pamenepo mutanyenga kuseli kwa bala ku unjeni kwa kauta. Ee kukhala kwa bwanji kumeneko? Tapangani tizi... tizi hihihihihih
0
20.309375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_642.wav
Amwene mavuto amwene iii azanga aine ndawatenga amagona kunoko eti. of course timagona limodzi ndi Kelvin. Wandemvu zake uja. Zonse za Ndemvu zimagona kunoko zimandipatsa busy ndi ndemvu zaozo. apa tagopita ku village basi. Ati agona komweko anyenge Hihih ihih iii guys.
0
20.48
./data/chichewa-dataset\audio\segment_643.wav
Kodi ukumwa chani? Castel? kapena Chill? kapena kachasu
0
5.632
./data/chichewa-dataset\audio\segment_644.wav
Alright thanks a Shad kugoti ee aise maluzi atikwapula. i am really broke,broke. mwenzi watha koma ndilibe kalikonse aise. Kalikese ndilibe aise
0
15.018688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_645.wav
Pa gulupu pano ndiku……muli ndi chibwana
0
4.245375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_646.wav
Bwanji uyu wotsongolera Anti-corruption bureau. Ameneyu asamasankhidwe ndi presidenti chifukwa ambiri amakonda kulakhula mau akuti munthu saluma chala chimene chikumdyetsa amatero wanthu Mm inu mudzalola kuti mphamvu imeneyi,mutakhala presidenti musakhale nayo yosanlhaa…. Ndinje kusintha maganizo anga. Zimene zinja...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_647.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_648.wav
60
71.125375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_649.wav
Hallo? Yeah yes madala. Yes madala mwaswera? Ndaswera bwino kaya inu? Ah taswera. Ndaona unjeni ah website yanu Uh uh Ah wina wake mzanga ananditumizira Uh Eh ndiye ndimaiona going through kupeza kuti ah introduction ya on herbals ikupezeka kuti exactry reeflet yanga kuti ah zikukhala bwanji? Iayi sitinapangeyi...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_650.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_651.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_652.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_653.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_654.wav
150
178.816
./data/chichewa-dataset\audio\segment_655.wav
Ku 24, 23 kumaoneka chochi. 24 ndiku 23 eh anthu aku 24 ndi 23 kwanu kumaoneka chochi. Ayi ndithu. Ndiye mumadutsa pati
0
19.876313
./data/chichewa-dataset\audio\segment_656.wav
Komanso zimene ndisakusangalatsidwa nazo ndi chonena kuti, munthu pulizitu mundivetsetse!. Mundivetsetse. Sindikufuna kuti musamutenge iai koma inuyo mundivetsetse. Ineyo munthu sindikumudziwa sinamuonepo. Mukundivetsa eti?. Koma mavuto aku Malawi ndimawadziwa chifukwa ndabadwira mkoko ndakulira mkoko and munthu akaman...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_657.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_658.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_659.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_660.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_661.wav
150
180
./data/chichewa-dataset\audio\segment_662.wav
180
205.524
./data/chichewa-dataset\audio\segment_663.wav
Amkolo kumeneko ntchito anampezera kale ndipo mzunguyo amene atakagwire ntchitoyo tayakhula naye Benard yoo ndipo akumuuza kuti nthawi inailiyonse anganyamuke pa mwenzi uno ntchito akayamba akudikira iyeyo. Ndiye ah za kolonazo tinaesera kufotokoza koma iyeyo wanena kuti ayi apitebe ndithu za kolona m’boza zakutinso ...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_664.wav
30
57.3
./data/chichewa-dataset\audio\segment_665.wav
Ah Amkolo ndinanena kuti ndimagwira kanganyu kwa Bodwe ndiye ndimagulitsa mu gulosale mwawo ndiye mudziwa January yuu ka golosale atseka. Ndiye sizikuyenda. Ndiye apapa pali chipwilikiti ndimafunako Kandalama chithandizo kuti ndiyambileko kabisiznesi town muno. Ndisafala ni wana ndiye ndikhala bwanji town ndi wana mun...
0
24.617375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_666.wav
Ayise, ayise machine amene ndimakuuza ndi amenewa Ada. Ndi amene ndimaku ndimakuuza. Ndiye mwina zitatero kuti ngati zingakhale zotheka kuti mbale wanga ungomugulira amenewa basi
0
14.121375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_667.wav
Abwera awa? Ee ndibwera ndi mmene timakhuthulira….. Mwawaonetsa mwala uwowo? Ee sir ichi Ichi, ichi chimwalachi cha uku mwauna direct mwala uwo? Miyala iyi ili ukuyi Ili ukukuyi? Ee Ayi safika kwinakuyi yofunika kuinyamula eh abwera awa? Eh kubwerera ibwelera koma ima…….
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_668.wav
30
38.761375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_669.wav
Abwera awa? Ee ndibwera ndi mmene timakhuthulira….. Mwawaonetsa mwala uwowo? Ee sir ichi Ichi, ichi chimwalachi cha uku mwauna direct mwala uwo? Miyala iyi ili ukuyi Ili ukukuyi? Ee Ayi safika kwinakuyi yofunika kuinyamula eh abwera awa? Eh kubwerera ibwelera koma ima…….
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_670.wav
30
35.412
./data/chichewa-dataset\audio\segment_671.wav
Hallo amkolo ndine Amon, Amon, Amon Chandawira. Kodi malume munatitaya chocho chifukwa chani malume tazanu. Kunoko sitikugwira timaganyutu. Ndimafuna amkolo tiyambeko ka business kenakake mwina kogulitsa Chimanga cha Nsima. Mutitumizireko pang’ono tazanu ndili kuno ku Mzuzu kumudzi sindinapite iai. Pakati apa ndithu...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_672.wav
30
35.22
./data/chichewa-dataset\audio\segment_673.wav
Ah Amkolo ndinanena kuti; ndimagwira kaganyu kwa Bondwe ndiye ndimagulitsa mu golosale mwawo ndiye mukudziwa January yuu kagolosale atseka. Zithu sizikuyenda. Ndiye apapa pali chipwilikiti. Ndimafunako ka ndalama chithandizo kuti ndiyambileko business mtawunimu muno. Ndisafala ni wana nanga ndipanga nawo bwanji wana? M...
0
24.617375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_674.wav
Hallo Amkolo, ndiye mwati vuto ndi chani? Sindinamve chilichonse ine! Pakakhala vuto ine Asante amandi…. amandiuza ndiye sanandiuzeko chilichonse
0
15.7
./data/chichewa-dataset\audio\segment_675.wav
Nkhani iyiyi nkhani iyiyi nawonso ankhala ngati kuti alowa maganizo mwathu. Kuteloko tikubwer ku maliro a Getu kuja tikakambilananso mgalimoto. Timanena kuti tikafika, tii tipeza kanthawi yoti anthu akumudzi anja asanapite, tikhale pansi tiiikambilane patalipatali. Ifenso tinapangadi chimenechocho kuti iwowo akonze nj...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_676.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_677.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_678.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_679.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_680.wav
150
180
./data/chichewa-dataset\audio\segment_681.wav
180
191.721375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_682.wav
Amkolo muli bwanji? A Matekenya. Ndine Amon Chandawira kuno ku Mzuzu. Tati tikupatseni moni. Komanso tikufuna tikufotokozereni kuti aeni ake a foniyi nawonso ndi amisili ndimanena anja. Moti akudikiratu ulendo wakuzomba kuti uli pati? Ndithu Amkolotu. Ndiye mmene zililimo muzitifotokozera. Zikomo.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_683.wav
30
31.892
./data/chichewa-dataset\audio\segment_684.wav
Hallo amkolo ndine Amon, Amon, Amon Chandawira. Kodi malume munatitaya chocho chifukwa chani malume tazanu. Kunoko sitikugwira timaganyutu. Ndimafuna amkolo tiyambeko ka business kenakake mwina kogulitsa Chimanga cha Nsima. Mutitumizireko pang’ono tazanu ndili kuno ku Mzuzu kumudzi sindinapite iai. Pakati apa ndithu...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_685.wav
30
35.22
./data/chichewa-dataset\audio\segment_686.wav
Iii koma ii koma koma ndi zabwinotu koma ii ayi the feeling kuti mwina board yathu amatipatsaa ndalama zochepa koma iii ndiye utenge chibenzi cha nyuwani chinja. Osagochitenga bwanji? Ah kumeneko ngati athu amapangapanga Ngozi? Palibe zoti ungagwe misewu yake yabwinobwino. Kungoyitenga. Iii ndinaona benzi ina yake muâ...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_687.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_688.wav
60
81.385375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_689.wav
Yeah pano tili ndi munthu yemwe anapezeka ku Ligoni amanena kuti wamwalira unja komano athu anagotenga mtembo wa eniake. Mwini wake weni-weni ndi uyuyu. Akulu tafotokozani bwinobwino Ah chimene chinachitika ndi choti ine ndinali ndili kwa Namatchowa ndikumwa mowa. Ndiye abale anga anagomupeza munthu wina wache atafa. A...
0
29.977
./data/chichewa-dataset\audio\segment_690.wav
Kumupeza kuti zimayi wadutsa, basi ‘ona mwendo, mwendo, mwendo; mwendo’ Hahahaha Ah moti mzoona zoti munthu amayenda miyendo zachilendo? Ayi Zachilendo? Nkhaniyi ndi chimasomaso
0
19.086813
./data/chichewa-dataset\audio\segment_691.wav
Ndiye ndiayimbile foni mwina
0
8.128
./data/chichewa-dataset\audio\segment_692.wav
Ah ndawapatsa koma akuti aitanitsa ati a Fyuzgo ndiye mwina afika kaya ma week ati kuchokera ku south africa. koma poti dzulolo imavuta ati mmene amachoka town imagoti phuphuphu ndiye akagoikabe awowo akudikira a fyuzgo woo kuti asafike
0
22.654688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_693.wav
Apa ndikubwerako ndimafuna ndikafikano ndiye tiyankhulane. apa tikuthamangira pa boarder ya pa Songwe. koma ma unjeni anja ndinagula ma pakate awiri koma ma pack awowo amakhala a excel amakhala 15, 15. Ndiye ndinawafunsa ngati ali ndi yotsegula kuti tiwone quality yake ndiye anati aah alibe yotsegula komanso awowo sang...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_694.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_695.wav
60
65.172
./data/chichewa-dataset\audio\segment_696.wav
Ndiye awowo alipo ma pack awiri ndikujambulirani ndikutumizirani. Ndiye ndia... ndiwapatsira a head chifukwa ndili ndi a head ndiye kuti akawapatsira. Ndithu. ndiye mmene aneneremo ndiye kuti ndizigula type imeneyo. Ngati anganene kuti type imeneyo siyabwino ndiye kuti tisitha ndikatenge type ina. Koma vuto lake ndilo...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_697.wav
30
33.556
./data/chichewa-dataset\audio\segment_698.wav
Okay ndiitanitse invoice mpopanopo
0
4.372
./data/chichewa-dataset\audio\segment_699.wav
Inu ndinu ndani chimwemwe Bwanali TNM call centre ee mukuti bwanji amwene? ee tinatumiza ma message mwenzi wathawu ehe eee okuti chani? okuti mupange sim-card update sim-card yanu sindikudziwa kuti ma message atabwera munapanga follow? ee ndinapanga kale update koma mu system mwathu simukuonetsa kuti munapanga updat...
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_700.wav
30
60