audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
A Mkandawire anena izi pa mkumano omwe anali nawo mmawa wa Lachinayi ndi mabungwe omenyera ufulu wa anthu | A Mkandawire anena izi pa mkumano omwe anali nawo mmawa wa Lachinayi ndi mabungwe omenyera ufulu wa anthu | famale | |
Polankhula ndi olemba nkhani mu mzinda wa Lilongwe, a Benedicto Kondowe omwe anatsogolera amabungwewa anati iwo anafunsa a Mkandawire kuti ndi chifukwa chiyani pali chiopsyezo chofuna kumanga a Gondwe omwe ndi oulula zakatangale | Polankhula ndi olemba nkhani mu mzinda wa Lilongwe, a Benidikito Kondowe omwe anatsogolera amabungwewa anati iwo anafunsa a Mkandawire kuti ndi chifukwa chiyani pali chiopsyezo chofuna kumanga a Gondwe omwe ndi oulula zakatangale | famale | |
A Kondowe ati a Mkandawire awatsimikizira iwo kuti pakadali pano palibe chikonzero choitanitsa a Gondwe ndipo kuti ngati kungafunike kuti a Gondwe akafotokoze zina ndi zina, boma lidzatero motsata malamulo | A Kondowe ati a Mkandawire awatsimikizira iwo kuti pakadali pano palibe chikonzero choitanitsa a Gondwe ndipo kuti ngati kungafunike kuti a Gondwe akafotokoze zina ndi zina, boma lidzatero motsata malamulo | famale | |
Nduna yoona za malamulo, a Titus Mvalo yati mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera wakhululukira akaidi oposa 8,000 kuchoka m'chaka cha 2020 | Nduna yoona za malamulo, a Taitasi Mvalo yati mtsogoleri wadziko lino a Lazalasi Chakwera wakhululukira akaidi oposa eiti sauzande kuchoka m'chaka cha twente twente | famale | |
Iwo ati kukhulukira akaidiku ndi njira imodzi yochepetsera kuthithikana ndi mu ndende za dziko lino | Iwo ati kukhulukira akaidiku ndi njira imodzi yochepetsera kuthithikana ndi mu ndende za dziko lino | famale | |
A Mvalo, omwe ndi wapampando wa komiti yomwe imaunikira nkhani zokhulukira akaidi, ayankhula izi atatsogolera komitiyi, kuona zomwe akaidi ku ndende yaikulu ya Zomba akukumana nazo | A Mvalo, omwe ndi wapampando wa komiti yomwe imaunikira nkhani zokhulukira akaidi, ayankhula izi atatsogolera komitiyi, kuona zomwe akaidi ku ndende yaikulu ya Zomba akukumana nazo | famale | |
Mwa zina, zinadziwika kuti pa ndende ya Zomba pali akaidi okwana 2,126 ngakhale ndendeyi inamangidwa kuti muzikhala akaidi 800 | Mwa zina, zinadziwika kuti pa ndende ya Zomba pali akaidi okwana thu sauzande wani handede andi twente sikisi ngakhale ndendeyi inamangidwa kuti muzikhala akaidi eiti handede | famale | |
Aphunzitsi akuluakulu m'sukulu zina za pulayimale m'boma la Salima ati akukhonzekera kuchita ziwonetsero zabata | Aphunzitsi akuluakulu m'sukulu zina za pulayimale m'boma la Salima ati akukhonzekera kuchita ziwonetsero zabata | famale | |
pofuna kusonyoza kusakondwa ndi kuchedwa kwa bungwe la National Registration bureau (NRB) kuti liwapatse malipiro pa ntchito yomwe anagwira chaka chatha | pofuna kusonyoza kusakondwa ndi kuchedwa kwa bungwe la neshono legisitileshoni byulo (eni ala Bi) kuti liwapatse malipiro pa ntchito yomwe anagwira chaka chatha | famale | |
Mphunzitsi wamkulu pa Ntchentche pulayimale m'bomali a Nera Chapendeka wauza Times 360 Malawi | Mphunzitsi wamkulu pa Ntchentche pulayimale m'bomali a Nera Chapendeka wauza Taimusi fili sikisite Malawi | famale | |
kuti iwo anagwira ntchito kwa masiku 14 m'mwezi wa August koma kufikira lero, malipiro awo sakubwera komanso sakudziwa kuti alandira ndalama zingati | kuti iwo anagwira ntchito kwa masiku fotini m'mwezi wa Ogasiti koma kufikira lero, malipiro awo sakubwera komanso sakudziwa kuti alandira ndalama zingati | famale | |
Awa a NRB sakutiganizira, tinapereka mabanki akaunti tili mkati mwa ntchito pamapeto pake n'kumauzidwa kuti tinapereka ma akaunti olakwika chifukwa ichichi sichokwanira, anatero a Chapendeka | Awa a Eni ala bii sakutiganizira, tinapereka mabanki akaunti tili mkati mwa ntchito pamapeto pake n'kumauzidwa kuti tinapereka ma akaunti olakwika chifukwa ichichi sichokwanira, anatero a Chapendeka | famale | |
Ndipo mkulu wa bungwe la NRB m'boma la Salima a Malla Zimba wati ndi zoonadi kuti aphuzitsiwa anagwira ntchito koma iwo ati akukayikira kuti malipiro awo akhoza kukhala kuti achedwadi kaamba ka ma akaunti omwe anapereka | Ndipo mkulu wa bungwe la Eni ala bii m'boma la Salima a Mala Zimba wati ndi zoonadi kuti aphuzitsiwa anagwira ntchito koma iwo ati akukayikira kuti malipiro awo akhoza kukhala kuti achedwadi kaamba ka ma akaunti omwe anapereka | famale | |
M'malo mwake, iwo ati afufuza bwino lomwe za vutoli kuti aphunzitsiwa athandizidwe | M'malo mwake, iwo ati afufuza bwino lomwe za vutoli kuti aphunzitsiwa athandizidwe. | famale | |
Ntchito za malonda zikadali chiimire pa town ya Liwonde m'boma la Machinga pomwe bata likukanika kubwelera kutsatira zionetsero zomwe amalonda pa msikawu akuchita | Ntchito za malonda zikadali chiimire pa town ya Liwonde m'boma la Machinga pomwe bata likukanika kubwelera kutsatira zionetsero zomwe amalonda pa msikawu akuchita | famale | |
Apolisi akugwiritsabe utsi okhetsa misozi kubalalitsa gulu la anthu okwiyawa omwe akugendabe Anthu ochita malonda osiyanasiyana pa Liwonde main market atseka malo awo ochitira malonda | Apolisi akugwiritsabe utsi okhetsa misozi kubalalitsa gulu la anthu okwiyawa omwe akugendabe Anthu ochita malonda osiyanasiyana pa Liwonde meyini maketi atseka malo awo ochitira malonda. | famale | |
Anthu ochita malonda osiyanasiyana pa Liwonde main market atseka malo awo ochitira malonda | Anthu ochita malonda osiyanasiyana pa Liwonde meyini maketi atseka malo awo ochitira malonda. | famale | |
Apolisi ku Jenda m'boma la Mzimba amanga wochita malonda wina, a Bleston Meya, pomuganizira kuti anali ndi matumba 72 a feteleza wa NPK wachinyengo | Apolisi ku Jenda m'boma la Mzimba amanga wochita malonda wina, a Bulesitoni Meya, pomuganizira kuti anali ndi matumba sevente thu a feteleza wa eni pikeyi wachinyengo | famale | |
Wofalitsa nkhani pa polisi ya Jenda, a MacFarlane Mseteka, wati woganiziridwayu amagulitsa fetelezayu, yemwe anali wa ma kilogalamu 50 | Wofalitsa nkhani pa polisi ya Jenda, a makifaleni Mseteka, wati woganiziridwayu amagulitsa fetelezayu, yemwe anali wa ma kilogalamu fifite | famale | |
A Mseteka ati kafukufuku waonetsa kuti iwo amaphatikiza dothi ndi feteleza ndipo pakadali pano, apolisi alanda matumba onse kuti akayezedwenso ku malo ochitira kafukufuku a Lunyangwa | A Mseteka ati kafukufuku waonetsa kuti iwo amaphatikiza dothi ndi feteleza ndipo pakadali pano, apolisi alanda matumba onse kuti akayezedwenso ku malo ochitira kafukufuku a Lunyangwa | famale | |
Potsatira izi, apolisi alangiza anthu kuti azikhala tcheru akamagula feteleza kuti asagule wachinyengo ndipo azikaneneza anthu omwe akuchita izi | Potsatira izi, apolisi alangiza anthu kuti azikhala tcheru akamagula feteleza kuti asagule wachinyengo ndipo azikaneneza anthu omwe akuchita izi | famale | |
Apolisi anathira utsi wokhetsa msonzi pomwe ochita malonda ayamba kugenda maofesi akhonsolo ya boma la Machinga | Apolisi anathira utsi wokhetsa msonzi pomwe ochita malonda ayamba kugenda maofesi akhonsolo ya boma la Machinga | famale | |
Mmodzi wa apolisi anagwira wina mwa ochita malondawa pomwe amamukokera mu maofesi a khonsoloyi Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera wapempha Amalawi kuti asiye ndale zachimidzi | Mmodzi wa apolisi anagwira wina mwa ochita malondawa pomwe amamukokera mu maofesi a khonsoloyi , Mtsogoleri wa dziko lino a LazalasiChakwera wapempha Amalawi kuti asiye ndale zachimidzi | famale | |
A Chakwera anena izi pa bwalo la zamasewero la Chinsapo UNICEF mu mzinda wa Lilongwe. Malingana ndi a Chakwera, Amalawi ambiri amakonda ndale zokangana zomwe iwo sachita | A Chakwera anena izi pa bwalo la zamasewero la Chinsapo Yunisefu mu mzinda wa Lilongwe. Malingana ndi a Chakwera, Amalawi ambiri amakonda ndale zokangana zomwe iwo sachita | famale | |
Iwo ati pali Amalawi ena amafuna kuti iwo adziyambana ndi wachiwiri wawo a Saulos Chilima. Malingana ndi a Chakwera ndale zawo ndi zachitukuko ndi zotumikira a Malawi | Iwo ati pali Amalawi ena amafuna kuti iwo adziyambana ndi wachiwiri wawo a Saulosi Chilima. Malingana ndi a Chakwera ndale zawo ndi zachitukuko ndi zotumikira a Malawi | famale | |
Nthambi yoona za kusitha kwanyengo m'dziko muno yati pali chiyembekezo chachikulu kuti mvula iyamba kugwa mawa pa 1 February m'zigawo zonse za m'dziko muno | Nthambi yoona za kusitha kwanyengo m'dziko muno yati pali chiyembekezo chachikulu kuti mvula iyamba kugwa mawa pa wani febuluwale m'zigawo zonse za m'dziko muno | famale | |
Wofalitsa nkhani Ku nthambiyi a Yobu Kachiwanda watsimikizira Times 360 Malawi za izi ponena kuti zigawo zonse m'dziko muno zikuyembekezeka kuyamba kulandira mvula mwezi wa February | Wofalitsa nkhani Ku nthambiyi a Yobu Kachiwanda watsimikiziraTaimusi fili sikisite Malawi za izi ponena kuti zigawo zonse m'dziko muno zikuyembekezeka kuyamba kulandira mvula mwezi wa Febuluwale | famale | |
Madera ambiri akuchigawo chapakati komanso ummwera kwa dziko lino akhala asakulandira mvula kwa sabata imodzi koma kuyambila lachinayi mvula iyamba kutsika kufikira kumapeto a sabatayi, atero a achiwanda | Madera ambiri akuchigawo chapakati komanso ummwera kwa dziko lino akhala asakulandira mvula kwa sabata imodzi koma kuyambila lachinayi mvula iyamba kutsika kufikira kumapeto a sabatayi, atero a achiwanda | famale | |
Izi zikudza pomwe alimi m'dziko muno akhala ali kakasi ndi ng'amba yomwe inayamba kuwononga chimanga komanso mbewu zina zakumunda | Izi zikudza pomwe alimi m'dziko muno akhala ali kakasi ndi ng'amba yomwe inayamba kuwononga chimanga komanso mbewu zina zakumunda | famale | |
Kale kale, kulibe mwa zina ma foni apamwamba, komanso makina a internet, anthu ankalumikizana polemberana kalata Angakhale pofunsira, anyamata amaponya liwu kudzera makalata | Kale kale, kulibe mwa zina ma foni apamwamba, komanso makina a intaneti, anthu ankalumikizana polemberana kalata Angakhale pofunsira, anyamata amaponya liwu kudzera makalata | famale | |
Koma mu nyengo ino chikhalidwe cholemberana makalata chidatha Koma bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (Macra) likuti chikhalidwe cholemberana makalata tisachitaye | Koma mu nyengo ino chikhalidwe cholemberana makalata chidatha Koma bungwe la Malawi komyunikeshonzi legyuletale ofolite (Makila) likuti chikhalidwe cholemberana makalata tisachitaye | famale | |
chifukwa, mwa zina, chimathandizira kumbali yozama mu mawerengedwe komanso kulemba | chifukwa, mwa zina, chimathandizira kumbali yozama mu mawerengedwe komanso kulemba | famale | |
N'chifukwa chake bungweli mothandizana ndi bungwe la Universal Postal Union lidabweretsa mpikisano wolemba kalata kwa ophunzira mu sukulu za sekondale Mpikisanowu umachitika Chaka chilichonse ndipo Chaka chino ndi cha 53 | N'chifukwa chake bungweli mothandizana ndi bungwe la yuniveso posito unyoni lidabweretsa mpikisano wolemba kalata kwa ophunzira mu sukulu za sekondale, Mpikisanowu umachitika Chaka chilichonse ndipo Chaka chino ndi cha fifite filii | famale | |
Ophunzira akuyenera kulemba kalata pa mutu womwe awupereka ndipo kuyamba kulandira makalata womwe akufunika kulembedwa pa manja adayamba pa January 22 2024 ndipo atseka pa March 31 2024 | Ophunzira akuyenera kulemba kalata pa mutu womwe awupereka ndipo kuyamba kulandira makalata womwe akufunika kulembedwa pa manja adayamba pa Januwale twente thu twente thwente folo ndipo atseka pa Malichi fete wani twente twente folo | famale | |
Wopambana mwa zina akuyembekezeka kulandira laptop, mendulo ya golide, makope komanso zipangizo zina zophunzilira | Wopambana mwa zina akuyembekezeka kulandira laputopu, mendulo ya golide, makope komanso zipangizo zina zophunzilira | famale | |
Bungwe logulitsa madzi la Blantyre Water Board lati liyamba ntchito yobwezeretsa ma meter a madzi akale omwe amatchedwa "post paid" m'chingerezi | Bungwe logulitsa madzi la Bulantaya wota bodi lati liyamba ntchito yobwezeretsa ma meter a madzi akale omwe amatchedwa "positi peyidi" m'chingerezi | famale | |
Izi zikutsatira madando omwe anthu ena akhala akupereka kubungeli kuti zikumavuta kugwiritsa ntchito mayunitsi kudzera ku ma meter a madzi a "Prepaid" omwe bungweli lakhala likupereka m'madera ena | Izi zikutsatira madando omwe anthu ena akhala akupereka kubungeli kuti zikumavuta kugwiritsa ntchito mayunitsi kudzera ku ma meter a madzi a "pulipeyidi" omwe bungweli lakhala likupereka m'madera ena | famale | |
M'chikalata chomwe bungweli latulutsa, lati liyamba kuchotsa ma metre atsopanowa ndipo pakadali pano likukumana ndi kampani zina zomwe zingapereke makina atsopano omwe angagwire ntchito bwino | M'chikalata chomwe bungweli latulutsa, lati liyamba kuchotsa ma mita atsopanowa ndipo pakadali pano likukumana ndi kampani zina zomwe zingapereke makina atsopano omwe angagwire ntchito bwino | famale | |
Mfumu yayikulu Makanjira yati anthu ochokera m'dera mwake omwe anathamangitsidwa m'minda yawo ndi Asilikali adziko la Mozambique tsopano ayambanso kulima m'mindayo | Mfumu yayikulu Makanjira yati anthu ochokera m'dera mwake omwe anathamangitsidwa m'minda yawo ndi Asilikali adziko la Mozambiki tsopano ayambanso kulima m'mindayo | famale | |
A Makanjira ati iwo pamodzi ndi mafumu ena anakakambirana ndi mkulu wa asilikali aku Mozambique m'derali komanso mafumu awo, kuti alole Amalawi kuti azikalima m'mindayo monga momwe zidaliri kale | A Makanjira ati iwo pamodzi ndi mafumu ena anakakambirana ndi mkulu wa asilikali aku Mozambiki m'derali komanso mafumu awo, kuti alole Amalawi kuti azikalima m'mindayo monga momwe zidaliri kale | famale | |
Sabata yathayi asilikali adziko la Mozambique anatchetcha chimanga m'minda ya nzika zina za dziko lino ponena kuti mindayo Ili m'dziko la Mozambique malingana ndi malire atsopano | Sabata yathayi asilikali adziko la Mozambiki anatchetcha chimanga m'minda ya nzika zina za dziko lino ponena kuti mindayo Ili m'dziko la Mozambiki malingana ndi malire atsopano | famale | |
Ngakhale izi zili chomwechi, a Makanjira ati n'kofunika kuti zokambirana pakati pa maiko a Malawi ndi Mozambique zipitilire pofuna kupeza yankho lokhazikika m'derali | Ngakhale izi zili chomwechi, a Makanjira ati n'kofunika kuti zokambirana pakati pa maiko a Malawi ndi Mozambiki zipitilire pofuna kupeza yankho lokhazikika m'derali | famale | |
Ogwira tchito ku Kampani ya Mota-Engil mu mzinda wa Lilongwe ayamba kunyanyala ntchito Times 360 Malawi yafika ku malo amodzi omwe anthu asonkhana | Ogwira tchito ku Kampani ya Mota-Enjelo mu mzinda wa Lilongwe ayamba kunyanyala ntchito, Taimusi fili sikisite Malawi yafika ku malo amodzi omwe anthu asonkhana | famale | |
Kumeku ndi m'mbali mwa msewu wa Mzimba (Mzimba Street) umene ukumangidwa mu mzinda wa Lilongwe | Kumeku ndi m'mbali mwa msewu wa Mzimba (Mzimba sitiliti) umene ukumangidwa mu mzinda wa Lilongwe | famale | |
Mmodzi wa anthu ogwira ntchito ku kampaniyi wauza Times 360 Malawi kuti akhala zaka 6 akugwira ntchito osawakwezera malipiro. | Mmodzi wa anthu ogwira ntchito ku kampaniyi wauza Taimusi fili sikisite Malawi kuti akhala zaka sikisi akugwira ntchito osawakwezera malipiro. | famale | |
Ndipo yemwe amayankhulira kampaniyi aThomas Chafunya wati akudziwa za nkhaniyi koma akuluakulu a kampaniyi akukambirana za madandaulowa | Ndipo yemwe amayankhulira kampaniyi aThomasi Chafunya wati akudziwa za nkhaniyi koma akuluakulu a kampaniyi akukambirana za madandaulowa | famale | |
Apolisi ku Lilongwe amanga wolemba nkhani pa masamba a mchezo Rodgers Kadiso pomuganizira kuti amabera anthu powanamiza kuti awathandiza kupita m'dziko la Israel kukagwira ntchito zakuminda | Apolisi ku Lilongwe amanga wolemba nkhani pa masamba a mchezo lojasi Kadiso pomuganizira kuti amabera anthu powanamiza kuti awathandiza kupita m'dziko la izilaeli kukagwira ntchito zakuminda | famale | |
Mneneri wa Polisi a Peter Kalaya watsimikiza za izi ndipo wati a Kadiso amachita izi pogwiritsa ntchito dzina la mneneri wa mtsogoleri wa dziko lino a Anthony Kasunda | Mneneri wa Polisi a Pita Kalaya watsimikiza za izi ndipo wati a Kadiso amachita izi pogwiritsa ntchito dzina la mneneri wa mtsogoleri wa dziko lino a Anthone Kasunda | famale | |
A Kalaya ati a Kadiso, omwe pakadali pano akusungidwa ku polisi ya Lingadzi, amauza anthuwo pogwiritsa ntchito dzina la a Kasunda | A Kalaya ati a Kadiso, omwe pakadali pano akusungidwa ku polisi ya Lingadzi, amauza anthuwo pogwiritsa ntchito dzina la a Kasunda | famale | |
kuti iwo awathandiza kupita ku Israel ngati angapereke ndalama yokwana K150,000 | kuti iwo awathandiza kupita ku Izilaeli ngati angapereke ndalama yokwana handede andi fifite sauzande kwacha | famale | |
A Kasunda ndi omwe adzadandaula ku polisi kuti dzina lawo limagwiritsidwa ntchito kuchita zaumbanda ndipo tawamanga a Kadiso | A Kasunda ndi omwe adzadandaula ku polisi kuti dzina lawo limagwiritsidwa ntchito kuchita zaumbanda ndipo tawamanga a Kadiso | famale | |
Pakadali pano tionkhetsa kuti ndi ndalama zingati zomwe adalandira chifukwa madandaulo alipo angapo, atero a Kalaya | Pakadali pano tionkhetsa kuti ndi ndalama zingati zomwe adalandira chifukwa madandaulo alipo angapo," atero a Kalaya | famale | |
Nthawi ikamati 6 koloko mmawa, nsima imakhala kuti yapsa kale pa depoti ya Mzimba, mu mzinda wa Mzuzu | Nthawi ikamati sikisi koloko mmawa, nsima imakhala kuti yapsa kale pa depoti ya Mzimba, mu mzinda wa Mzuzu | famale | |
Anthu ena akumadya nsima mmawa ngati kadzutsa ndipo malingana ndi ogulitsa, chiwerengero cha anthu otero chakwera kamba ka kusowa komanso kudula kwa shuga mu nzindawu | Anthu ena akumadya nsima mmawa ngati kadzutsa ndipo malingana ndi ogulitsa, chiwerengero cha anthu otero chakwera kamba ka kusowa komanso kudula kwa shuga mu nzindawu | famale | |
Kit Master wa timu ya Flames Richard Justin Zawazawa, yemwe amutchuka ndi dzina lokuti Dinho, walandira mphatso ya nyumba pa malo okwana ndime ya 15m ndi 30m, omwe bungwe la ana a m'mudzi anamugulira | Kiiti masitawa timu ya fulemuzi litchadi jesitini Zawazawa, yemwe amutchuka ndi dzina lokuti Dinyo, walandira mphatso ya nyumba pa malo okwana ndime ya fifitini mitazi ndi fete mitazi, omwe bungwe la ana a m'mudzi anamugulira | famale | |
Apolisi m'boma la Kasungu, amanga a Goodson Alli, a zaka 35, atapezeka ndi ma plasma TV anayi , omwe akuwaganizira kuti ndi obedwa. | Apolisi m'boma la Kasungu, amanga a Gudusoni Ali, a zaka fete faifi, atapezeka ndi ma pulazima tivi anayi , omwe akuwaganizira kuti ndi obedwa. | famale | |
Malingana ndi wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za polisi m'bomali, a Miracle Mkozi, woganiziridwawayu adamangidwa m'mudzi wa Chitete, pa 28 January, chaka chino, atatsinidwa khutu ndi anthu akufuna kwabwino | Malingana ndi wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za polisi m'bomali, a Milako Mkozi, woganiziridwawayu adamangidwa m'mudzi wa Chitete, pa twente eiti januwale, chaka chino, atatsinidwa khutu ndi anthu akufuna kwabwino | famale | |
Titakachita chipikisheni ku nyumba kwa woganiziridwawayu, tidapezadi katunduyu, ndipo titawafunsa kuti afotokoze bwino za katunduyo adalephera kuyankha, atero a Mkozi | Titakachita chipikisheni ku nyumba kwa woganiziridwawayu, tidapezadi katunduyu, ndipo titawafunsa kuti afotokoze bwino za katunduyo adalephera kuyankha, atero a Mkozi | famale | |
A Alli, omwe amachokera m'mudzi wa Dzimbiri, mfumu yaikulu Jalasi, m'boma la Mangochi, akuyembekezeka kukonekera ku bwalo la milandu posachedwapa komwe akayankhe mlandu wopezeka ndi katundu wobedwa | A Ali, omwe amachokera m'mudzi wa Dzimbiri, mfumu yaikulu Jalasi, m'boma la Mangochi, akuyembekezeka kukonekera ku bwalo la milandu posachedwapa komwe akayankhe mlandu wopezeka ndi katundu wobedwa | famale | |
Mneneri wa chipani cha Malawi Congress Party (MCP) Mchigawo cha pakati a Abraham Liwonde lero wapereka thandizo kwa anthu amene anakhudzidwa ndi ngozi ya kusefukira kwa madzi m'dera la mfumu yayikulu Dzoole, m'boma la Dowa | Mneneri wa chipani cha Malawi Kongelesi Pate (Emu si pi) Mchigawo cha pakati a Abulahamu Liwonde lero wapereka thandizo kwa anthu amene anakhudzidwa ndi ngozi ya kusefukira kwa madzi m'dera la mfumu yayikulu Dzoole, m'boma la Dowa | famale | |
Wina mwa katundu amene waperekedwa ndi matumba a chimanga, mabulangete, sopo, sugar, mafuta ophikira, ziwiya zotungira madzi ndi K20, 000, banja lirilonse lokhudzidwa | Wina mwa katundu amene waperekedwa ndi matumba a chimanga, mabulangete, sopo, shuga, mafuta ophikira, ziwiya zotungira madzi ndi Twente sauzande kwacha, banja lirilonse lokhudzidwa | famale | |
Abraham Liwonde wauza Times 360 Malawi kuti anachiona chanzeru kudzathandiza abale awo omwe anakhudzidwa ndi ngozi yamadzi, komanso ngati mwana wochokera kuderali | Abraham Liwonde wauza Taimusi fili sikisite Malawi kuti anachiona chanzeru kudzathandiza abale awo omwe anakhudzidwa ndi ngozi yamadzi, komanso ngati mwana wochokera kuderali | famale | |
Amfumu Soko amene anayimira mfumu yayikulu Dzoole ayamikira a Liwonde kaamba kathandizoli ndipo iwo ati labwera panthawi yake pomwe anthuwa akusowa zinthu zosiyanaaiyana | Amfumu Soko amene anayimira mfumu yayikulu Dzoole ayamikira a Liwonde kaamba kathandizoli ndipo iwo ati labwera panthawi yake pomwe anthuwa akusowa zinthu zosiyanaaiyana | famale | |
Phungu wa kunyumba ya Malamulo wa dera la kumvuma kwa Machinga, yemweso ndi mkulu womema anthu mu chipani cha UDF, a Esther Jolobala | Phungu wa kunyumba ya Malamulo wa dera la kumvuma kwa Machinga, yemweso ndi mkulu womema anthu mu chipani cha Yu di efu, a Esita Jolobala | famale | |
wati ndi wokhumudwa ndi zomwe a Uladi Mussa anayankhula dzulo (Lolemba) m'boma la Salima, pomwe amalowa m'chipani cha MCP | wati ndi wokhumudwa ndi zomwe a Uladi Musa anayankhula dzulo (Lolemba) m'boma la Salima, pomwe amalowa m'chipani cha Emu si pi | famale | |
A Jolobala ati a Mussa apepese kwa amayi m'dziko muno; Iwo ati mawu a Uladi Mussa asambula ulemu wa amayi | A Jolobala ati a Musa apepese kwa amayi m'dziko muno; Iwo ati mawu a Uladi Mussa asambula ulemu wa amayi | famale | |
pomwe iwo anayerekeza kuimitsidwa kwawo m'chipani cha DPP kwa miyezi isanu ndi inayi, 9, ngati ali ndi pakati | pomwe iwo anayerekeza kuimitsidwa kwawo m'chipani cha Di pi pii kwa miyezi isanu ndi inayi, naini, ngati ali ndi pakati | famale | |
Malingana ndi a Jolobala, a Mussa adagwiritsa ntchito Chichewa cholakwika ndipo ngati mmodzi wa amayi, ndi okhumudwa ndi mawuwa Koma a Mussa ati sangayankhulepo chilichonse pa nkhaniyi | Malingana ndi a Jolobala, a Musa adagwiritsa ntchito Chichewa cholakwika ndipo ngati mmodzi wa amayi, ndi okhumudwa ndi mawuwa Koma a Musa ati sangayankhulepo chilichonse pa nkhaniyi | famale | |
Pafupifupi nyumba iliyonse ya m'midzi ya Alekaawo komanso Khisimisi, pansi pa mfumu yaikulu Ngabu m'boma la Chikwawa yakwanitsa kumanganso chimbudzi | Pafupifupi nyumba iliyonse ya m'midzi ya Alekaawo komanso Khisimisi, pansi pa mfumu yaikulu Ngabu m'boma la Chikwawa yakwanitsa kumanganso chimbudzi | famale | |
kutsatira kugwa kwa nyumba za ulemuzi kaamba ka mphepo yamkuntho ya Cyclone Freddy chaka chatha | kutsatira kugwa kwa nyumba za ulemuzi kaamba ka mphepo yamkuntho ya saikuloni fulede chaka chatha | famale | |
Nyakwawa yaikulu Jombo yati kusowa kwa malo odzithandizirawa kunaonjezera chiopsezo cha matenda osiyanasiyana, monga kolera Mabungwe a Oxfam | Nyakwawa yaikulu Jombo yati kusowa kwa malo odzithandizirawa kunaonjezera chiopsezo cha matenda osiyanasiyana monga kolera. Mabungwe a Okosi famu | famale | |
komanso Hygiene Village Project ndi amene atsogolera ntchito yolimbikitsa kuti nyumba iliyonse ikhale ndi chimbudzi chakechake ndi cholinga chopititsa patsogolo ukhondo komanso kupewa matenda | komanso haijini vileji pulojekiti ndi amene atsogolera ntchito yolimbikitsa kuti nyumba iliyonse ikhale ndi chimbudzi chakechake ndi cholinga chopititsa patsogolo ukhondo komanso kupewa matenda | famale | |
Wachiwiri kwa oyimira bungwe la Unicef kuno ku Malawi a Gerrit Malitz wati ndi okhutira ndi momwe ntchito yolimbikitsira anthu kutenga gawo polondoloza ukhondo ikuyendera m'boma la Chikwawa | Wachiwiri kwa oyimira bungwe la yunisefu kuno ku Malawi a geliti malizi wati ndi okhutira ndi momwe ntchito yolimbikitsira anthu kutenga gawo polondoloza ukhondo ikuyendera m'boma la Chikwawa | famale | |
Bungwe la Zoe Empowers Malawi lero lapereka zipangizo zosiyanasiyana kwa achinyamata okwana 120 | Bungwe la Zowe impawazi Malawi lero lapereka zipangizo zosiyanasiyana kwa achinyamata okwana handede andi twente | famale | |
ochokera m'madera osiyanasiyana m'boma la Dowa, za ndalama yokwana K57 miliyoni, zoti ziwathandizire kuyamba zamalonda | ochokera m'madera osiyanasiyana m'boma la Dowa, za ndalama yokwana fifite seveni miliyoni kwacha, zoti ziwathandizire kuyamba zamalonda | famale | |
Zina mwa zipangizo zimene bungweli lapereka ndi makina osokera, zipangizo za Saloon, zipangizo zometera, zipangizo za bizinesi yowotchelera, zipangizo za ukalipentala ndi zina zambiri | Zina mwa zipangizo zimene bungweli lapereka ndi makina osokera, zipangizo za Saloon, zipangizo zometera, zipangizo za bizinesi yowotchelera, zipangizo za ukalipentala ndi zina zambiri | famale | |
Mlangizi wamkulu wa bungweli a Esther Chinkhadze wauza Times 360 Malawi kuti bungwe lawo lapereka zipangizozi | Mlangizi wamkulu wa bungweli a Esita Chinkhadze wauza Taimusi fili sikisite Malawi kuti bungwe lawo lapereka zipangizozi | famale | |
ndi cholinga choti achinyamatawa athe kukhala odzidalira komanso kufuna pothetsa umphawi pakati pa achinyamata omwe ali ovutikitsitsa | ndi cholinga choti achinyamatawa athe kukhala odzidalira komanso kufuna pothetsa umphawi pakati pa achinyamata omwe ali ovutikitsitsa | famale | |
A Chinkhadze apempha achinyamatawa kuti akagwiritse bwino ntchito zipangizozi cholinga choti miyoyo yawo isinthe | A Chinkhadze apempha achinyamatawa kuti akagwiritse bwino ntchito zipangizozi cholinga choti miyoyo yawo isinthe | famale | |
Mmodzi wa achinyamatawa Thokozani Petro wochokera dela la Takondwela Msatsi, mfumu yayikulu Dzoole wati imene ayambe kaamba ka zipangizozi | Mmodzi wa achinyamatawa Thokozani Petulo wochokera dela la Takondwela Msatsi, mfumu yayikulu Dzoole wati imene ayambe kaamba ka zipangizozi | famale | |
imuthandiza kupeza chakudya komanso sukulu fees ndi zina zambiri zofunika pa moyo wa tsiku ndi tsiku | imuthandiza kupeza chakudya komanso sukulu fizi ndi zina zambiri zofunika pa moyo wa tsiku ndi tsiku | famale | |
Pali chiyembekezo kuti anthu osaona okwana 1,000 ayamba kuona tsopano, kutsatira thandizo la madotolo ochoka m'dziko la Brazil omwe athandize anthuwa | Pali chiyembekezo kuti anthu osaona okwana wani sauzande ayamba kuona tsopano, kutsatira thandizo la madotolo ochoka m'dziko la Bulazilu omwe athandize anthuwa | famale | |
Kazembe wa dziko la Brazil kuno ku Malawi Dr Breno Tavares Nogueira ndiye atsogolere ntchitoyi m'miyezi iwiri ikudzayi | Kazembe wa dziko la Bulazilu kuno ku Malawi Dokota Buleno Tavalesi Nogwela ndiye atsogolere ntchitoyi m'miyezi iwiri ikudzayi | famale | |
A Nogueira, lero masanawu, adakumana ndi mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ndipo akambirananso ma pulani omanga sukulu yosula madotolo a maso komanso opanga ma opaleshoni a maso | A Nogwela, lero masanawu, adakumana ndi mtsogoleri wa dziko lino a Lazalasi Chakwera ndipo akambirananso ma pulani omanga sukulu yosula madotolo a maso komanso opanga ma opaleshoni a maso | famale | |
Polankhula ndi atolankhani atamaliza zokambiranazo, a Nogueira ati iwo pamodzi ndi madotolo a maso a ku Brazil abwera kuno ku Malawi kudzathandiza anthu 1,000 osaona ndi ma opaleshon | Polankhula ndi atolankhani atamaliza zokambiranazo, a Nogwelaa ati iwo pamodzi ndi madotolo a maso a ku Bulazilu abwera kuno ku Malawi kudzathandiza anthu wanu sauzande osaona ndi ma opaleshon | famale | |
Nduna ya zaumoyo a Khumbize Kandodo Chiponda yati mtsogoleri wa dziko lino ndi wokondwa ndi thandizoli chifukwa vuto la khungu kuno ku Malawi ndi lalikulu | Nduna ya zaumoyo a Khumbize Kandodo Chiponda yati mtsogoleri wa dziko lino ndi wokondwa ndi thandizoli chifukwa vuto la khungu kuno ku Malawi ndi lalikulu | famale | |
ndipo pali anthu ambiri oti atha kuonanso atalandira thandizo loyenelera | ndipo pali anthu ambiri oti atha kuonanso atalandira thandizo loyenelera | famale | |
Mbali ya boma yamaliza kupelekera umboni pa mlandu omwe a Bon Kalindo akuwaganizira kuti anayambitsa ziwawa pa zionetsero zomwe anakonza ku Zomba pa 23 November, chaka chatha | Mbali ya boma yamaliza kupelekera umboni pa mlandu omwe a Boni Kalindo akuwaganizira kuti anayambitsa ziwawa pa zionetsero zomwe anakonza ku Zomba pa twente filii Novemba, chaka chatha | famale | |
Mboni ziwiri ndi zomwe zapelekera umboni lero, kufikitsa chiwerengo cha mboni kufika zisanu pa mlanduwu | Mboni ziwiri ndi zomwe zapelekera umboni lero, kufikitsa chiwerengo cha mboni kufika zisanu pa mlanduwu | famale | |
Imodzi mwa mbonizi yemwe ndi mkulu wapamalo pogulitsa zakumwa pa Kangaroo Trading, a Christopher Ndanga, wauza bwalo lamilandu lero | Imodzi mwa mbonizi yemwe ndi mkulu wapamalo pogulitsa zakumwa pa Kangalu thileding’i, a khilisitofa Ndanga, wauza bwalo lamilandu lero | famale | |
kuti zakumwa komanso katundu wandalama zokwana K8.5 million zinaongeka kutsatira ziwawa zomwe zinayamba mkatikati mwa zionetserezo | kuti zakumwa komanso katundu wandalama zokwana Eiti pointi faifi miliyoni kwacha zinaongeka kutsatira ziwawa zomwe zinayamba mkatikati mwa zionetserezo | famale | |
Iwo ati mwa zina, anthu anaba ma crate a mowa osiyanasiyana pamalopo, omwe ali ku dera la Chinamwali ku Zomba | Iwo ati mwa zina, anthu anaba ma kileti a mowa osiyanasiyana pamalopo, omwe ali ku dera la Chinamwali ku Zomba | famale | |
Mboni zina za boma ndi a Isaac Mdala, Stella Likukuta, Harry Dongolosi komanso Inspector Gauti, omwe onse ndi apolisi | Mboni zina za boma ndi a aizeki Mdala, Sitela Likukuta, Hale Dongolosi komanso insipekita Gauti, omwe onse ndi apolisi | famale | |
Oweruza mlandu a Martin Chipofya akuyembekezeka kudzapereka chigamulo ngati a Kalindo ali ndi mlandu woti ayankhe pa 21 February | Oweruza mlandu a Martin Chipofya akuyembekezeka kudzapereka chigamulo ngati a Kalindo ali ndi mlandu woti ayankhe pa twente wani febuluwale February | famale | |
Atsikana, mumatha kucheza? Yesani mwayi ndi Onesimus kuti mudzakadye naye chakudya cha madzulo pa Valentines Day, komanso kudzakhala mpando wa patsogolo pamene adzaimbe mwapadera patsikuli | Atsikana, mumatha kucheza? Yesani mwayi ndi Onesimus kuti mudzakadye naye chakudya cha madzulo pa Valentaizi dei, komanso kudzakhala mpando wa patsogolo pamene adzaimbe mwapadera patsikuli | famale | |
Kuti mupambane, chitani izi: Tsatirani tsamba la Times 360 Malawi pa Facebook Pangani tag anzanu atatu ndi kutsitsa mfundo m'munsimu yomukopa Onesimus | Kuti mupambane, chitani izi: Tsatirani tsamba la Taimusi fili sikisite Malawi pa Fesibuku Pangani tagi anzanu atatu ndi kutsitsa mfundo m'munsimu yomukopa Onesimus | famale | |
Lembani nyimbo zitatu za Onesimus, Tsiku layamba bwanji?. Osayiwala kulengeza business yanu mu pologalamu ya Geni Nkujiya | Lembani nyimbo zitatu za Onesimus, Tsiku layamba bwanji?. Osayiwala kulengeza business yanu mu pologalamu ya Geni Nkujiya | famale | |
Pologalamu iyi imapeleka danga kwa a business zing'onozing'ono kuti athe kulengeza malonda pa mtengo wofewa. Tchayani lamya pa 0883397257 kuti mulumikizane nafe | Pologalamu iyi imapeleka danga kwa a business zing'onozing'ono kuti athe kulengeza malonda pa mtengo wofewa. Tchayani lamya pa zilo eiti eiti filii filii , naini seveni thu faifi seveni, kuti mulumikizane nafe | famale | |
Chipani cha DPP chadzudzula mchitidwe wong'amba nsalu ya chipanichi umene unachitidwa ndi otsatira a Kondwani Nankhumwa Lamulungu lapitali | Chipani cha Di pi pii chadzudzula mchitidwe wong'amba nsalu ya chipanichi umene unachitidwa ndi otsatira a Kondwani Nankhumwa Lamulungu lapitali | famale | |
Mu chikalata chomwe mneneri wa chipanichi a Shadric Namalomba atulutsa, iwo ati zomwe anachita otsatira a a Nankhumwa ndi zachikale ndiponso zomvetsa chisoni chifukwa zidaonetseratu kuti anthuwo sakudziwa chomwe akulondola | Mu chikalata chomwe mneneri wa chipanichi a Shadileki Namalomba atulutsa, iwo ati zomwe anachita otsatira a a Nankhumwa ndi zachikale ndiponso zomvetsa chisoni chifukwa zidaonetseratu kuti anthuwo sakudziwa chomwe akulondola | famale |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.