audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
ndipo anaba njinga za moto zokwana 46 komanso ma belo a kaunjika okwana 84, zonse za ndalama yokwana K155 million
ndipo anaba njinga za moto zokwana fote sikisi komanso ma belo a kaunjika okwana eite folo, zonse za ndalama yokwana wani handedi andi fifite faifi miliyoni kwacha
Female
A Chigalu ati anthuwa ndi Davie Livalo a zaka 34, Paul Mkambeni 36, Aaron Jere 29, Chifundo Makele 2
A Chigalu ati anthuwa ndi Devi Livalo a zaka fete folo, Po Mkambeni fete sikisi, Aloni Jere twente naini, Chifundo Makele twente naini
Female
Keni Mbewe twente naini, Tamandani Matope twente seveni, Chifuniro Makele twente naini ndi Chifundo Phiri wa zaka twente faifi
Keni Mbewe twente naini, Tamandani Matope twente seveni, Chifuniro Makele twente naini ndi Chifundo Phiri wa zaka twente faifi
Female
Malinga ndi a Chigalu, mlonda wa pamalo osungira katunduyo ndi yemwe adathandizira kubako ndipo m'mwezi wa December
Malinga ndi a Chigalu, mlonda wa pamalo osungira katunduyo ndi yemwe adathandizira kubako ndipo m'mwezi wa Disemba
Female
apolisi adamanga mlondayo ndi kupeza ma belo a kaunjika 30 ndi njinga yamoto imodzi ndipo mlondayo adauza apolisi
apolisi adamanga mlondayo ndi kupeza ma belo a kaunjika fete ndi njinga yamoto imodzi ndipo mlondayo adauza apolisi
Female
kuti anzake omwe anaba nawo akugwiritsa ntchito njinga zinazo ngati Kabaza ku Area 25 ndi Area 50
kuti anzake omwe anaba nawo akugwiritsa ntchito njinga zinazo ngati Kabaza ku Eliya twente faifi ndi Eliya fifite
Female
Apa ndi pomwe apolisi amanga anthu 7-wa, mlondayo atakawaloza ndipo pakadali pano apolisi akusaka yemwe adatsogolera chiwembucho yemwe akuti amadziwika ndi dzina loti Nana
Apa ndi pomwe apolisi amanga anthu seveniwa, mlondayo atakawaloza ndipo pakadali pano apolisi akusaka yemwe adatsogolera chiwembucho yemwe akuti amadziwika ndi dzina loti Nana
Female
Prophet David Mbewe watsutsa zina mwa mphekesera zomwe zimamveka ku Zomba ku m'mawaku kuti iwo adagwiritsa ntchito ma ID a anthu ena polembetsa chipani chawo
Prophet David Mbewe watsutsa zina mwa mphekesera zomwe zimamveka ku Zomba ku m'mawaku kuti iwo adagwiritsa ntchito ma Ayidi a anthu ena polembetsa chipani chawo
Female
Ku m'mawaku gulu la amayi ena lidasonkhana ku Annie's Lodge ku Zomba, komwe akuti m'mbuyomu adaperekako maina awo, zithunzi komanso adajambula zithunzi za ziphaso zawo za unzika
Ku m'mawaku gulu la amayi ena lidasonkhana ku Anezi Loji ku Zomba, komwe akuti m'mbuyomu adaperekako maina awo, zithunzi komanso adajambula zithunzi za ziphaso zawo za unzika
Female
Iwo akukaikira kuti a Annie Fletcher adagwiritsa ntchito izi kuti atolere ma ID a anthuwa polembetsera chipani chatsopano cha a Mbewe
Iwo akukaikira kuti a Ani Fuletcha adagwiritsa ntchito izi kuti atolere ma ayidi a anthuwa polembetsera chipani chatsopano cha a Mbewe
Female
M'modzi wa amayiwa wati potenga zithunzi za nkhope ndi ma ID awo, ankawauza kuti awapatsa ngongole, koma izi sizikuchitika
M'modzi wa amayiwa wati potenga zithunzi za nkhope ndi ma ayidi awo, ankawauza kuti awapatsa ngongole, koma izi sizikuchitika
Female
Koma a Mbewe ati chipani chawo chilibe munthu wa dzina longa limenelo Ndipo a Fletcher anati sangayankhulepo kanthu kaamba koti adali mu mkumano wina
Koma a Mbewe ati chipani chawo chilibe munthu wa dzina longa limenelo Ndipo a Fuletcha anati sangayankhulepo kanthu kaamba koti adali mu mkumano wina
Female
Apolisi ku Machinga amanga abambo atatu powaganizira kuti anatema anthu atatu komanso kuzula mpunga m'munda
Apolisi ku Machinga amanga abambo atatu powaganizira kuti anatema anthu atatu komanso kuzula mpunga m'munda
Female
pa chipolowe chomwe chidabuka pakati pa anthu a midzi ya Lipuluma ndi Misi pomwe amakanganirana minda ya mpunga
pa chipolowe chomwe chidabuka pakati pa anthu a midzi ya Lipuluma ndi Misi pomwe amakanganirana minda ya mpunga
Female
Wofalitsa nkhani za polisi ya Machinga a Western Kansire wati atatuwa ndi a White Maononga azaka 42, a Austin Major azaka 37
Wofalitsa nkhani za polisi ya Machinga a Wesiteni Kansire wati atatuwa ndi a Waiti Maononga azaka fote thu, a Ositini Meja azaka sate seveni
Female
komanso a Freston Major azaka 31 a m'mudzi wa Misi kudera la mfumu yaikulu Mchinguza m'bomali
komanso a fulesitoni meja azaka fete wani a m'mudzi wa Misi kudera la mfumu yaikulu Mchinguza m'bomali
Female
A Kansire ati ena mwa ovulalawa akupezako bwino pomwe adalandira thandizo la chipatala koma mmodzi mwa iwo ali mu ululu waukulu pa chipatala cha Machinga
A Kansire ati ena mwa ovulalawa akupezako bwino pomwe adalandira thandizo la chipatala koma mmodzi mwa iwo ali mu ululu waukulu pa chipatala cha Machinga
Female
Pakadali pano polisi ya m'bomali yapempha anthu kuti adzitha kukambirana mwa mtendere ngati asemphana pa nkhani za malo kapena kupempha uphungu kwa mafumu kapena adindo ena
Pakadali pano polisi ya m'bomali yapempha anthu kuti adzitha kukambirana mwa mtendere ngati asemphana pa nkhani za malo kapena kupempha uphungu kwa mafumu kapena adindo ena
Female
Anthu ena amene amakhala nyumba za Malawi Housing Corporation ku Area 6 mu mzinda wa Lilongwe adandaula ndi ganizo la bungweri
Anthu ena amene amakhala nyumba za Malawi Hauzing’I kopaleshoni ku eliya sikisi mu mzinda wa Lilongwe adandaula ndi ganizo la bungweri
Female
limene likufuna kuti anthuwa achoke pofika pa 31 mwezi uno Kudzera mu kalata imene bungweri lidalemba pa 28 December chaka chatha ndikusainiridwa ndi mkulu wa bungweri
limene likufuna kuti anthuwa achoke pofika pa satefete wani mwezi uno Kudzera mu kalata imene bungweri lidalemba pa twente eiti Disemba chaka chatha ndikusainiridwa ndi mkulu wa bungweri
Female
m'chigawo cha pakati a Ndifanji Kabango, bungweri lidathetsa mgwirizano wake ndi anthuwa ndikuwapatsa mwezi umodzi kuti asamuke
m'chigawo cha pakati a Ndifanji Kabango, bungweri lidathetsa mgwirizano wake ndi anthuwa ndikuwapatsa mwezi umodzi kuti asamuke
Female
Koma pamene pangotsala masiku asanu ndi anayi, ena mwa anthu amene amakhala mnyumbazi a Eunice Sauli komanso a Chimwemwe Musa ati pofika pano alibe koti angapite kaamba koti, mwa zina, nyumba zikusowa
Koma pamene pangotsala masiku asanu ndi anayi, ena mwa anthu amene amakhala mnyumbazi a Yunisi Sauli komanso a Chimwemwe Musa ati pofika pano alibe koti angapite kaamba koti, mwa zina, nyumba zikusowa
Female
Anthuwa ati bungweri likadakhala kuti lidawapatsa nyumba zina kuti asamukireko, akadasamuka nthawiyi isadathe
Anthuwa ati bungweri likadakhala kuti lidawapatsa nyumba zina kuti asamukireko, akadasamuka nthawiyi isadathe
Female
Malinga ndi anthuwa, ndizodandaulitsa kuti bungweri labweretsa kale anthu ogwira ntchito ake kumalowa ngakhale kuti nthawi imene anthu amene akukhala mnyumbazi adapatsidwa, sidathe
Malinga ndi anthuwa, ndizodandaulitsa kuti bungweri labweretsa kale anthu ogwira ntchito ake kumalowa ngakhale kuti nthawi imene anthu amene akukhala mnyumbazi adapatsidwa, sidathe
Female
Wofalitsa nkhani za bungweri a Enerstina Lunguzi anapempha nthawi kuti ayankhulepo pa nkhaniyi Zikumveka kuti anthuwa akatuluka, nyumbazi zisandutsidwa likulu la bungweri
Wofalitsa nkhani za bungweri a Enesitina Lunguzi anapempha nthawi kuti ayankhulepo pa nkhaniyi Zikumveka kuti anthuwa akatuluka, nyumbazi zisandutsidwa likulu la bungweri
Female
Pakadali pano, nyumba zisanu pa nyumba 18 za pa malowa zasamukidwa kale
Pakadali pano, nyumba zisanu pa nyumba eitini za pa malowa zasamukidwa kale
Female
A Tiyamike Nyirenda, omwe ndi a zaka 42 ndipo amachokera ku dera la Chiwavi mu mzinda wa Mzuzu apata ndalama zokwana K500,000
A Tiyamike Nyirenda, omwe ndi a zaka fote thu ndipo amachokera ku dera la Chiwavi mu mzinda wa Mzuzu apata ndalama zokwana Fafi handede sauzande kwacha
Female
mu mpikisano wa Shake-Shake Bonanza omwe akuchitsa ndi a kampani ya Chibuku
mu mpikisano wa Sheki-Sheki Bonanza omwe akuchitsa ndi a kampani ya Chibuku
Female
A Nyirenda ati iwo anangogula mapaketi awiri a Chibuku ndipo anali odabwa atapeza kanthu kolembedwa mphoto ya ndalamazi kamba koti samkadziwa za mpikisanowu
A Nyirenda ati iwo anangogula mapaketi awiri a Chibuku ndipo anali odabwa atapeza kanthu kolembedwa mphoto ya ndalamazi kamba koti samkadziwa za mpikisanowu
Female
Iwo, omwe alandira ndalama zawo lero ku maofesi a Chibuku mu mzinda wa Mzuzu, akuti alowetsa ndalamazi mu ulimu wa chimanga
Iwo, omwe alandira ndalama zawo lero ku maofesi a Chibuku mu mzinda wa Mzuzu, akuti alowetsa ndalamazi mu ulimu wa chimanga
Female
ndipo malingaliro awo n'kudzagulitsanso chimangachi ku kampani yomweyi ya Chibuku
ndipo malingaliro awo n'kudzagulitsanso chimangachi ku kampani yomweyi ya Chibuku
Female
M'modzi wa akuluakulu a kampani ya Chibuku kuchigawo chakumpoto a Patrick Dzanja wati anthu ayembekezere zakumwa za tsopano kuchokera ku kampaniyi
M'modzi wa akuluakulu a kampani ya Chibuku kuchigawo chakumpoto a Patiliki Dzanja wati anthu ayembekezere zakumwa za tsopano kuchokera ku kampaniyi
Female
Bwalo la milandu ku Jenda m'boma la Mzimba lagamula kuti galimoto ina, yomwe inagwiritsidwa ntchito kuti inyamulire nzika 98
Bwalo la milandu ku Jenda m'boma la Mzimba lagamula kuti galimoto ina, yomwe inagwiritsidwa ntchito kuti inyamulire nzika nainte eiti
Female
za m'dziko la Ethiopia zomwe zinalowa m'dziko opanda chilorezo, iperekedwe ku nthambi ya apolisi
za m'dziko la Efiyopiya zomwe zinalowa m'dziko opanda chilorezo, iperekedwe ku nthambi ya apolisi
Female
Galimotoyi inanyamula nzika za m'dziko la Ethiopia ndipo imalowera ku Lilongwe koma oyendetsa galimotoyi ndi womuthandizira wake adathawa ataona apolisi
Galimotoyi inanyamula nzika za m'dziko la Efiyopiya ndipo imalowera ku Lilongwe koma oyendetsa galimotoyi ndi womuthandizira wake adathawa ataona apolisi
Female
Apa n'kuti galimotoyi ikadali kuyenda ndipo idaomba galimoto ina Nzika 98 zonse zavomera mlandu wolowa m'dziko muno opanda chilorezo
Apa n'kuti galimotoyi ikadali kuyenda ndipo idaomba galimoto ina Nzika nainte eiti zonse zavomera mlandu wolowa m'dziko muno opanda chilorezo
Female
ndipo azigamula kuti zikakhale ku ndende kwa miyezi itatu kenako zizatumizidwenso ku dziko lawo
ndipo azigamula kuti zikakhale ku ndende kwa miyezi itatu kenako zizatumizidwenso ku dziko lawo
Female
Galimoto ya mtundu wa lorry yagubuduzika pa msewu wa Usisya m'boma la Nkhata Bay. Msewu-wu ndi woonongeka ndipo kukagwa mvula, mbali ina imatelera kuchititsa galimoto zina kulephera kuyenda
Galimoto ya mtundu wa lore yagubuduzika pa msewu wa Usisya m'boma la Nkhata Bay. Msewu-wu ndi woonongeka ndipo kukagwa mvula, mbali ina imatelera kuchititsa galimoto zina kulephera kuyenda
Female
A polisi sanayankhulapo pa ngoziyi ndipo pakadali pano, sizikudziwika kuti anthu akhudzidwa motani pa ngoziyi
A polisi sanayankhulapo pa ngoziyi ndipo pakadali pano, sizikudziwika kuti anthu akhudzidwa motani pa ngoziyi
Female
Mtsikana wa zaka zisanu ndi chimodzi , Mphatso Zephania, wamwalira atagundidwa ndi galimoto pa 19 January 2024
Mtsikana wa zaka zisanu ndi chimodzi , Mphatso Zefaniya, wamwalira atagundidwa ndi galimoto pa naintini Januwale twente twente folo
Female
nthawi ya 4 koloko madzulo, pa msewu wa fumbi wochokera ku Madisi kupita ku Bowe, m'boma la Dowa
nthawi ya folo koloko madzulo, pa msewu wa fumbi wochokera ku Madisi kupita ku Bowe, m'boma la Dowa
Female
Mneneri wa polisi ya Mponela a Macpatson Msadala watsimikiza za ngoziyi, ndipo wati ngoziyi yachitika pomwe a Josephy Kambewu Nyamulani anayendetsa modutsa mulingo
Mneneri wa polisi ya Mponela a Makipatisoni Msadala watsimikiza za ngoziyi, ndipo wati ngoziyi yachitika pomwe a Joszefe Kambewu Nyamulani anayendetsa modutsa mulingo
Female
galimoto lomwe amaphuzira kuyendetsa okha, ndikukagunda malemuwa pa sukulu ya pulayimale ya Chimkoka m'bomali
galimoto lomwe amaphuzira kuyendetsa okha, ndikukagunda malemuwa pa sukulu ya pulayimale ya Chimkoka m'bomali
Female
Anthu anathamangira nawo malemuwa kuchipatala chaching'ono cha Bowe komwe achipatala anatsimikizira kuti mtsikanayu wamwalira
Anthu anathamangira nawo malemuwa kuchipatala chaching'ono cha Bowe komwe achipatala anatsimikizira kuti mtsikanayu wamwalira
Female
Pakadali pano a Josephy Kambewu akusungidwa mu chitokosi cha polisi, kudikira kukayankha mlandu
Pakadali pano a Jozefe Kambewu akusungidwa mu chitokosi cha polisi, kudikira kukayankha mlandu
Female
A Zephania amachokera m'mudzi wa M'biya, pamene a Josephy Kambewu Nyamulani, a zaka 33, amachokera m'mudzi wa Chimkoka, onse m'dera la mfumu yayikulu Chakhaza m'boma la Dowa
A Zephania amachokera m'mudzi wa M'biya, pamene a Jozefe Kambewu Nyamulani, a zaka fete fili, amachokera m'mudzi wa Chimkoka, onse m'dera la mfumu yayikulu Chakhaza m'boma la Dowa
Female
Dziko la Malawi tsopano liyamba kugula chimanga m'dziko la Tanzania kutsatira kuchotsedwa kwa chiletso chomwe chidaikidwa, kuletsa kugula chimangacho kamba ka nthenda yomwe idakhudza chimanga cha dzikoli
Dziko la Malawi tsopano liyamba kugula chimanga m'dziko la Tanzaniya kutsatira kuchotsedwa kwa chiletso chomwe chidaikidwa, kuletsa kugula chimangacho kamba ka nthenda yomwe idakhudza chimanga cha dzikoli
Female
Mu chikalata chomwe unduna wa zaulimi, kudzera mwa mlembi mu undunawu a Dickxie Kampani watulutsa, anthu ochita malonda a chimanga tsopano atha kuyitanitsanso chimangachi
Mu chikalata chomwe unduna wa zaulimi, kudzera mwa mlembi mu undunawu a Dikisi Kampani watulutsa, anthu ochita malonda a chimanga tsopano atha kuyitanitsanso chimangachi
Female
Chikalatachi chati boma la Tanzania laperekanso umboni wosonyeza kuti chimangacho sichili pa chiopsezo cha matenda a Lethal Necrosis omwe adakhudza chimangacho
Chikalatachi chati boma la Tanzaniya laperekanso umboni wosonyeza kuti chimangacho sichili pa chiopsezo cha matenda a lefo nekulosisi omwe adakhudza chimangacho
Female
Kuyitanitsa chimanga kuchoka m'dziko la Tanzania kudadza kutsatira kuchepa kwa chimanga m'dziko muno
Kuyitanitsa chimanga kuchoka m'dziko la Tanzaniya kudadza kutsatira kuchepa kwa chimanga m'dziko muno
Female
Bodi ya Mulhako wa Alhomwe yapempha mamembala ake kuti aziunika bwino nkhani zina asadayankhulepo
Bodi ya Mulhako wa Alomwe yapempha mamembala ake kuti aziunika bwino nkhani zina asadayankhulepo
Female
Wapampando wa bodiyi a Muchanakwaye Mpuluka wati pali ndondomeko zokhazikika zimene adaziika zimene anthu ayenera kutsatira akakhala ndi nkhawa zawo, mmalo mongothamangira kwa atolankhani
Wapampando wa bodiyi a Muchanakwaye Mpuluka wati pali ndondomeko zokhazikika zimene adaziika zimene anthu ayenera kutsatira akakhala ndi nkhawa zawo, mmalo mongothamangira kwa atolankhani
Female
Iwo amayankhapo malinga ndi zimene ena mwa mafumu a chi Lhomwe adafotozera atolankhani Lachisanu kuti sakugwirizana ndi kusankhidwa kwa a Kaduya kukhala mfumu yaikulu ya Alhomwe
Iwo amayankhapo malinga ndi zimene ena mwa mafumu a chi Lomwe adafotozera atolankhani Lachisanu kuti sakugwirizana ndi kusankhidwa kwa a Kaduya kukhala mfumu yaikulu ya Alomwe
Female
A Mpuluka adati gulu la Mulhako wa Alhomwe ndi la chikhalidwe osati za ndale kapena chipembedzo
A Mpuluka adati gulu la Mulakho wa Alomwe ndi la chikhalidwe osati za ndale kapena chipembedzo
Female
Iwo apempha anthu a mtunduwu kuti apewe kuwagwiritsa ntchito pokwaniritsa zolinga zoposa za gululi
Iwo apempha anthu a mtunduwu kuti apewe kuwagwiritsa ntchito pokwaniritsa zolinga zoposa za gululi
Female
A Kaduya adasankidwa kukhala ogwilizila mfumu ya alomwe mchaka cha 2021, ndiye n'chifukwa chiyani anthuwa akubwera pano ndi nkhawa zawo" Iwo adafunsa
A Kaduya adasankidwa kukhala ogwilizila mfumu ya alomwe mchaka cha twente twente wani, ndiye n'chifukwa chiyani anthuwa akubwera pano ndi nkhawa zawo" Iwo adafunsa
Female
Oweruza milandu pa bwalo la milandu la Mchinji First Grade magistrate a Yohane Nkhata walamula wokuba ng’ombe, a Chiletso Tembo a zaka 31
Oweruza milandu pa bwalo la milandu la Mchinji fesiti giledi majesitileti a Yohane Nkhata walamula wokuba ng’ombe, a Chiletso Tembo a zaka fete wani
Female
yemwe pamodzi ndi anzake akhala akuzunguza m'dera la Kamwendo ndi midzi ina yoyandikana nayo kukakhala ku ndende zaka 9
yemwe pamodzi ndi anzake akhala akuzunguza m'dera la Kamwendo ndi midzi ina yoyandikana nayo kukakhala ku ndende zaka naini
Female
Woimira boma, Inspector Peter Fuluwenza adauza bwaloli kuti chaka chatha m’mwezi wa September, apolisi pa Kamwendo Trading adalandira malipoti akuthyoledwa khola m’mudzi wa Chalilima
Woimira boma, Insipekita pita Fuluwenza adauza bwaloli kuti chaka chatha m’mwezi wa Sepitemba, apolisi pa Kamwendo Thileding’I adalandira malipoti akuthyoledwa khola m’mudzi wa Chalilima
Female
pomwe mbava zidaba ng’ombe zitatu; ziwiri zazikazi ndi imodzi yaimuna yokoka ngolo ya ndalama zokwana pafupifupi K1.6 million usiku wa pa September 12, 2023
pomwe mbava zidaba ng’ombe zitatu; ziwiri zazikazi ndi imodzi yaimuna yokoka ngolo ya ndalama zokwana pafupifupi wani pointi sikisi miliyoni usiku wa pa sepitemba twelofu twente twente fili
Female
Asanagamulidwe mlanduwo, a Tembo anali ndi milandu ina iwiri yoti ayankhe yokhudzaso kuba ng’ombe, komanso kuthawathawa
Asanagamulidwe mlanduwo, a Tembo anali ndi milandu ina iwiri yoti ayankhe yokhudzaso kuba ng’ombe, komanso kuthawathawa
Female
Mchitidwe wakuba ng'ombe ukukula zomwe zapangitsa eni ng'ombe kumaziika m'makola apafupi ndi pakhomo pawo
Mchitidwe wakuba ng'ombe ukukula zomwe zapangitsa eni ng'ombe kumaziika m'makola apafupi ndi pakhomo pawo
Female
A Tembo amachokera m'mudzi mwa Mzikawola, mfumu yayikulu Mlonyeni ndipo a Jeffrey Chibwinja amachokera kwa Kamwendo, mfumu yayikulu Zulu m'boma la Mchinji
A Tembo amachokera m'mudzi mwa Mzikawola, mfumu yayikulu Mlonyeni ndipo a Jeffrey Chibwinja amachokera kwa Kamwendo, mfumu yayikulu Zulu m'boma la Mchinji
Female
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu achikulire m'dziko muno la Malawi Network of Older Persons Organisations ladzudzula mchitidwe wopitilira kupha anthu achikulire umene ukupitilira m'dziko muno pa nkhani zopanda pake
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu achikulire m'dziko muno la Malawi Netiweki ofu ewoda pewosonzi oganaizeshonzi ladzudzula mchitidwe wopitilira kupha anthu achikulire umene ukupitilira m'dziko muno pa nkhani zopanda pake
Female
Mkulu wa bungweli a Andrew Kabvala, wati boma, nthambi yoona zachitetezo komanso mabungwe omwe siaboma akuyenera kugwirana manja pothana ndi mchitidwewu
Mkulu wa bungweli a Andrew Kabvala, wati boma, nthambi yoona zachitetezo komanso mabungwe omwe siaboma akuyenera kugwirana manja pothana ndi mchitidwewu
Female
Ine ndi wokhumudwa kuona kuti boma komanso mabungwe ena amene anapatsidwa mphanvu zothetsa mchitidwewu sakuchitapo kanthu
Ine ndi wokhumudwa kuona kuti boma komanso mabungwe ena amene anapatsidwa mphanvu zothetsa mchitidwewu sakuchitapo kanthu
Female
Pempholi likudza kutsatira kuphedwa kwa a Linly Ngoloma a zaka 84 ochokera m'mudzi wa Gulumba
Pempholi likudza kutsatira kuphedwa kwa a Linile Ngoloma a zaka eite folo ochokera m'mudzi wa Gulumba
Female
mfumu yayikulu Chikumbu m'boma la Mulanje amene abale awo amawakaikira kuti ndi mfiti, A Ngoloma anaphedwa usiku wa pa 18 January chaka chino
mfumu yayikulu Chikumbu m'boma la Mulanje amene abale awo amawakaikira kuti ndi mfiti, A Ngoloma anaphedwa usiku wa pa eitini Januwale chaka chino
Female
Bambo wina wa zaka makumi atatu wa m’mudzi wa Misale mfumu yaikulu Mlonyeni m’boma la Mchinji wadabwitsa anthu atapha ng'ombe ya mwini masana alero, anthu akuona
Bambo wina wa zaka makumi atatu wa m’mudzi wa Misale mfumu yaikulu Mlonyeni m’boma la Mchinji wadabwitsa anthu atapha ng'ombe ya mwini masana alero, anthu akuona
Female
ati poyiganizira kuti inamupondera ndikudya tomato wake yemwe anayala panja pa khomo la makolo ake masiku angapo apitawa
ati poyiganizira kuti inamupondera ndikudya tomato wake yemwe anayala panja pa khomo la makolo ake masiku angapo apitawa
Female
Malingana ndi mwini ng'ombeyo a Chrispine Chimkono a mdera lomwelo, chiwetocho chinaponda tomato wa munthu wina ndipo mnyamatayu anatenga khasu ndikuyamba kutema ng'ombeyo
Malingana ndi mwini ng'ombeyo a Khilisipini Chimkono a mdera lomwelo, chiwetocho chinaponda tomato wa munthu wina ndipo mnyamatayu anatenga khasu ndikuyamba kutema ng'ombeyo
Female
yomwe inali pamodzi ndi zinzake, mpaka kupha kwinaku akuopseza abusa ndi eni akewo kuti awaphera limodzi
yomwe inali pamodzi ndi zinzake, mpaka kupha kwinaku akuopseza abusa ndi eni akewo kuti awaphera limodzi
Female
M'modzi wa anthu omwe anaona izi zikuchitika a Alufandiga Kamsuliza ati aliyense anaima mutu posakhulupirira zomwe zimachitika pa nthawiyI
M'modzi wa anthu omwe anaona izi zikuchitika a Alufandiga Kamsuliza ati aliyense anaima mutu posakhulupirira zomwe zimachitika pa nthawiyI
Female
Atatero, mnyamatayo anayamba kuyikokera ng'ombeyo kunyumba kwa makolo ake ndi kumauza anthu kuti amene atamuyandikire nayeso aona zomwe ng'ombe-yo yaona, kwinaku akumwa bibida
Atatero, mnyamatayo anayamba kuyikokera ng'ombeyo kunyumba kwa makolo ake ndi kumauza anthu kuti amene atamuyandikire nayeso aona zomwe ng'ombe-yo yaona, kwinaku akumwa bibida
Female
Apolisi atafika pamalopo, mkuluyu sanathawe koma kuwalondola ndi kuyamba kuwatukwana, n'kumawaopseza
Apolisi atafika pamalopo, mkuluyu sanathawe koma kuwalondola ndi kuyamba kuwatukwana, n'kumawaopseza
Female
Anthu ena omwe amaona izi zikuchitika ati akuganizira kuti mnyamatayo anali atadya fodya wamkulu chifukwa ngakhale m'mbuyomu
Anthu ena omwe amaona izi zikuchitika ati akuganizira kuti mnyamatayo anali atadya fodya wamkulu chifukwa ngakhale m'mbuyomu
Female
wakhala akuopseza mayi ake omwe kuti akapitiriza kupanga chibwana tsiku lina adzawakwilira a moyo
wakhala akuopseza mayi ake omwe kuti akapitiriza kupanga chibwana tsiku lina adzawakwilira a moyo
Female
Pakadali pano, apolisi amanga mkuluyu ndipo akumusunga ku Namizana, kudikira kukaonekera ku khothi
Pakadali pano, apolisi amanga mkuluyu ndipo akumusunga ku Namizana, kudikira kukaonekera ku khothi
Female
Bwalo la milandu ku Thyolo lagamula a Miliward Stanley a zaka 18 zakubadwa kukagwira ndende ya zaka khumi ndi zinayi atapeza wolakwa pa mlandu wogwilira ana atatu, onse azaka zinayi
Bwalo la milandu ku Thyolo lagamula a Miliwadi sitanile a zaka 18 zakubadwa kukagwira ndende ya zaka khumi ndi zinayi atapeza wolakwa pa mlandu wogwilira ana atatu, onse azaka zinayi
Female
Felix Senzani yemwe ndi oyimira boma pa milandu anauza bwaloli kuti pa 17 mwezi uno wa January, a Stanley anakokera anawa m'munda wa chimanga
Felikisi Senzani yemwe ndi oyimira boma pa milandu anauza bwaloli kuti pa seventini mwezi uno wa Januwale, a Sitanile anakokera anawa m'munda wa chimanga
Female
mmene anawagwilira, panthawi yomwe ankapita kunyumba kuchokera ku mtsinje wa Namichimba
mmene anawagwilira, panthawi yomwe ankapita kunyumba kuchokera ku mtsinje wa Namichimba
Female
Iwo anauzanso bwaloli kuti mnyamata yemwe amadutsa ndiye anagwila wopalamulayu kutsatira mfuwu womwe unamveka kuchokera m'mundamu
Iwo anauzanso bwaloli kuti mnyamata yemwe amadutsa ndiye anagwila wopalamulayu kutsatira mfuwu womwe unamveka kuchokera m'mundamu
Female
Ndipo poonekera kubwalori a Stanley anavomera mlanduwu. Apa oweruza milandu Kondani Chinangwa anagamula wopalamulayu kukakhala kundende zaka 14
Ndipo poonekera kubwalori a Sitanile anavomera mlanduwu. Apa oweruza milandu Kondani Chinangwa anagamula wopalamulayu kukakhala kundende zaka fotini
Female
kuti ena akhalidwe longa ili atengerepo phunziro, ponena kuti mchitidwe wogwilira ukuchulukira m'bomali
kuti ena akhalidwe longa ili atengerepo phunziro, ponena kuti mchitidwe wogwilira ukuchulukira m'bomali
Female
Stanley amachokera m'mudzi wa Chibwana mfumu yaikulu Nchiramwera m'bomali
Sitanile amachokera m'mudzi wa Chibwana mfumu yaikulu Nchiramwera m'bomali
Female
Achinyamata m'boma la Likoma awapempha kuti akhale patsogolo kuphunzitsa komanso kudziwisa anthu za kufunikira kotenga gawo pa zitukuko zosiyanasiyana komanso nkhani za umoyo m'bomali
Achinyamata m'boma la Likoma awapempha kuti akhale patsogolo kuphunzitsa komanso kudziwisa anthu za kufunikira kotenga gawo pa zitukuko zosiyanasiyana komanso nkhani za umoyo m'bomali
Female
Izi aziyankhula pamene komiti yaikulu yoona za achinyamata m'bomali inakumana ndi magulu a achinyamata okwana khumi ndi awiri ochokera m'bomali
Izi aziyankhula pamene komiti yaikulu yoona za achinyamata m'bomali inakumana ndi magulu a achinyamata okwana khumi ndi awiri ochokera m'bomali
Female
ndipo akambirana nkhani zosiyanasiyana za mmene angapitisire patsogolo ntchito zachitukuko komanso umoyo wabwino
ndipo akambirana nkhani zosiyanasiyana za mmene angapitisire patsogolo ntchito zachitukuko komanso umoyo wabwino
Female
Poyankhula ndi Times 360 Malawi, wachiwiri kwa wapampando wa komitiyi, a Emanuel Kapekenya wati ndi kofunika kwambiri
Poyankhula ndi Taimusi fili sikisite Malawi, wachiwiri kwa wapampando wa komitiyi, a Emanuwelo Kapekenya wati ndi kofunika kwambiri
Female
kuti achinyamatawa azitenga nawo gawo pachitukuko ndi kulimbikisa anthu pa ntchito komanso nkhani zokhudza umoyo wabwino
kuti achinyamatawa azitenga nawo gawo pachitukuko ndi kulimbikisa anthu pa ntchito komanso nkhani zokhudza umoyo wabwino
Female
Iwo ati nthawi zambiri anthu okhala m'bomali amayang'anira kwambiri ntchito za usodzi kusiya zitukuko monga misewu, nyumba zabwino, komanso zokhudza zaukhondo monga kukhala ndi zimbuzi zabwino
Iwo ati nthawi zambiri anthu okhala m'bomali amayang'anira kwambiri ntchito za usodzi kusiya zitukuko monga misewu, nyumba zabwino, komanso zokhudza zaukhondo monga kukhala ndi zimbuzi zabwino
Female
Kotero, a Kapekenya ati ndi udindo wa achinyamatawa kuthana ndi mavutowa kuti bomali likhale lotukuka komanso lathanzi
Kotero, a Kapekenya ati ndi udindo wa achinyamatawa kuthana ndi mavutowa kuti bomali likhale lotukuka komanso lathanzi
Female
Wachiwiri kwa nduna yoona za maphunziro m'dziko muno a Nancy Chaola Mdooko walangiza ophunzira pa sukulu ya sekondale
Wachiwiri kwa nduna yoona za maphunziro m'dziko muno a Nanse Chaola Mdooko walangiza ophunzira pa sukulu ya sekondale
Female
yoyendera ya Holy Family m'boma la Phalombe kuti azilimbikira maphunziro awo ndi cholinga choti adzakwaniritse masomphenya a Malawi 2063
yoyendera ya Hole Famile m'boma la Phalombe kuti azilimbikira maphunziro awo ndi cholinga choti adzakwaniritse masomphenya a Malawi twente sikisite filii
Female
Ndunayi yayankhula izi pamene imayendera pulojekiti ya Malawi Education Reform Program, m'mene undunawu ukumanga midadada yophunzilira m'sukulu za pulaimale komanso sekondale
Ndunayi yayankhula izi pamene imayendera pulojekiti ya Malawi Edukeshoni lifomu pulogalamu , m'mene undunawu ukumanga midadada yophunzilira m'sukulu za pulaimale komanso sekondale
Female
m'maboma onse 34 a dziko lino. Zambiri zili mu kanemayu. Wolemba ndi kujambula Grecium Gama
m'maboma onse fete folo a dziko lino. Zambiri zili mu kanemayu. Wolemba ndi kujambula Gileshamu Gama
Female
Ena mwa akadaulo a ntchito za malonda komanso chuma m'dziko muno afotokozapo za kufunikira kokhala ochangamuka pofikira ndondomeko zimene zingathandizire kupititsa patsogolo ntchito za chuma
Ena mwa akadaulo a ntchito za malonda komanso chuma m'dziko muno afotokozapo za kufunikira kokhala ochangamuka pofikira ndondomeko zimene zingathandizire kupititsa patsogolo ntchito za chuma
Female
Mkulu wa kampani ya Legacy BV, Benedicto Bena Nkhoma, amayankhula pa mwambo wapadera wotchedwa ‘Meet and greet cocktail’
Mkulu wa kampani ya Legase BiVi, Benedikiti Bena Nkhoma, amayankhula pa mwambo wapadera wotchedwa ‘miti andi giliti kokotelo
Female
umene Kampani yophunzitsa anthu ukadaulo wa ntchito ya Sycamore Consult idachititsa mu mzinda wa Blantyre
umene Kampani yophunzitsa anthu ukadaulo wa ntchito ya Sikamo konzati idachititsa mu mzinda wa Bulantaya
Female
Wapampando wa board ya kampani ya Sycamore Consult John Kamanga wati cholinga cha mkumanowu chinali kubweretsa pamodzi atsogoleri
Wapampando wa bodi ya kampani ya Sikamo Konzati Joni Kamanga wati cholinga cha mkumanowu chinali kubweretsa pamodzi atsogoleri
Female