audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Iwo ati, ndi zomvetsanso chisoni kuti anthuwo amaonetsa mkwiyo woterowo pamalo omwe ali mbali ya mpingo
Iwo ati, ndi zomvetsanso chisoni kuti anthuwo amaonetsa mkwiyo woterowo pamalo omwe ali mbali ya mpingo
famale
Chipanichi chapempha ochitsatira kuti asabwezere choipa Kwa otsatira a a Nankhumwa koma apereke chidwi pofuna kuthana ndi matenda a zachuma omwe abwera chifukwa chakulephera Kwa boma
Chipanichi chapempha ochitsatira kuti asabwezere choipa Kwa otsatira a a Nankhumwa koma apereke chidwi pofuna kuthana ndi matenda a zachuma omwe abwera chifukwa chakulephera Kwa boma
famale
Kumva akumayesesa kumva komano kulankhula chichewa kukumvutilapo Maskal
Kumva akumayesesa kumva komano kulankhula chichewa kukumvutilapo Masiko
famale
Usiku uno akhala ali ku illusionz kumene akuyimba ndi azimzake amene adali limodzi kale kale mu Ndefeyo entertainment, Piksy ndi Armstrong ( Onesimus )
Usiku uno akhala ali ku iluzyonzi kumene akuyimba ndi azimzake amene adali limodzi kale kale mu Ndefeyo entatenimenti, pikise ndi Amusitulong’o ( Onesimasi )
famale
Tuyenda mwa cheu cheu, Tumachita kukanika kuwayika pa status, Tukanika kumasuka kumabello Zibwenzi za anthu otchuka zanyinyilika
Tuyenda mwa cheu cheu, Tumachita kukanika kuwayika pa sitetasi, Tukanika kumasuka kumabelo. Zibwenzi za anthu otchuka zanyinyilika
famale
Zati tsopano a Malawi awonjeza ntopola ndipo kupanga chibwenzi ndi Celeb, automatically anthu maso akumakhala pa iwe ndipo zumawopsa
Zati tsopano a Malawi awonjeza ntopola ndipo kupanga chibwenzi ndi selebu, otomatikale anthu maso akumakhala pa iwe ndipo zumawopsa
famale
Ine olo kuma belo kukasankha dzovala ndimapita mwa nkhawa. Nthawi inayake ena adandijambulapo ndikusankha zovala nkukaponya pa gulupu ati akazi a uje amangokhalila ma belo
Ine olo kuma bello kukasankha dzovala ndimapita mwa nkhawa. Nthawi inayake ena adandijambulapo ndikusankha zovala nkukaponya pa gulupu ati akazi a uje amangokhalila ma belo
famale
Pano nduyenda mwa cheu cheu kuopa kuti ena andiona ndipo awatengetsa amunanga acelebu - Walila mtsikana wina amene akuchita chibwenzi ndi oyimba wina otchuka
Pano nduyenda mwa cheu cheu kuopa kuti ena andiona ndipo awatengetsa amunanga aselebu - Walila mtsikana wina amene akuchita chibwenzi ndi oyimba wina otchuka
famale
Nsaname, ine olo mkazi wanga oyimba kumuyika pa status tili limodzi pakhomo ndumachita kuopa. Sindingathe kumuyika pa status alibe make up atavala chitenje chake koma ayi ena atola screenshot nkachipeza muma group
Nsaname, ine olo mkazi wanga oyimba kumuyika pa status tili limodzi pakhomo ndumachita kuopa. Sindingathe kumuyika pa status alibe meki apu atavala chitenje chake koma ayi ena atola sikilini shoti nkachipeza muma gulupu
famale
Nane sindumasuka mokwanila. Inu kugwidwa ndi munthu otchuka nawe umafunika kulimba mtima , Mwanuna wina amene naye adagwila mkazi wocelebuka walila
Nane sindumasuka mokwanila. Inu kugwidwa ndi munthu otchuka nawe umafunika kulimba mtima, Mwanuna wina amene naye adagwila mkazi wocelebuka walila
famale
Apolisi ku Zomba amanga bambo wa zaka 25, Chimwemwe Zololo pomuganizira kuti amagulitsa mwana wake wammuna womupeza wa zaka ziwiri
Apolisi ku Zomba amanga bambo wa zaka twente faifi, Chimwemwe Zololo pomuganizira kuti amagulitsa mwana wake wammuna womupeza wa zaka ziwiri
famale
Othandizira kufalitsa nkhani ku polisi ya Zomba, a Aaron Chilala ati mkuluyu akuganiziridwa kuti anapalamula mlanduwu loweruka lapitali m'mudzi wa Njala, dera la mfumu yaikulu Mwambo m'bomali
Othandizira kufalitsa nkhani ku polisi ya Zomba, a Aloni Chilala ati mkuluyu akuganiziridwa kuti anapalamula mlanduwu loweruka lapitali m'mudzi wa Njala, dera la mfumu yaikulu Mwambo m'bomali
famale
Bamboyu patsikuli anaimbira foni mpondamatiki wina wakuderali, kumutsatsa malonda amwanayo
Bamboyu patsikuli anaimbira foni mpondamatiki wina wakuderali, kumutsatsa malonda amwanayo
famale
Mpondamatikiyu anauza mkuluyu kuti akumane ndi ogulitsayu pamalo pena pomwe anatsina khutu apolisi, anafotokoza a Chilala
Mpondamatikiyu anauza mkuluyu kuti akumane ndi ogulitsayu pamalo pena pomwe anatsina khutu apolisi, anafotokoza a Chilala
famale
Apolisi anagwira mkuluyo pamalo omwe anagwirizana kukagulitsa mwanayo kwa mpondamatikiyo
Apolisi anagwira mkuluyo pamalo omwe anagwirizana kukagulitsa mwanayo kwa mpondamatikiyo
famale
Apolisi atafunsa akazi ake ngati amadziwapo za nkhaniyi, iwo anati bamboyu anawauza za nkhaniyi pomwe anati amafuna kuthetsa mavuto azachuma omwe amakumana nawo, koma mkaziyu anawaletsa za ganizoli

Timu ya mpira wa manja ya Islanders Sisters yakhala kwatswiri itagonjetsa team ya DYCO sisters pa masewero omwe achitika Lamulungu pa bwalo la Likoma community netball ground m'boma la Likoma
Timu ya mpira wa manja ya ailandazi sisitazi yakhala kwatswiri itagonjetsa timu ya Daiko sisitazi pa masewero omwe achitika Lamulungu pa bwalo la Likoma comyunite netibo galaundi m'boma la Likoma
famale
mu mpikisano omwe anachitisa ndi phungu la dera la bomali a Christopher Ashems Songwe. Polankhula ndi Times 360 Malawi, mphunzitsi wamkulu wa timuyi a Stevie Ndube Chirwa
mu mpikisano omwe anachitisa ndi phungu la dera la bomali a Khilisitofa Ashimuzi Songwe. Polankhula ndi Taimusi fili sikisite Malawi, mphunzitsi wamkulu wa timuyi a Sitivi Ndube Chirwa
famale
wati ndi wosangalala ndi chipambano chawo ndipo wapempha osewera ake kuti akhalebe ochilimika kuti apitirize kupambana m'ma ligi ena mtsogolomu
wati ndi wosangalala ndi chipambano chawo ndipo wapempha osewera ake kuti akhalebe ochilimika kuti apitirize kupambana m'ma ligi ena mtsogolomu
famale
Ndipo m'mawu ake, mphunzitsi wa timu ya DYCO sisters, Njikho Chipewa wayamikira osewera ake poikapo mtima pamasewerowa ndipo wati ali ndi chikhulupiliro kuti ulendo wina adzakhala opambana
Ndipo m'mawu ake, mphunzitsi wa timu ya Daiko sisitazi, Njikho Chipewa wayamikira osewera ake poikapo mtima pamasewerowa ndipo wati ali ndi chikhulupiliro kuti ulendo wina adzakhala opambana
famale
Mpikisanowu wachitika ndi ndalama zokwana K1.5 million ndipo Timu ya Islanders sisters Yatenga ndalama zokwana K230,000
Mpikisanowu wachitika ndi ndalama zokwana wani pointi fafi muliyoni kwacha ndipo Timu ya ailandazi sisitazi Yatenga ndalama zokwana thu nandede andi fete sauzande kwacha
famale
komanso Chikho pomwe Timu ya Daiko sisitazi, yomwe yakhala yotsatira, yatenga ndalama zokwana handede andi eyite sauzande kwacha
komanso Chikho pomwe Timu ya Daiko sisitazi, yomwe yakhala yotsatira, yatenga ndalama zokwana handede andi eyite sauzande kwacha
famale
Amalawi awapempha kuti apitirize kulondoloza mmene ndalama zimene boma limabwereka zikugwilira ntchito m'dziko muno
Amalawi awapempha kuti apitirize kulondoloza mmene ndalama zimene boma limabwereka zikugwilira ntchito m'dziko muno
famale
Poyankhula m'boma la Mzimba ndi adindo aku khonsolo ya M'mbelwa, mkulu wa bungwe la Malawi Economic Justice Network-Mejn, a Bertha Lipipa Phiri wati izi zithandiza kuti boma lisatenge ngongole zosafunikira
Poyankhula m'boma la Mzimba ndi adindo aku khonsolo ya M'mbelwa, mkulu wa bungwe la Malawi ikonomiki netiweki jasitisi-Mejini, a Befa Lipipa Phiri wati izi zithandiza kuti boma lisatenge ngongole zosafunikira
famale
Iwo ati ngakhale kuti boma layamba kubweretsa poyera ngongole zimene limatenga, Amalawi akuyenera kudziwa mwakuya phindu la ndalama zotero pozindikira kuti nzika za dziko lino ndizo zimabweza kudzera kumisonkho

Wapampando wa mabungwe omwe siaboma ku Mzimba a Christopher Melele ati awonesetsa kuti zitukuko zomwe zikuchitika kudzera ku ndalama za ngongole yaboma zithe munthawi yake
Wapampando wa mabungwe omwe siaboma ku Mzimba a khilisitofa Melele ati awonesetsa kuti zitukuko zomwe zikuchitika kudzera ku ndalama za ngongole yaboma zithe munthawi yake
famale
ndi cholinga choti chiongola dzanja chisachuluke pobweza Pakadali pano, boma liri ndi ngongole pafupifupi K13 trillion
ndi cholinga choti chiongola dzanja chisachuluke pobweza Pakadali pano, boma liri ndi ngongole pafupifupi fetini thililiyoni kwacha
famale
Anthu omwe anabwera kudzaonera mwambo umene mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera amalandira sukulu m'boma la Salima, kukanganirana zitenje zaulere zomwe zimagawidwa pamalapo
Anthu omwe anabwera kudzaonera mwambo umene mtsogoleri wa dziko lino a Lazalasi Chakwera amalandira sukulu m'boma la Salima, kukanganirana zitenje zaulere zomwe zimagawidwa pamalapo
famale
Wachiwiri kwa wa mkulu woyang'anira ntchito za ulimi m'boma la Dedza a Aina Chikankheni, wati pa anthu 100 aliwonse, anthu khumi ndi asanu ndi omwe akhudzidwa ndi njala m'boma la Dedza
Wachiwiri kwa wa mkulu woyang'anira ntchito za ulimi m'boma la Dedza a Aina Chikankheni, wati pa anthu handede aliwonse, anthu khumi ndi asanu ndi omwe akhudzidwa ndi njala m'boma la Dedza
female
A Chikankheni anena izi Lolemba m'dera la mfumu yayikulu Tambala m'bomali pamene phungu wa nyumba ya malamulo wa dera la kumpoto kwa bomali
A Chikankheni anena izi Lolemba m'dera la mfumu yayikulu Tambala m'bomali pamene phungu wa nyumba ya malamulo wa dera la kumpoto kwa bomali
female
a Savel Kachifwafwa amagawa mbewu ya chinangwa kwa maanja oposela 500 ngati njira imodzi yofuna kuthana ndi njala
a Savo Kachifwafwa amagawa mbewu ya chinangwa kwa maanja oposela faifi handede ngati njira imodzi yofuna kuthana ndi njala
female
M'mawu ake, Mfumu Yayikulu Tambala inati njala m'dera mwake yafika posauzana pomwe mango komanso zikhawo zomwe anthu amadalira nazo zatha
M'mawu ake, Mfumu Yayikulu Tambala inati njala m'dera mwake yafika posauzana pomwe mango komanso zikhawo zomwe anthu amadalira nazo zatha
female
A Tambala ati alimbikitsa anthu awo kuti ayike patsogolo ulimi wa chinangwa omwe umachita bwino mu nyengo zonse ponena kuti ili ndi yankho lokhalo lomwe angagonjetsere njala m'derali
A Tambala ati alimbikitsa anthu awo kuti ayike patsogolo ulimi wa chinangwa omwe umachita bwino mu nyengo zonse ponena kuti ili ndi yankho lokhalo lomwe angagonjetsere njala m'derali
female
Bwalo la milandu la First Grade Magistrate ku Mchinji lalamula a Julius Tsamba a zaka 20 kukakhala kundende kwa zaka 14 chifukwa chogwilira msungwana wa zaka 12
Bwalo la milandu la Fesiti Giledi majesitileti ku Mchinji lalamula a Juliyasi Tsamba a zaka Twente kukakhala kundende kwa zaka fotini chifukwa chogwilira msungwana wa zaka Thwelofu
female
A Tsamba adawambanga pa 18 December, 2023, mayi ake a msungwanayu atamupeza bamboyu akuzikakamiza pa thupi la mwanayo
A Tsamba adawamanga pa eyitini Disemba, Twente twente fili, mayi ake a msungwanayu atamupeza bamboyu akuzikakamiza pa thupi la mwana-yo
female
Mayi a msungwanayu adali atalandila uthenga ali ku msika kuti munthu wina wa chilendo watenga mwana wawo ndi kumulowetsa m'nyumba
Mayi a msungwanayu adali atalandila uthenga ali ku msika kuti munthu wina wa chilendo watenga mwana wawo ndi kumulowetsa m'nyumba.
female
A Tsamba adawukana mlanduwu ndipo izi zinachititsa bwaloli kupeza mboni zinayi kuphatikizapo umboni wa zotsatira zaku chipatala ndipo pamapeto pake adamupeza wolakwa
A Tsamba adawukana mlanduwu ndipo izi zinachititsa bwaloli kupeza mboni zinayi kuphatikizapo umboni wa zotsatira zaku chipatala ndipo pamapeto pake adamupeza wolakwa
female
Woweruza milandu a Yohane Nkhata analamula bamboyu kukhala kundende Kwa zaka 14 ndi kukagwira ntchito yakalavula gaga chifukwa chosemphana ndi gawo 139 la malamulo
Woweruza milandu a Yohane Nkhata analamula bamboyu kukakhala kundende Kwa zaka fotini ndi kukagwira ntchito yakalavula gaga chifukwa chosemphana ndi gawo wani fete naini la malamulo
female
Phungu wa chipani cha Democratic Progressive Party wa dera la kumpoto m'boma la Mangochi, Benedicto Chambo, wati agwira ntchito yothandiza kuti mu 2025, President Lazarus Chakwera apitirize kulamula dziko lino
Phungu wa chipani cha demokilatiki pulogilesivi pate wa dera la kumpoto m'boma la Mangochi, Benedikito Chambo, wati agwira ntchito yothandiza kuti mu twente twente faifi, pulezidenti lazalasi Chakwera apitirize kulamula dziko lino
female
Phunguyu lero adali nawo pa msonkhano wa chipani cha Malawi Congress umene unachitikira pa bwalo la masewero la Dzenza, ku Area 25 m'boma la Lilongwe
Phunguyu lero adali nawo pa msonkhano wa chipani cha Malawi kongilesi umene unachitikira pa bwalo la masewero la Dzenza, ku eliya twente faifi m'boma la Lilongwe
female
Mlendo wolemekezeka pa msonkhanowu adali nduna ya maboma aang'ono a Richard Chimwendo Banda yemwenso ndi mkulu wa achinyamata mu chipani cha MCP
Mlendo wolemekezeka pa msonkhanowu adali nduna ya maboma aang'ono a Litchadi Chimwendo Banda yemwenso ndi mkulu wa achinyamata mu chipani cha Emu sipi
female
Amayi ena amene akuti ndi otsatira chipani cha DPP ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre, Ang'amba nsalu ya chipanichi, akuti posonyeza kusakondwa ndi kuchotsedwa kwa a Kondwani Nankhumwa m'chipanichi
Amayi ena amene akuti ndi otsatira chipani cha Di Pipii ku Ndirande mu mzinda wa Bulantaya, Ang'amba nsalu ya chipanichi, akuti posonyeza kusakondwa ndi kuchotsedwa kwa a Kondwani Nankhumwa m'chipanichi
female
Mwana wa zaka 7 Yamikani Witness wa m'mudzi wa Makangata kudera la mfumu yaikulu Nkoola ku Machinga wamwalira, pomwe anthu ena asanu anathamangira nawo ku chipatala, atadya nsima ya deya
Mwana wa zaka seveni Yamikani Witinesi wa m'mudzi wa Makangata kudera la mfumu yaikulu Nkoola ku Machinga wamwalira, pomwe anthu ena asanu anathamangira nawo ku chipatala, atadya nsima ya deya
female
Wapampando wa komiti ya chitukuko ya kuderali a Idrisa Mmeta wauza Times 360 Malawi kuti anthu onsewa, omwe ndi a banja limodzi, adayamba kusanza komanso kutsegula m'mimba kosalekeza
Wapampando wa komiti ya chitukuko ya kuderali a Idrisa Mmeta wauza Taimusi fili sikisite Malawi kuti anthu onsewa, omwe ndi a banja limodzi, adayamba kusanza komanso kutsegula m'mimba kosalekeza
female
atangotha kudya nsimayi ndipo anthu akufuna kwabwino ndi omwe anathamangira nawo ku chipatala, koma mwana wamng'onoyo wamwalira
atangotha kudya nsimayi ndipo anthu akufuna kwabwino ndi omwe anathamangira nawo ku chipatala, koma mwana wamng'onoyo wamwalira
female
Ofalitsa nkhani za umoyo pa chipatala chachikulu cha m'boma la Machinga a Wongani Nyirenda watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati zotsatira za chipatala zasonyeza kuti anthuwa adadya chokudya chomwe akuchiganizira kuti chidali cha poizoni

Malingana ndi a Nyirenda, mayi pamodzi ndi mwana wina mmodzi akupezako bwino pomwe akulandira thandizo la mankhwala pa chipatalachi
Malingana ndi a Nyirenda, mayi pamodzi ndi mwana wina mmodzi akupezako bwino pomwe akulandira thandizo la mankhwala pa chipatalachi
female
Mapemphero alephereka pa mpingo wa Namiyango CCAP ku Bangwe mu mzinda wa Blantyre pamene akhristu akukana kuti mbusa wawo a Victor Chisuse awasamutse pa mpingowu
Mapemphero alephereka pa mpingo wa Namiyango sisepi ku Bangwe mu mzinda wa Bulantaya pamene akhristu akukana kuti mbusa wawo a Vikita Chisuse awasamutse pa mpingowu
female
Akhristuwa ati amvetsedwa kuti sinodi ya Blantyre ili ndi malingaliro ofuna kusamutsa mbusayu koma iwo sakugwirizana ndi ganizoli
Akhristuwa ati amvetsedwa kuti sinodi ya Bulantaya ili ndi malingaliro ofuna kusamutsa mbusayu koma iwo sakugwirizana ndi ganizoli
female
ponena kuti mbusayu wangotha miyezi isanu ndi inayi yokha pa mpingowu
ponena kuti mbusayu wangotha miyezi isanu ndi inayi yokha pa mpingowu
female
Anthuwa, uku atanyamula mapepala amene adalembedwa mawu osutsana ndi ganizo lofuna kusamutsa mbusa Chisuse, adaimba nyimbo zoonetsa mkwiyo wawo
Anthuwa, uku atanyamula mapepala amene adalembedwa mawu osutsana ndi ganizo lofuna kusamutsa mbusa Chisuse, adaimba nyimbo zoonetsa mkwiyo wawo
female
Akhristuwa apereka kalata ya madandulo kwa mlembi pa mpingowu a Gilbert Kachamba yoti ayipereke ku sinodiyi, Sinodi ya Blantyre sinayankhulepo pa nkhaniyi
Akhristuwa apereka kalata ya madandulo kwa mlembi pa mpingowu a Gilibati Kachamba yoti ayipereke ku sinodiyi, Sinodi ya Bulantaya sinayankhulepo pa nkhaniyi
female
Mmodzi wa akonzi a 'School Days' Kendall Kamwendo wauza anthu ku Amaryllis Hotel mu mzinda wa Blantyre kuti iwo atulutsanso kanema wina wokoma kuposa School Days mu December
Mmodzi wa akonzi a 'sukulu deizi’ Kendo Kamwendo wauza anthu ku Amarezi Hotelo mu mzinda wa Bulantaya kuti iwo atulutsanso kanema wina wokoma kuposa sukulu deizi mu Disemba
female
Kendall wauzanso anthu kuti akufuna thandizo kuchokera kwa Amalawi kuti kenamayu amuonetse m'malo ambiri m'dziko muno
Kendo wauzanso anthu kuti akufuna thandizo kuchokera kwa Amalawi kuti kenamayu amuonetse m'malo ambiri m'dziko muno
female
Kendall watinso ayamba kuyendera sukulu zosiyasiyana komwe aluso omwe ali mu kanemayu akuphunzitsa anthu za kuipa Kochitilana za mtopola
Kendo watinso ayamba kuyendera sukulu zosiyasiyana komwe aluso omwe ali mu kanemayu akuphunzitsa anthu za kuipa Kochitilana za mtopola
female
Anthu awonera kanema ya School Days ku Amaryllis Hotel mu mzinda wa Blantyre ndipo mu kanema wotsatirayu, Kendall Kamwendo akuwawonetsa ena mwa aluso amene adatenga nawo gawo
Anthu awonera kanema ya Sukulu deizi ku Amarezi Hotelo mu mzinda wa Bulantaya ndipo mu kanema wotsatirayu, Kendo Kamwendo akuwawonetsa ena mwa aluso amene adatenga nawo gawo
female
Bwalo la milandu m'boma la Nkhotakota lalamula mnyamata wa zaka 34 kuti akakhale kundende kwa zaka ziwiri kamba konamiza anthu kuti ndi msilikali wa MDF
Bwalo la milandu m'boma la Nkhotakota lalamula mnyamata wa zaka fete folo kuti akakhale kundende kwa zaka ziwiri kamba konamiza anthu kuti ndi msilikali wa Emu Di Efu
female
Wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Nkhotakota a Chisomo Chuma wauza Times 360 Malawi lero kuti, wopalamulayu ndi a Steve Manda
Wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Nkhotakota a Chisomo Chuma wauza Taimusi fili sikisite Malawi lero kuti, wopalamulayu ndi a Sitivi Manda
female
a m'mudzi wa Muwanga m'dera la mfumu yayikulu Mwamlowe m'boma la Rumphi. Bwaloli lidamva kuti pa 18 mwezi uno
m'mudzi wa Muwanga m'dera la mfumu yayikulu Mwamlowe m'boma la Rumphi. Bwaloli lidamva kuti pa eyitini mwezi uno
female
wopalamulayu adakakamiza anthu pa Nkhotakota boma kuti amupatse ndalama komanso mowa ponena kuti mphamvu za ntchito yake zimamulola kuti atero
wopalamulayu adakakamiza anthu pa Nkhotakota boma kuti amupatse ndalama komanso mowa ponena kuti mphamvu za ntchito yake zimamulola kuti atero
female
Wopalamulayu adamangidwa anthu akufuna kwabwino atatsina khutu apolisi za nkhaniyi
Wopalamulayu adamangidwa anthu akufuna kwabwino atatsina khutu apolisi za nkhaniyi
female
Oweruza milandu pa bwaloli a Felix Phaiya adalamula mkuluyu, yemwe adauvomera mlanduwu, kuti akakhale kundende kwa zaka ziwiri
Oweruza milandu pa bwaloli a Felikisi Phaiya adalamula mkuluyu, yemwe adauvomera mlanduwu, kuti akakhale kundende kwa zaka ziwiri
female
Phungu wa kunyumba ya malamulo wa dera la kummwera kwa boma la Balaka, a Ireen Mambala walimbikitsa anthu a m'bomali kuti abzale mitengo ya zipatso pomwe nyengo yobzala mitengo ili mkati m'dziko muno
Phungu wa kunyumba ya malamulo wa dera la kummwera kwa boma la Balaka, a ailini Mambala walimbikitsa anthu a m'bomali kuti abzale mitengo ya zipatso pomwe nyengo yobzala mitengo ili mkati m'dziko muno
female
A Mambala anena izi lero pomwe anatsogolera anthu pa ntchito yobzala mitengo 100 ya mango m'dera la mfumu yaikulu Phalula m'bomali
A Mambala anena izi lero pomwe anatsogolera anthu pa ntchito yobzala mitengo wani handiledi ya mango m'dera la mfumu yaikulu Phalula m'bomali
female
Iwo ati mitengo ya zipatso iri ndi kuthekera kothandizira ku kadyedwe kabwino komanso kumbali ya chuma ponena kuti anthuwa akhoza kumapeza ndalama akamagulitsa zipatso zochokera m'mitengoyi
Iwo ati mitengo ya zipatso iri ndi kuthekera kothandizira ku kadyedwe kabwino komanso kumbali ya chuma ponena kuti anthuwa akhoza kumapeza ndalama akamagulitsa zipatso zochokera m'mitengoyi
female
Gulupu Ntchona ya m'derali yayamikira phunguyu popereka mitengoyi komanso kuthandizira pa ntchito yobzalayi ponena kuti izi zipititsa patsogolo chitukuko cha derali
Gulupu Ntchona ya m'derali yayamikira phunguyu popereka mitengoyi komanso kuthandizira pa ntchito yobzalayi ponena kuti izi zipititsa patsogolo chitukuko cha derali
female
Phungu wakunyumba ya malamulo wadera la pakati m'boma la Salima Gerald Kapiseni phiri wapepha anthu kuti asiye mchitidwe wochitira chipongwe anthu oyendetsa kabaza wa njinga zakapalasa m'bomali
phungu wakunyumba ya malamulo wadera la pakati m'boma la Salima Jeladi Kapiseni phiri wapepha anthu kuti asiye mchitidwe wochitira chipongwe anthu oyendetsa kabaza wa njinga zakapalasa m'bomali
female
A Phiri ayakhula izi pamapeto pa mpikisano wa a njinga zakapalasa omwe anakonza lero Loweluka mmawa
A Phiri ayakhula izi pamapeto pa mpikisano wa a njinga zakapalasa omwe anakonza lero Loweluka mmawa
female
Anthu omwe amachita kabaza wa njinga zakapalasa ndi anthu ofunika kwambiri ndipo onse ochitira chipongwe anthu awawa akuyenera kumagwidwa, anatero a Phiri
Anthu omwe amachita kabaza wa njinga zakapalasa ndi anthu ofunika kwambiri ndipo onse ochitira chipongwe anthu awawa akuyenera kumagwidwa, anatero a Phiri
female
Ndipo yemwe wapatsa mphoto ya njinga yatsopano atapambana pa mpikisanowu, Alfred Banda, wayamikira phunguyu kaamba ka mpikisanowu
Ndipo yemwe wapatsa mphoto ya njinga yatsopano atapambana pa mpikisanowu, Alafuledi Banda, wayamikira phunguyu kaamba ka mpikisanowu
female
ponena kuti njingayi ikuza malonda ake a kabaza kaamba koti alemba ntchito munthu wina ndi kumupatsa njingayo kuti aziyendera pansewu
ponena kuti njingayi ikuza malonda ake a kabaza kaamba koti alemba ntchito munthu wina ndi kumupatsa njingayo kuti aziyendera pansewu
female
Akabanza okwana 270 ndi omwe anayamba nawo mpikisanowo ndipo opambana alandira njinga Zakabaza pomwe ena alandira mateyala komanso chubu
Akabanza okwana thuhandede sevente ndi omwe anayamba nawo mpikisanowo ndipo opambana alandira njinga Zakabaza pomwe ena alandira mateyala komanso chubu
female
Apolisi m'boma la Ntchisi amanga a Vincent Mwale, a zaka 26, ochokera m'mudzi wa Magana mfumu yayikulu Vuso Jere ya m'bomali kaamba kowaganizira kuti amagona ndi mbuzi
Apolisi m'boma la Ntchisi amanga a Vinisenti Mwale, a zaka twente sikisi, ochokera m'mudzi wa Magana mfumu yayikulu Vuso Jere ya m'bomali kaamba kowaganizira kuti amagona ndi mbuzi
female
Mneneri wa polisi ya Ntchisi a Salomy Zgambo wauza Times 360 Malawi kuti nkhaniyi inachitika pa 25 January
Mneneri wa polisi ya Ntchisi a Salome Zyambo wauza Taimusi fili sikisite Malawi kuti nkhaniyi inachitika pa twente faifi Januwale
female
2024 m'mudzi wa Galang'ande m'bomali, nthawi ya 12 koloko masana
Twente twente folo m'mudzi wa Galang'ande m'bomali, nthawi ya twelofu koloko masana
female
A Zgambo ati mwini mbuzi anadabwa pa tsikuli pamene anamva phokoso lomwe limachokera komwe adamanga mbuzi yake, ndipo atathamangira konko kuti akaone, anapeza woganiziridwayu akugona mbuzi yakeyo
A Zyambo ati mwini mbuzi anadabwa pa tsikuli pamene anamva phokoso lomwe limachokera komwe adamanga mbuzi yake, ndipo atathamangira konko kuti akaone, anapeza woganiziridwayu akugona mbuzi yakeyo
female
A Mwale atazindikira kuti mwini mbuziyo wamuona anathawa pamalopo koma anthu a m'mudzimu anagwirizana kumusaka ndi kumugwira
A Mwale atazindikira kuti mwini mbuziyo wamuona anathawa pamalopo koma anthu a m'mudzimu anagwirizana kumusaka ndi kumugwira
female
Anthu okhala kuderali auza aplisi kuti aka sikoyamba kumupeza woganiziridwayu akugonana ndi mbuzi
Anthu okhala kuderali auza aplisi kuti aka sikoyamba kumupeza woganiziridwayu akugonana ndi mbuzi
female
Nyumba zokwana 55 komanso misewu itatu zaonongeka ndi mvula kuyambira pa 1 January kufikira lero ku Likoma, malingana ndi akulukakulu oona za ngozi zogwa mwadzidzidzi m'bomalo
Nyumba zokwana fifite faifi komanso misewu itatu zaonongeka ndi mvula kuyambira pa wani januwale kufikira lero ku Likoma, malingana ndi akulukakulu oona za ngozi zogwa mwadzidzidzi m'bomalo
female
Ngozizi zachitikika m'midzi 11 m'madera a mafumu akuluakulu Nkhumpha komanso Kabuthu
Ngozizi zachitikika m'midzi leveni m'madera a mafumu akuluakulu Nkhumpha komanso Kabuthu
female
Mwa zina, zinthu monga malata, ufa ndi zakudya zina komanso zofunda zaonongeka, koma palibe munthu yemwe wavulala ndi ngozizi
Mwa zina, zinthu monga malata, ufa ndi zakudya zina komanso zofunda zaonongeka, koma palibe munthu yemwe wavulala ndi ngozizi
female
Mkulu woona za ngozi zogwa mwadzidzidzi m'bomali a Tamanda Nkhoma wati boma, kudzera mu nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi m'dziko muno, likuchita chothekera pofuna kuthandiza anthuwa
Mkulu woona za ngozi zogwa mwadzidzidzi m'bomali a Tamanda Nkhoma wati boma, kudzera mu nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi m'dziko muno, likuchita chothekera pofuna kuthandiza anthuwa
female
Nthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzizi m'boma la Dedza, yati ifikira anthu okwana 44,000 ndi thandizo la chakudya chomwe boma likugawa kwa maanja omwe akusowa chakudya m'dziko muno
Nthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzizi m'boma la Dedza, yati ifikira anthu okwana fote folo sauzande ndi thandizo la chakudya chomwe boma likugawa kwa maanja omwe akusowa chakudya m'dziko muno
female
Bwanamkubwa wa boma la Dedza a Thomas Chigwenembe, polankhula pokhazikitsa ndondomekoyi
Bwanamkubwa wa boma la Dedza a Thomasi Chigwenembe, polankhula pokhazikitsa ndondomekoyi
female
lero m'dera la mfumu yayikulu Kamenyagwaza, ati maanja okhudzidwa alandira chimanga kwa miyezi iwiri ya January ndi February
lero m'dera la mfumu yayikulu Kamenyagwaza, ati maanja okhudzidwa alandira chimanga kwa miyezi iwiri ya Januwale ndi Febuluwale
female
Iwo ati boma la Dedza lakhudzidwa ndi njala kaamba ka mvula yochuluka yomwe inagwa m'mmadera ena ndipo inakhudza zokolola, komanso ng'amba
Iwo ati boma la Dedza lakhudzidwa ndi njala kaamba ka mvula yochuluka yomwe inagwa m'mmadera ena ndipo inakhudza zokolola, komanso ng'amba
female
M'mawu ake, Mfumu Yayikulu Kamenyagwaza, yati pomwe maanja a m'dera lake okwana 604 alandira thandizo la chakudyachi
M'mawu ake, Mfumu Yayikulu Kamenyagwaza, yati pomwe maanja a m'dera lake okwana sikisi handede andi folo alandira thandizo la chakudyachi
female
inamema anthu omwe alandira thandizoli kuti asagulitse kapena kulola kuti anthu ena awalande
inamema anthu omwe alandira thandizoli kuti asagulitse kapena kulola kuti anthu ena awalande
female
M'modzi wa anthu omwe alandira chimangachi, Lugaliyo M'mvumbi anati akuvutika kwambiri, moti pena akumagonera nkhwani
M'modzi wa anthu omwe alandira chimangachi, Lugaliyo M'mvumbi anati akuvutika kwambiri, moti pena akumagonera nkhwani
female
Nduna yoona za Mphamvu za magetsi m'dziko muno a Ibrahim Matola yati unduna wawo uwonesetsa kuti mnyamata yemwe anapanga magetsi a mpweya ndi mphepo
Nduna yoona za Mphamvu za magetsi m'dziko muno a Ibulahimu Matola yati unduna wawo uwonesetsa kuti mnyamata yemwe anapanga magetsi a mpweya ndi mphepo
female
m'boma la Dowa wathandizidwa kuti luso lake lipindule mdziko muno
m'boma la Dowa wathandizidwa kuti luso lake lipindule mdziko muno
female
A Matola alankhula izi lero pomwe anakayendera mnyamatayu, Enerst Andrew wa zaka 19, wochokera m'mudzi wa Chinguwo, mfumu yayikulu Chiwere m'boma la Dowa
A Matola alankhula izi lero pomwe anakayendera mnyamatayu, Enesiti Andulu wa zaka Naintini, wochokera m'mudzi wa Chinguwo, mfumu yayikulu Chiwere m'boma la Dowa
female
Iwo ati sangamukakamize Andrew kukayambanso sukulu koma boma ndi magulu osiyanasiyana achita zothekera kumuthandiza ndi zipangizo zosiyanasiyana ndi cholinga chofuna kukwaniritsa luso lake
Iwo ati sangamukakamize Andulu kukayambanso sukulu koma boma ndi magulu osiyanasiyana achita zothekera kumuthandiza ndi zipangizo zosiyanasiyana ndi cholinga chofuna kukwaniritsa luso lake
female
Mkulu woona za chisamaliro cha anthu ku khonsolo ya M'mbelwa, a Benard Nangwale, wapempha makolo omwe anapita ku South Africa kuti azionesetsa kuti akupereka thandizo loyenera kwa ana omwe awasiya
Mkulu woona za chisamaliro cha anthu ku khonsolo ya M'mbelwa, a Benadi Nangwale, wapempha makolo omwe anapita ku Saufi afilika kuti azionesetsa kuti akupereka thandizo loyenera kwa ana omwe awasiya
female
A Nangwale anati kusapereka thandizo lokwanira kwa ana, omwe ambiri amawasiya kwa agogo awo, kukulozera ukwati wa ana omwe akumalowa m'banja pofuna thandizo
A Nangwale anati kusapereka thandizo lokwanira kwa ana, omwe ambiri amawasiya kwa agogo awo, kukulozera ukwati wa ana omwe akumalowa m'banja pofuna thandizo
female
Iwo amayankhula pa mkumano omwe anali nawo akuluakulu aku khonsolo ya Zomba, ofuna kukambirana m'mene angathetsere ukwati wa ana
Iwo amayankhula pa mkumano omwe anali nawo akuluakulu aku khonsolo ya Zomba, ofuna kukambirana m'mene angathetsere ukwati wa ana
female
Zadziwika kuti mbali ya kummwera kwa boma la Mzimba kunachitika ukwati wa ana okwana 368 m'chaka cha 2023
Zadziwika kuti mbali ya kummwera kwa boma la Mzimba kunachitika ukwati wa ana okwana fili handede andi sikisite eyiti m'chaka cha twente twente fili
female
Mfumu yaikulu Chambwe, m'boma la Kasungu yapempha boma kuti lichite machawi pobweretsa chimanga ku msika wa Admarc ku dera lawo
Mfumu yaikulu Chambwe, m'boma la Kasungu yapempha boma kuti lichite machawi pobweretsa chimanga ku msika wa Adimaki ku dera lawo
female
Mfumuyi yayankhula izi pa mwambo umene bungwe la boma lobwereketsa ngongole la National Economic Empowerment Fund (NEEF), limapereka mjigo
Mfumuyi yayankhula izi pa mwambo umene bungwe la boma lobwereketsa ngongole la Neshono Ikonomiki Impawamenti fandi (nifi), limapereka mjigo
female
Poyankhapo, phungu wa ku nyumba ya malamulo wa kummwera cha kumvuma m'bomali, yemweso ndi nduna yoona za umoyo a Khumbize Kandodo Chiponda
Poyankhapo, phungu wa ku nyumba ya malamulo wa kummwera cha kumvuma m'bomali, yemweso ndi nduna yoona za umoyo a Khumbize Kandodo Chiponda
female