audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
komanso kusanthulira limodzi ndondomeko za mmene akulu akulu angayendetsere ntchito za mabungwe awo
komanso kusanthulira limodzi ndondomeko za mmene akulu akulu angayendetsere ntchito za mabungwe awo
Female
Bwalo la milandu ku Nkhata Bay lagamula kuti Yoswa Nyirenda, yemwe anatsegula chipatala mkati mwa nyumba yake popanda chilolezo
Bwalo la milandu ku Nkhata Bay lagamula kuti Yoswa Nyirenda, yemwe anatsegula chipatala mkati mwa nyumba yake popanda chilolezo
Female
apereke chindapusa cha ndalama zokwana K100,000 pa mlanduwu, Nyirenda anavomera mlanduwu
apereke chindapusa cha ndalama zokwana wani handede sauzande kwacha pa mlanduwu, Nyirenda anavomera mlanduwu
Female
Nyirenda anavomera mlanduwu ndipo anapempha kuti chigamulo chake chisakhale chokhwima popeza amadwala matenda a kuthamanga kwa magazi komanso kuti ndi wa ulumali mbali ina
Nyirenda anavomera mlanduwu ndipo anapempha kuti chigamulo chake chisakhale chokhwima popeza amadwala matenda a kuthamanga kwa magazi komanso kuti ndi wa ulumali mbali ina
Female
Amene anayimira boma pa mlanduwu anati bamboyu si katswiri wopereka mankhwala kwa anthu zomwe zimayika miyoyo yawo pa chiopsezo
Amene anayimira boma pa mlanduwu anati bamboyu si katswiri wopereka mankhwala kwa anthu zomwe zimayika miyoyo yawo pa chiopsezo
Female
Nyirenda walipira ndalamayi koma bwalo lamuchenjeza kuti asadzachitenso za chipatala pokhapokha atapatsidwa chilolezo kutero
Nyirenda walipira ndalamayi koma bwalo lamuchenjeza kuti asadzachitenso za chipatala pokhapokha atapatsidwa chilolezo kutero
Female
Thupi la malemu Katelele Ching'oma tsopano likutengedwa ku nyumba ya Chisoni ya chipatala chachikulu cha Kamuzu ku Lilongwe kupita kumudzi kwawo ku Nsanje
Thupi la malemu Katelele Ching'oma tsopano likutengedwa ku nyumba ya Chisoni ya chipatala chachikulu cha Kamuzu ku Lilongwe kupita kumudzi kwawo ku Nsanje
Female
Katelele, yemwe wamwalira kucha kwa lero, ayikidwa m’manda mawa ku Nsanje. Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera mmawa uno
Katelele, yemwe wamwalira kucha kwa lero, ayikidwa m’manda mawa ku Nsanje. Mtsogoleri wa dziko lino a Lazalasi Chakwera mmawa uno
Female
akuyendera ntchito yokuza madzi m'boma la Nkhata Bay, yomwe ili pansi pa bungwe la Northern Region Water Board
akuyendera ntchito yokuza madzi m'boma la Nkhata Bay, yomwe ili pansi pa bungwe la Noveni lijoni wota bodi
Female
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wapempha mfumu ya Alhomwe a Kaduya imene angoikhazikitsa kumene kukhala chida cholunzanitsa anthu
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wapempha mfumu ya Alomwe a Kaduya imene angoikhazikitsa kumene kukhala chida cholunzanitsa anthu
Female
Chakwera wapemphanso mfumuyi kuonetsetsa kuti akugwira ntchito za chitukuko pamodzi ndi atsogoleri a boma
Chakwera wapemphanso mfumuyi kuonetsetsa kuti akugwira ntchito za chitukuko pamodzi ndi atsogoleri a boma
Female
Mtsogoleri wa dziko linoyu wadzodza Kaduya kukhala mfumu yaikulu ya Alhomwe ndipo ilowa m'malo mwa malemu Ngolongoliwa
Mtsogoleri wa dziko linoyu wadzodza Kaduya kukhala mfumu yaikulu ya Alomwe ndipo ilowa m'malo mwa malemu Ngolongoliwa
Female
Bungwe la Malawi Gaming and Lotteries Authority (Magla) lalipirira ndalama ya mayeso ophunzira okwana 753 omwe anakanika kulipira ndalama kuti alembe mayeso a boma a chaka chino
Bungwe la Malawi Geming’I andi lotalezi ofolite (Magila) lalipirira ndalama ya mayeso ophunzira okwana seveni handede andi fifite fili omwe anakanika kulipira ndalama kuti alembe mayeso a boma a chaka chino
Female
Bungweli lalipira ndalama zokwana K15 miliyoni ndipo lathandiza ophunzira amene akuyembekezela kulemba mayeso a mpulaimale, a sekondale , JCE komanso MSCE
Bungweli lalipira ndalama zokwana fifitini miliyoni kwacha ndipo lathandiza ophunzira amene akuyembekezela kulemba mayeso a mpulaimale, a sekondale, a Jeyisii ii komanso Emuesisi ii
Female
Poyankhula pa mwambo wopereka ndalamazi mu mzinda wa Zomba, mkulu wa Magla Rachel Mijiga wati bungweli linakhudzidwa ndi chiwerengero cha ophunzira amene anakanika kulipira kuti alembe mayeso
Poyankhula pa mwambo wopereka ndalamazi mu mzinda wa Zomba, mkulu wa Magila Recho Mijiga wati bungweli linakhudzidwa ndi chiwerengero cha ophunzira amene anakanika kulipira kuti alembe mayeso
Female
Bwalo la First Grade Magistrate ku Mponela m’boma la Dowa lagamula kuti Yohane Chiphwanya wa zaka 24 akagwire ukayidi kwa zaka zinayi litamupeza wolakwa pa mulandu wothyola nyumba ndi kuba
Bwalo la Fesiti giledi majesitileti ku Mponela m’boma la Dowa lagamula kuti Yohane Chiphwanya wa zaka twente folo akagwire ukayidi kwa zaka zinayi litamupeza wolakwa pa mulandu wothyola nyumba ndi kuba
Female
Amene anayimira mbali ya boma pa mulanduwu Evance Chambuluka anauza bwalo kuti Chiphwanya anathyola nyumba yogulitsiramo zakumwa zoledzeretsa
Amene anayimira mbali ya boma pa mulanduwu Evansi Chambuluka anauza bwalo kuti Chiphwanya anathyola nyumba yogulitsiramo zakumwa zoledzeretsa
Female
chaka chatha ndikubamo katundu wa ndalama zokwana K250,000. Woyankhulira polisi ya Mponela Macpatson Msadala
chaka chatha ndikubamo katundu wa ndalama zokwana thu handede andi fifite sauzande kwacha . Woyankhulira polisi ya Mponela Mackipatisoni Msadala
Female
wati Chambuluka anapempha bwalo kuti lipereke chilango chokhwima kwa wolakwayu kuti ena atengerepo phunziro
wati Chambuluka anapempha bwalo kuti lipereke chilango chokhwima kwa wolakwayu kuti ena atengerepo phunziro.
Female
Woweruza milandu Talakwanji M'ndala anagwirizana ndi woyimira boma ndipo analamula kuti Chiphwanya akagwire ukayidi kwa zika zinayi
Woweruza milandu Talakwanji M'ndala anagwirizana ndi woyimira boma ndipo analamula kuti Chiphwanya akagwire ukayidi kwa zika zinayi
Female
Mkuluyu amachokera m’mudzi wa Makwani, mfumu yayikulu Dzoole m’boma la Dowa. Maanja okwana 1,000 ku Chatoloma ndi madera ena ku Kasungu
Mkuluyu amachokera m’mudzi wa Makwani, mfumu yayikulu Dzoole m’boma la Dowa. Maanja okwana wanis auzande ku Chatoloma ndi madera ena ku Kasungu
Female
tsopano atuluka mu nsinga za vuto la kusowa kwa madzi limene linayamba mphasa kwa nthawi yayitali m’madera ambiri m’bomali
tsopano atuluka mu nsinga za vuto la kusowa kwa madzi limene linayamba mphasa kwa nthawi yayitali m’madera ambiri m’bomali
Female
Mnyamata wa zaka 24 Maxwell Sithole, yemwenso ndi mwiniwake wa Kampani yaying’ono yogawa madzi a pampopi, ndi amene wapulumutsa maanjawa
Mnyamata wa zaka twent efolo Makisiwelo Sithole, yemwenso ndi mwiniwake wa Kampani yaying’ono yogawa madzi a pampopi, ndi amene wapulumutsa maanjawa
Female
Sithole wauza Times 360 Malawi kuti anayamba malonda ogulitsa madzi pofuna kuchepetsa vuto la kusowa kwa madzi komanso kuti anthu azimwa madzi otetezedwa
Sithole wauza Taimusi fili sikisike Malawi kuti anayamba malonda ogulitsa madzi pofuna kuchepetsa vuto la kusowa kwa madzi komanso kuti anthu azimwa madzi otetezedwa
Female
Moffat Kajekeko ndi m’modzi wa makasitomala a kampani ya Sithole ndipo akuyikira umboni kuti banja lake tsopano likugwiritsa ntchito madzi a ukhondo
Mofati Kajekeko ndi m’modzi wa makasitomala a kampani ya Sithole ndipo akuyikira umboni kuti banja lake tsopano likugwiritsa ntchito madzi a ukhondo
Female
Akazi anga amadzuka m'cha mma wani koloko usiku kukasaka madzi, komanso madzi ake sanali otetezedwa. Koma kaamba ka kubwera kwa kampaniyi, vuto la kusowa kwa madzi pano ndi mbiri ya kale watero Kajekeko
Akazi anga amadzuka m'cha mma wani koloko usiku kukasaka madzi, komanso madzi ake sanali otetezedwa. Koma kaamba ka kubwera kwa kampaniyi, vuto la kusowa kwa madzi pano ndi mbiri ya kale watero Kajekeko
Female
Wayilesi ya BBC m'dzikolo yati Mfumu Charles ikudwala matenda okhudza njira yotayira madzi ndipo mfumuyi ikhala ikulowa m'chipatala posachedwa kuti akayipime
Wayilesi ya Bibisi m'dzikolo yati Mfumu Tchalosi ikudwala matenda okhudza njira yotayira madzi ndipo mfumuyi ikhala ikulowa m'chipatala posachedwa kuti akayipime
Female
Pakadali pano, mfumuyi yayamba yaimitsa maulendo ndi ntchito zina zomwe imayenera kugwira, mpaka itapeza bwino
Pakadali pano, mfumuyi yayamba yaimitsa maulendo ndi ntchito zina zomwe imayenera kugwira, mpaka itapeza bwino
Female
A Charles analowa ufumu mai awo Elizabeth atamwalira. Mfumukazi Elizabeth yachiwiri inakhala pa mpandowu kwa zaka 70 A Charles anawalonga ufumu pa 6 May 2023
A Tchalosi analowa ufumu mai awo Elizabefi atamwalira. Mfumukazi Elizabefi yachiwiri inakhala pa mpandowu kwa zakas evente A Tchalosis anawalonga ufumu pa Sikisi meyi twente twente fili
Female
Ena akuti matimu a mpira azikhala ndi sing’anga ngati akufuna kupambana pa masewero, pomwe ena akuti mankhwala sagwira ntchito mu mpira ndipo n’zotayitsa chabe nthawi
Ena akuti matimu a mpira azikhala ndi sing’anga ngati akufuna kupambana pa masewero, pomwe ena akuti mankhwala sagwira ntchito mu mpira ndipo n’zotayitsa chabe nthawi
Female
A Leo Mpulula a Mighty Wakawaka Tigers ali ndi maganizo ena. Apolisi m'boma la Mzimba amanga wophunzira kugwira ntchito ku khonsolo ya M'mbelwa, Gibson Kapeye
A Leo Mpulula a Maiite Wakawaka Taigazi ali ndi maganizo ena. Apolisi m'boma la Mzimba amanga wophunzira kugwira ntchito ku khonsolo ya M'mbelwa, Gibisoni Kapeye
Female
wa zaka 29 pomuganizira kuti anaba lamya ziwiri zamtundu wa Lenovo Mneneri wa polisi ya Mzimba a Peter Botha
wa zaka twente naini pomuganizira kuti anaba lamya ziwiri zamtundu wa Lenovo Mneneri wa polisi ya Mzimba a Pita Botha
Female
wati akuluakulu a khonsolo ya M'mbelwa ndiwo anadandaula za kusowa kwa lamyazi zomwe zinali zochitira kafukukufuku mu ofesi yoona kayendetsedwe ka ntchito za ma project
wati akuluakulu a khonsolo ya M'mbelwa ndiwo anadandaula za kusowa kwa lamyazi zomwe zinali zochitira kafukukufuku mu ofesi yoona kayendetsedwe ka ntchito za ma pulojekiti
Female
Ndipo apolisi akuti kafukufuku wawo wapeza kuti a Kapeye, omwe amagwira ntchito ku nthambi yoyang'anira ogwira ntchito ku khonsoloyi ndiwo anaba
Ndipo apolisi akuti kafukufuku wawo wapeza kuti a Kapeye, omwe amagwira ntchito ku nthambi yoyang'anira ogwira ntchito ku khonsoloyi ndiwo anaba
Female
Lamya yomwe anagulitsa ku Kasungu pamtemgo wa K20,000 ayipeza pomwe ina yapezakanso kunyumba komwe amakhala A Kapeye amachokera m'mudzi mwa Simon, mfumu yaikulu Kyungu m'boma la Karonga
Lamya yomwe anagulitsa ku Kasungu pamtemgo wa twente sauzande kwacha ayipeza pomwe ina yapezakanso kunyumba komwe amakhala A Kapeye amachokera m'mudzi mwa Simoni, mfumu yaikulu Kyungu m'boma la Karonga
Female
A polisi m'boma la Balaka apempha adindo a zipani zosiyanasiyana m'bomali kuti apewe mchitidwe wa ziwawa pamene nthawi yokopa anthu ikuyembekezeka kuyamba posachedwapa
A polisi m'boma la Balaka apempha adindo a zipani zosiyanasiyana m'bomali kuti apewe mchitidwe wa ziwawa pamene nthawi yokopa anthu ikuyembekezeka kuyamba posachedwapa
Female
Poyankhula ndi Times 360 Malawi pa mkumano umene polisi ya Balaka inakonza, mkulu wa polisiyi, Dan Sauteni
Poyankhula ndi Times 360 Malawi pa mkumano umene polisi ya Balaka inakonza, mkulu wa polisiyi, Dan Sauteni
Female
wati anthu achipani sakuyenela kuyambisa zachipolowe pa nthawi yomwe akuchititsa msonkhano wa ndale m'madera osiyanasiyana m'bomali ponena kuti izi zimabwezeretsa chitukuko m'mbuyo
wati anthu achipani sakuyenela kuyambisa zachipolowe pa nthawi yomwe akuchititsa msonkhano wa ndale m'madera osiyanasiyana m'bomali ponena kuti izi zimabwezeretsa chitukuko m'mbuyo
Female
Malingana ndi Sauteni, iwo alonjeza kugwira ntchito ndi aliyense posatengela chipani chimene akutsatira
Malingana ndi Sauteni, iwo alonjeza kugwira ntchito ndi aliyense posatengela chipani chimene akutsatira
Female
Ndipo m'modzi wa anthu amene anali nawo pa mkumanowu Hadja George Makalakala wati msokhanowu ndi wofunika kwambiri ndipo wabwera pa nthawi yake pamene zipani zikhale zikupangitsa misonkhano yosiyanasiyana
Ndipo m'modzi wa anthu amene anali nawo pa mkumanowu Haja joji Makalakala wati msokhanowu ndi wofunika kwambiri ndipo wabwera pa nthawi yake pamene zipani zikhale zikupangitsa misonkhano yosiyanasiyana
Female
Pamsokhanowu panali azipani monga, DPP, MCP, UTM, PP, UDF ndi zina
Pamsokhanowu panali azipani monga, Dipipi, Emusipi, Yutiemu, pipi, Yudiefu ndi zina
Female
Anthu okhala mu mzinda wa Lilongwe adandaula kuti galimoto zikuonongeka podutsa misewu imene ikukonzedwa
Anthu okhala mu mzinda wa Lilongwe adandaula kuti galimoto zikuonongeka podutsa misewu imene ikukonzedwa
Female
Lero podutsa mu msewu umene ukhale ndi misewu isanu ndi umodzi, tinapeza galimoto zingapo zitaonongeka ma ball joint kamba ka ma bump
Lero podutsa mu msewu umene ukhale ndi misewu isanu ndi umodzi, tinapeza galimoto zingapo zitaonongeka ma Bo jointi kamba ka ma bampu
Female
A polisi m'boma la Balaka apempha adindo a zipani zosiyanasiyana m'bomali kuti apewe mchitidwe wa ziwawa pamene nthawi yokopa anthu ikuyembekezeka kuyamba posachedwapa
A polisi m'boma la Balaka apempha adindo a zipani zosiyanasiyana m'bomali kuti apewe mchitidwe wa ziwawa pamene nthawi yokopa anthu ikuyembekezeka kuyamba posachedwapa
Female
A Gusto Tuweh Gadama, omwe akuwazenga mlandu woyendetsa sukulu ya ukachenjede ya Cyprus komanso Jerusalem mopanda chilolezo chochokera kubungwe
A Gusito Tuwe Gadama, omwe akuwazenga mlandu woyendetsa sukulu ya ukachenjede ya saipulasi komanso Jerusalemu mopanda chilolezo chochokera kubungwe
Female
mopanda chilolezo chochokera kubungwe lomwe limayang'anira sukulu za ujachenjede za National Council for Higher Education, akuyembekezeka kufika ku bwalo la Milandu mu mzinda wa Lilongwe
mopanda chilolezo chochokera kubungwe lomwe limayang'anira sukulu za ujachenjede za Neshono khanso fo haya ejukeshoni, akuyembekezeka kufika ku bwalo la Milandu mu mzinda wa Lilongwe
Female
Bwalo la milandu m’boma la Mchinji lagamula bambo wa zaka makumi awiri a Akile Lyton kuti akakhale kundende zaka zitatu atapezeka wolakwa pa mlandu wothyola nyumba ndikuba katundu
Bwalo la milandu m’boma la Mchinji lagamula bambo wa zaka makumi awiri a Akile Layitoni kuti akakhale kundende zaka zitatu atapezeka wolakwa pa mlandu wothyola nyumba ndikuba katundu
Female
Woimira boma pa mlanduwo sergeant Misheck Kalawa, anauza bwaloli kuti bamboyu adamumanga pa 29 September, 2023 pomuganizira kuti anali m’modzi wa anthu
Woimira boma pa mlanduwo sergeant Misheki Kalawa, anauza bwaloli kuti bamboyu adamumanga pa twente naini sepitemba twente twente fili pomuganizira kuti anali m’modzi wa anthu
Female
omwe pa 3 January, 2022 anathyola nyumba yosungiramo katundu ya Mtapo ndi kuba katundu ndi zipangizo za magetsi oyendera mphamvu ya dzuwa za ndalama zoposa K1.7 million za alimi ku Kapiri
omwe pa fili januwale twente twente thu anathyola nyumba yosungiramo katundu ya Mtapo ndi kuba katundu ndi zipangizo za magetsi oyendera mphamvu ya dzuwa za ndalama zoposa wani pointi seveni miliyoni kwacha za alimi ku Kapiri
Female
Podandaula, bamboyu anapempha bwaloli kuti limuganizire kaamba adakali wachichepere, komanso kuti ali ndi banja lomwe limadalira iwowo
Podandaula, bamboyu anapempha bwaloli kuti limuganizire kaamba adakali wachichepere, komanso kuti ali ndi banja lomwe limadalira iwowo
Female
Koma woimira boma anapempha bwalo kuti lipereke chilango chokhwima chifukwa kuba ndi chimodzi mwa zinthu zomwe zikubwezeretsa m'mbuyo chitukuko cha dziko
Koma woimira boma anapempha bwalo kuti lipereke chilango chokhwima chifukwa kuba ndi chimodzi mwa zinthu zomwe zikubwezeretsa m'mbuyo chitukuko cha dziko
Female
Padakali pano apolisi akupitirizabe kusakasaka anthu ena omwe adali ndi a Lyton pamene amakaba katunduyo
Padakali pano apolisi akupitirizabe kusakasaka anthu ena omwe adali ndi a Lyitoni pamene amakaba katunduyo
Female
Oyimba Driemo komanso Eli Njuchi ndi omwe apata ndalama zambiri mu Blank Media Levy, ndalama zomwe zimaperekedwa ndi bungwe la Copyright Society of Malawi
Oyimba Diliyemo komanso Eli Njuchi ndi omwe apata ndalama zambiri mu Bulanki mediya leve, ndalama zomwe zimaperekedwa ndi bungwe la kopelaiti sosayate ofu malawi
Female
Iwo alandira ndalama zosachepera K5 million aliyense Skeffa Chimoto naye walandira ndalama yoti ndi yosachepera K4 million
Iwo alandira ndalama zosachepera faifi miliyoni kwacha a aliyense Skeffa Chimoto naye walandira ndalama yoti ndi yosachepera fo miliyoni kwacha
Female
Mukuyakhula kwake ngati mmodzi wa omwe alandira ndalama zambiri, Driemo wathokoza Cosoma kamba ka chikonzero chimenechi, ndipo wapempha aluso anzake kuti ndalamayi ayigwiritse bwino ntchito kuti iwapindulire kutsogolo
Mukuyakhula kwake ngati mmodzi wa omwe alandira ndalama zambiri, Diliyemo wathokoza kosoma kamba ka chikonzero chimenechi, ndipo wapempha aluso anzake kuti ndalamayi ayigwiritse bwino ntchito kuti iwapindulire kutsogolo
Female
Naye Soldier Lucius Banda, yemwe ali mlendo wolemekezeka, wapempha aluso kuti agwiritse bwino ntchito ndalamazi
Naye Soja Lusiyasi Banda, yemwe ali mlendo wolemekezeka, wapempha aluso kuti agwiritse bwino ntchito ndalamazi
Female
Mukanemayu, Driemo akulankhula pa mwambo wopereka ndalamazi ku hotela ya Crossroads ku Lilongwe, Lachitatu
Mukanemayu, Diliyemo akulankhula pa mwambo wopereka ndalamazi ku hotela ya khulosilodzi ku Lilongwe, Lachitatu
Female
Aluso osiyanasiyana kuphatikizapo oyimba ali ku hotela ya Crossroads mu mzinda wa Lilongwe komwe kuli mwambo wopereka ndalama za Blank Media Levy
Aluso osiyanasiyana kuphatikizapo oyimba ali ku hotela ya Khulosilodzi mu mzinda wa Lilongwe komwe kuli mwambo wopereka ndalama za Bulanki mediya leve
Female
Pa mwambowu, kumene mlendo wolemekezeka ndi Soldier Lucius Banda yemwe ndi mlangizi wa mtsogoleri wa dziko lino pa nkhani za achinyamata, kuperekedwa ma certificate kwa aluso omwe apeza ndalama zosachepera K1 million
Pa mwambowu, kumene mlendo wolemekezeka ndi Soldier Lucius Banda yemwe ndi mlangizi wa mtsogoleri wa dziko lino pa nkhani za achinyamata, kuperekedwa ma certificate kwa aluso omwe apeza ndalama zosachepera K1 million
Female
Ena mwa aluso omwe ali ku mwambowu ndi monga Driemo, Wikise, Skeffa Chimoto, Lawi, Joseph Nkasa, Hilco, Great Angels Choir, Zonke komanso Black Missionaries
Ena mwa aluso omwe ali ku mwambowu ndi monga Diliyemo, Wikise, Sikefa Chimoto, Lawi, Jozefe Nkasa, Hiuko, Gileti enjelozi kwaya, Zonke komanso Bulaki mishonalezi
Female
Bungwe la Copyright Society of Malawi (Cosoma) likupereka ndalama za Blank Media Levy zoyambira mwezi wa April 2023
Bungwe la kopelaiti sosayate ofu Malawi (kosoma) likupereka ndalama za Bulanki midiya levzi zoyambira mwezi wa epulo twente twente filii
Female
Mwa ena omwe ali m'gulu limeneli ndi Temwa, Rashley, Wikise, Joseph Nkasa, Billy Kaunda, Mlaka Maliro, Gwamba, Piksy
Mwa ena omwe ali m'gulu limeneli ndi Temwa, Rashile, Wikise, Jozefe Nkasa, bile Kaunda, Mlaka Maliro, Gwamba, Pikise
Female
Anthony Makondetsa, Black Missionaries, Great Angels, Hilco ndi Zonke. Komanso m'gulu lomweli muli aluso omwe adamwalira monga Atoht Manje, Tremour, WalyCris ndi Martse
Antone Makondetsa, Bulaki mishonalezi, Gileti enjelozi, Hiuko ndi Zonke. Komanso m'gulu lomweli muli aluso omwe adamwalira monga Atoti Manje, Thilema, wale khilisi ndi Matse
Female
Bwalo la milandu laling'ono ku Nathenje, latumiza mkulu woyang'anira nkhani za ndale m'chipani cha DPP, a Fredrick Billy Malata ku ndende ya Maula kwa masiku asanu ndi awiri
Bwalo la milandu laling'ono ku Nathenje, latumiza mkulu woyang'anira nkhani za ndale m'chipani cha Dipipi, a Fulediliki Bile Malata ku ndende ya Maula kwa masiku asanu ndi awiri
Female
A Malata, adamangidwa loweruka pa mlandu woipitsa mbiri ya wochita malonda a Alfred Gangata pogwiritsa ntchito masamba a mchezo
A Malata, adamangidwa loweruka pa mlandu woipitsa mbiri ya wochita malonda a Alafuledi Gangata pogwiritsa ntchito masamba a mchezo
Female
Iwo adatengeredwa ku bwalo la milandu ku Nathenje dzulo ndipo bwalo lawatumiza ku Maula kwa amasiku 7 ponena kuti chigamulo pa pempho lawo la belo chidzapelekedwa Lachiwiri sabata ya mawa
Iwo adatengeredwa ku bwalo la milandu ku Nathenje dzulo ndipo bwalo lawatumiza ku Maula kwa amasiku seveni ponena kuti chigamulo pa pempho lawo la belo chidzapelekedwa Lachiwiri sabata ya mawa
Female
Owayimilira a Malata a Gladwell Majekete atsimikiza za izi ndipo ati a Malata akasiyidwa ku Maula m'mawa wa lero atagona usiku wadzulo ku polisi ya Nathenje
Owayimilira a Malata a Giladiwelo Majekete atsimikiza za izi ndipo ati a Malata akasiyidwa ku Maula m'mawa wa lero atagona usiku wadzulo ku polisi ya Nathenje
Female
Akulowa ku ndende ya Maula, a Malata adalankhura mwachidule ndi Times 360 Malawi ndipo anati: "Amalawi akufuna kwabwino andithandize
Akulowa ku ndende ya Maula, a Malata adalankhura mwachidule ndi Taimusi fili sikisite Malawi ndipo anati: "Amalawi akufuna kwabwino andithandize
Female
Ombudsman, a Chief Justice komanso Inspector General of police andithandize ndikuvutika. Ndagona ku Area 3 police masiku atatu
Ombudzimani, a tchifi jasitisi komanso Insipekita jenelo ofu polisi andithandize ndikuvutika. Ndagona ku Areeliya fili pilisi masiku atatu
Female
dzulo ndagona ku Nathenje lero akukandisiya ku Maula pa nkhani zosamveka. Panopa mu zovala zanga muli msikidzi zokhazokha, ndikuvutika
dzulo ndagona ku Nathenje lero akukandisiya ku Maula pa nkhani zosamveka. Panopa mu zovala zanga muli msikidzi zokhazokha, ndikuvutika
Female
Madolo oyimba ndiye sakupuma chifukwa naye Onesimus akutsekulira chaka cha 2024 ndi mbale yaing’ono yomwe amayiti Extended Playlist mu chingerezi yotchedwa I am Strong
Madolo oyimba ndiye sakupuma chifukwa naye Onesimasi akutsekulira chaka cha twente twente folo ndi mbale yaing’ono yomwe amayiti ekisitendedi puleyi lisitit mu chingerezi yotchedwa ayi yamu sitiling’o
Female
Onesimus walengeza kale pa tsamba lake la mchezo kuti mwambo womvera nyimbo wa I am Strong, yomwe yasenza nyimbo zisanu ndi ziwiri, uchitikira ku Stakeout Bar, malo omwe ali ku hotela ya Amaryllis mu mzinda wa Blantyre
Onesimasi walengeza kale pa tsamba lake la mchezo kuti mwambo womvera nyimbo wa ayi yamu sitilong’o, yomwe yasenza nyimbo zisanu ndi ziwiri, uchitikira ku siteki auti ba, malo omwe ali ku hotela ya Amalezi mu mzinda wa Bulantaya
Female
Woimbayu yemwe amadziwikanso ndi nyimbo zake monga Solomon komanso Panado, wati akhalanso akukhazikitsa chimbalechi m'maiko monga South Africa, Kenya, Namibia ndi Botswana
Woimbayu yemwe amadziwikanso ndi nyimbo zake monga Solomoni komanso Panado, wati akhalanso akukhazikitsa chimbalechi m'maiko monga saufi afilika, Kenya, Namibiya ndi Botswana
Female
Zina mwa nyimbo zili mu chimbalechi chomwe chitulutsidwe pa 1 January ndi ‘Make Up Your Mind, Kubwera, I am Sorry, Nabanda komanso Runaway
Zina mwa nyimbo zili mu chimbalechi chomwe chitulutsidwe pa wani januwale ndi ‘meki apu yuwa maindi, Kubwera, ayi yamu sole, Nabanda komanso Ranawe
Female
Katswiri wochita zisudzo a Charles Mphoka, watipula osati sewero kumbali yochita zisudzo chifukwa pano akwanitsa zaka 43 mu ntchitoyi
Katswiri wochita zisudzo a Tchalosi Mphoka, watipula osati sewero kumbali yochita zisudzo chifukwa pano akwanitsa zaka fote fili mu ntchitoyi
Female
Mkuluyu, yemwenso ndi mkhalekale mu gulu la Kwathu Drama Group wananena izi Lolemba mu mzinda wa Blantyre pamene magulu awiri a anthu achichepere – Young Travellers komanso Arts Sustainability Lab
Mkuluyu, yemwenso ndi mkhalekale mu gulu la Kwathu Dilama gulupu wananena izi Lolemba mu mzinda wa Bulantaya pamene magulu awiri a anthu achichepere – Yang’i thilavelazi komanso Atsi sasitenabilite labu
Female
amaonetsa masewero awo otchedwa Fisi komanso Leaders at Crossroads ku Jacaranda Cultural Centre mu mzinda wa Blantyre
amaonetsa masewero awo otchedwa Fisi komanso lidazi ati khulosi lodzi ku Jakaranda kachulo senta mu mzinda wa Bulantaya
Female
Iwo anati zatengera chisomo cha Mulungu komanso khama ndi kukonda zisudzo kuti afike pamene ali pakadali pano
Iwo anati zatengera chisomo cha Mulungu komanso khama ndi kukonda zisudzo kuti afike pamene ali pakadali pano
Female
Mmayendedwe awo, a Mphoka womwe amadziwikanso kuti Magagula, alemba masewero ambiri a gulu la Kwathu pamodzi ndi malemu Eric Mabedi omwe amadziwika ndi dzina loti Jakobo
Mmayendedwe awo, a Mphoka womwe amadziwikanso kuti Magagula, alemba masewero ambiri a gulu la Kwathu pamodzi ndi malemu Eriki Mabedi omwe amadziwika ndi dzina loti Jakobo
Female
Nduna ya zaumoyo a Khumbize Kandodo Chiponda yati anthu asakhale ndi mantha kutsatira kudzanso kwa nthenda ya COVID-19. Izi zikudza anthu asanu nsi awiri atapezeka ndi nthendayi m'boma la Nsanje
Nduna ya zaumoyo a Khumbize Kandodo Chiponda yati anthu asakhale ndi mantha kutsatira kudzanso kwa nthenda ya COVIDI-naintini. Izi zikudza anthu asanu nsi awiri atapezeka ndi nthendayi m'boma la Nsanje
Female
Mu chikalata, ndunayi yati anthu akuyenerabe kukumbukira kutsatira njira zopewera nthendayi ndipo omwe sadabayitse katemera akuyenera kukabayitsa
Mu chikalata, ndunayi yati anthu akuyenerabe kukumbukira kutsatira njira zopewera nthendayi ndipo omwe sadabayitse katemera akuyenera kukabayitsa
Female
A Chiponda ati omwe adabayitsa katemera kamodzi kokha, akuyeneranso kukabayitsa booster. Ndunayi m'chikalatachi
A Chiponda ati omwe adabayitsa katemera kamodzi kokha, akuyeneranso kukabayitsa busita. Ndunayi m'chikalatachi
Female
yakumbutsanso anthu kuopsa kwa nthenda ya cholera yomwe yafala, ndipo yapempha anthu kutsatira njira zopewera nthendayi
yakumbutsanso anthu kuopsa kwa nthenda ya kolera yomwe yafala, ndipo yapempha anthu kutsatira njira zopewera nthendayi
Female
Chilengezereni za nthenda ya Cholera m'dziko muno mu March chaka chatha, anthu okwana 1,700 amwalira ndi nthendayi
Chilengezereni za nthenda ya kolera m'dziko muno mu machi chaka chatha, anthu okwana wani sauzande seveni handede amwalira ndi nthendayi
Female
Ofesi ya za umoyo ku Nsanje yalangiza anthu kuti atsatire njira zosiyanasiyana monga kuvala zotchinga kunkhope kuti apewe nthenda ya COVID-19
Ofesi ya za umoyo ku Nsanje yalangiza anthu kuti atsatire njira zosiyanasiyana monga kuvala zotchinga kunkhope kuti apewe nthenda ya COVIDI-naintini
Female
Izi zikutsatira kupezeka kwa anthu asanu ndi awiri amene ali ndi thendayi masiku awiri apitawa. Poyankhula ndi Times 360 Malawi, mneneri wa zaumoyo m'bomalo a George Mbotwa
Izi zikutsatira kupezeka kwa anthu asanu ndi awiri amene ali ndi thendayi masiku awiri apitawa. Poyankhula ndi Taimusi fili sikisite Malawi, mneneri wa zaumoyo m'bomalo a Joji Mbotwa
Female
wati mwa anthu anthu 7 apezekawa, awiri ndi ogwira ntchito zachipatala. Malingana ndi a Mbotwa, anthu atsopano omwe awapeza ndi matendawa amaonetsa zizindikiro za malungo
wati mwa anthu seveni apezekawa, awiri ndi ogwira ntchito zachipatala. Malingana ndi a Mbotwa, anthu atsopano omwe awapeza ndi matendawa amaonetsa zizindikiro za malungo
Female
koma atawayeza sanawapeze ndi malungo zomwe zinapangitsa kuti awayeze COVID-19 malingana n'kuti anali atatenga nthawi asanayeze matendawa
koma atawayeza sanawapeze ndi malungo zomwe zinapangitsa kuti awayeze COVIDI-naintini malingana n'kuti anali atatenga nthawi asanayeze matendawa
Female
Woyimba Driemo wati akuyembekezera kuchita zambiri zakupsya chaka chino pamene watulutsa nyimbo yatsopano yotchedwa 'Trailer' yomwe ikuchita bwino pa makina a internet pa masamba monga YouTube
Woyimba Diliemo wati akuyembekezera kuchita zambiri zakupsya chaka chino pamene watulutsa nyimbo yatsopano yotchedwa 'Thilera' yomwe ikuchita bwino pa makina a intaneti pa masamba monga yuchubu
Female
Mu nyimboyi, Driemo akuyimba za nyengo zomwe anthu amadutsamo tsiku ndi tsiku ndipo akufunsa Mulungu mafunso monga kuti n'chifukwa chani sadapereke danga loti anthu azitha kuona nyengo zomwe adutsemo
Mu nyimboyi, Driemo akuyimba za nyengo zomwe anthu amadutsamo tsiku ndi tsiku ndipo akufunsa Mulungu mafunso monga kuti n'chifukwa chani sadapereke danga loti anthu azitha kuona nyengo zomwe adutsemo
Female
Ndipo akupitiriza kuyankhanso kuti nyengo zimenezi zimabwera kuti mwina atizamitse kuti tiyende bwino m'moyomu
Ndipo akupitiriza kuyankhanso kuti nyengo zimenezi zimabwera kuti mwina atizamitse kuti tiyende bwino m'moyomu
Female
Driemo, yemwe chaka chatha adakaimba m'dziko la Ireland kwa nthawi yoyamba sadanene ngati kutulutsa 'Trailer' uli ulendo wogwiragwira chimbale koma wati anthu asimba lokoma chaka chino
Diliemo, yemwe chaka chatha adakaimba m'dziko la ailandi kwa nthawi yoyamba sadanene ngati kutulutsa 'Thilera' uli ulendo wogwiragwira chimbale koma wati anthu asimba lokoma chaka chino
Female
Chaka chatha, iye adatulutsa chimbale chotchedwa Mzaliwa. Pa nkhani ya misonkho, a Mulagha apempha boma kuti litchotse msonkho wa anthu a pantchito omwe amadula abusa
Chaka chatha, iye adatulutsa chimbale chotchedwa Mzaliwa. Pa nkhani ya misonkho, a Mulaya apempha boma kuti litchotse msonkho wa anthu a pantchito omwe amadula abusa
Female
Timalandila ndalama yapambale, nthawi zina imabwera yochepa, iwo atero. Iwo ati boma lichepetsenso msonkho omwe anthu amadulidwa akagula katundu ndi K10 pa K100 iliyonse
Timalandila ndalama yapambale, nthawi zina imabwera yochepa, iwo atero. Iwo ati boma lichepetsenso msonkho omwe anthu amadulidwa akagula katundu ndi teni kwacha pa handede kwacha iliyonse
Female
Mfumu yamzinda wa Lilongwe Khansala Richard Banda yatsimikizira anthu mumzindawu kuti boma litsiliza ntchito zokonza misewu
Mfumu yamzinda wa Lilongwe Khansala Litchadi Banda yatsimikizira anthu mumzindawu kuti boma litsiliza ntchito zokonza misewu
Female
zomwe layamba mumzindawu ndipo yapempha anthu kuti adekhe pomwe boma kudzera ku khonsoloyi likuyesetsa kukonza misewuyi kuti ikhale yolimba
zomwe layamba mumzindawu ndipo yapempha anthu kuti adekhe pomwe boma kudzera ku khonsoloyi likuyesetsa kukonza misewuyi kuti ikhale yolimba
Female
A Banda ati anthu asaone kuchedwa ndikutha kwa ntchitozi ponena kuti omwe akugwila ntchito zamisewuyi akungodikira kuti mvula ithe
A Banda ati anthu asaone kuchedwa ndikutha kwa ntchitozi ponena kuti omwe akugwila ntchito zamisewuyi akungodikira kuti mvula ithe
Female
kuti apitilize ntchitoyi poonjezera kuti khonsoloyi ikuonesetsa kuti misewu yomwe ikukonzedwa ikhala yapamwamba Iwo amalankhula izi lero mdera la Chipasula mumzindawu
kuti apitilize ntchitoyi poonjezera kuti khonsoloyi ikuonesetsa kuti misewu yomwe ikukonzedwa ikhala yapamwamba Iwo amalankhula izi lero mdera la Chipasula mumzindawu
Female
pomwe anatsogolera ntchito yokonza malo ena omwe aonongeka pa msewu wa Chipasula. Mfumuyi yati khonsoloyi ili ndi mapulani okonza msewu wa Chidzanja
pomwe anatsogolera ntchito yokonza malo ena omwe aonongeka pa msewu wa Chipasula. Mfumuyi yati khonsoloyi ili ndi mapulani okonza msewu wa Chidzanja
Female
kupita ku 23 komanso kuchoka pa Marshal kupita ku Malangalanga ndi ina. Mmodzi mwa anthu aku Chipasula, a Dorothy Mbedza yemwe wadzudzula boma lammbuyomu pomanga misewu yosalimba
kupita ku twente fili komanso kuchoka pa Mashol kupita ku Malangalanga ndi ina. Mmodzi mwa anthu aku Chipasula, a Dolofe Mbedza yemwe wadzudzula boma lammbuyomu pomanga misewu yosalimba
Female